Opezeka ndi Corona 8 athawa pamalo owasungira
Anthu asanu ndi atatu (8) omwe anapezeka ndikachilombo ka corona komwe kakumayambitsa matenda a COVID-19, athawa pamalo omwe amawasungira kwa Kameza mu nzinda wa Blantyre. Watsimikiza zankhaniyi ndi nkulu wa zaumoyo mu mzindawu Dr Gift… ...