Patricia Kaliati ayamikira wapampando wa MEC
M'modzi mwa akuluakulu a mgwirizano wa Tonse, a Patricia Kaliati, ayamikira wapampando wa bungwe loyendetsa zisankho la MEC a Justice Dr Chifundo Kachale ponena kuti akugwira bwino ntchito. A Kaliati amayankhula izi mu mchipinda cha… ...