Boma lati lichotsa eni migodi m’malo okwelera minibasi
Eni minibus atadandaula kuti akumapereka ndalama zambiri kwa eni migodi komanso oitanira, boma lati lichotsa anthuwa m'malo okwelera minibasi. Nduna ya Zofalitsa Nkhani, yemwenso ndi m'meneri wa boma a Gospel Kazako ndi omwe anena izi… ...