Bullets bus finally in Malawi

Nyasa Big Bullets Malawi Football

Just minutes after losing to Moyale Barracks in the Fisd Challenge Cup semifinals on Sunday, Nyasa Big Bullets fans found solace when the much awaited Marcopolo team bus arrived in the country from South Africa.

Nyasa Big Bullets Malawi FootballThe bus arrived at Mwanza border at exactly five o’clock and it was welcomed by thousands of supporters, as they danced around while praising sponsors Nyasa Manufacturing Company Limited.

On Tuesday, interim chairman Noel Lipipa and supporters chairman Stone Mwamadi, General Secretary for the supporters Mabvuto Chiwambo, Isaac Osman and Chingeni Gumbala left the country for the rainbow nation to collect the machine.

The purchase of the bus is one of the promises that have been fulfilled by NMC after officially taking over the club from supporters.

Apart from the bus, NMC will build a club house and a stadium and will list the club on Malawi Stock Exchange within the next five years, with at least 30 percent of the shares being offered to any interested supporter, investor or the general public.

Advertisement

95 Comments

 1. Ifetu ndi maule kaya mutukwana bwanji kaya munyoze bwanji ife sitidzasintha inu nkodzo wanuwo.Muli ndi chikho inu.?Kodi kwina ndikulira eti muuponda

 2. kangunje umakwana potinkhomera somali omaliza umatiimira unatimwesa wamkaka kananji mmesa amat zikho amatenga ndiyeyo watan kod adawanyenga akaz wake mwankhanza kod ndiye umkaz udakwiya

 3. Kkkkkkkk dzuro Neba mmalo moti aziimba nyimbo zotamanda Moyale amvekere Neba bus sikubwera ine shaaaaa kodi mumabwelera kuzaona bus? Kkkkkkkk ganyu azakupha Neba

 4. Zabwino zonse Mauleeeeeeeeeeee tili pambuyo panu

 5. kkkkkkkkkkk Kungokhala ngati mwanatu oti akamugulira Malaya anyowani ndi kabudula basi mudzi onse udziwe kkkkkk , any way congrats Neba , anzanu nawonso apeze chopwanya basi

 6. Aaaa kodi inu mene fans ya bb imachita matukutuku muja kumayika ma profile picture bus image mkuti bus imeneyo isanebwele?eeeee koma yeeee

 7. Olo chovala chatsopano chimakuonekera bwino ukavala uli ndi mtendere mumtima, bus mumati mukwera pa finals ija yabwera, koma mukumva?

 8. Kodi mwagulako ma spare window glass…..koma nyerere zayichalila bus imeneyi

 9. Tapeza chogenda sopano……munatiswela min bus yathu….chobweza kuwawa

 10. Had it been that NBB won that game Moyale could not have accepted the defit because of that pelnaty, alot could have been said like we could have been acused of buying the pelnaty etc, so think about that first!

 11. Had it been that NBB won that game, Moyale Fc could not have accepted the defit because of that pelnaty, alot could have been said like we could have been acused of buying the pelnaty etc

 12. Wakapado fc uzafa ndi bp.auzini abilu folowadiwo akubweleseleni yanu ya matabwa,bola pakhale sticker yolembedwa marcopolo.mwina tingafanane.

 13. Bola osaisowesa maspairs azikapezeka mu Ndirandemu ndi uvenda wakowo Neba,komanso ndiyamaplayer osati aliyense azifuna kuti izikagona kunyumba kwake ndikulozedwa kwakoko NEBA.Ndakunyadira.

 14. Bata Aka Kanundu Bullets Ayitibula, Bata Bullets tikuti ayifwafwantha, abale Kanundu FC akuti ayikwapula, jamani Bata ayipamantha, guys Bata Bullets ayikung’untha, akuluakulubndati Bata Bullets ayideweza, amzanga muli apa ndati Kanundu FC ayilikita, Kanundu FC ayithyola, Bata ayimenya, Bata ayikulunga, Chamba FC ayisyaga, Ndudu FC ayilukutula, abale chingambwe FC ayigudubula, Bata ayiwaza, ndati Bata Bullets ayisenda, tamvani akuti Bata ayithudzula, ayimweta, ayiswa, ayiphyota, ayidiula, ayididimukula, ayivina, ayikasa, ayichosa mano, ayiwonesa blackout, ayikazinga, ayigwagula, ayitimba, ayinyamulisa mfuti, ayipwagula, ayikalanga, ayisyagula, ayitumbula, ayiumbuza, ayithyakula, ayipanda, ayipha, ayikomola, ayiulaga, ayilemba ndi choko, ayikhadzula,ayithira seketera, ayikhwefula, ayidyesa jombo, ayiumbasya, ayiteketula, ayikodzera, ayithira tiya gas, ayiganga, ayiwamba, ayipanga kanyenya, ayiwotcha, ayikalanga, ayisyasyajila, ayiswa, ayichapa, ayisalanya komanso ayinyenyanya Bata Kanundu Bullets a Sulom azipha mtima kkkkk Bata mkumadzulo ibwenza

  1. Koma mkulu, mpira wakumalawi umautsata? Bata Bullets inatha kalekale kusanabwere ma TV, mpira tikumvera pa radio ya Nzeru. Kapena watuluka kumene kundende after serving a long sentence? Wise and move with time.

  2. Buzi Iwe Panga Za Timu Yako Osalimbana Ndi Bullets Kusadziwa Mpira Kodi Bata Ndi Timu Yakuti Machende Ako Wamva!! More Fire Nmc Bullets!!!

 15. Bus sisewela mpira penalty fc yasosoledwa lero osasintha nkhani apa ref kuyesetsa kupeleka penalty moyale kubweza kangunje ndikutimwetsa wa nkaka ife manoma

 16. Bus iyi inali kale ku Malawi konkuno anakayipent ku Jon chinampopa magazi chimenechi. Amasangira kuti ayiyambe akawina agwa nayo kulephera kuwapasa penate ya ulere

 17. NDE yafika titasadzidwa ndi moyale,ma defense ndi golo boy anayiwala kuti bus ikubwera, that’s why achinyitsa dzigoli

 18. Bus ndaiwona ikudutsa moatize,koma ndindalama zikutchulidwa zija zikugwilizana pa bus imeneija?machine apamwamba kwambiri komano maonekedwe ndi manvekedwe akuoneka ngati 2hand amene mukudziwa zoona tiuzeni.

Comments are closed.