Member of Parliament for Mzuzu city constituency Leonard Njikho has pumped in K2 million for a football trophy to be competed for by teams in the city.
The competition named Uncle Jossy Football Trophy is expected to start in November and will end in April next year.
According to general secretary for the trophy Mr Mkandawire, they are now in the process of registering teams for the competition.
“Teams are asked to register, the door is open to all non-league teams in the city and those that are playing in Division One,” said Mkandawire.
He however said teams which are playing in Simama League will not be allowed to participate.
Mkandawire added that all teams will be required to pay an amount of K7000 as a registration fee.
Uncle Jossy trophy is an on and off trophy that started years ago. The aim of the trophy is to identify the hidden talent that is in the city of Mzuzu.
Waphweka mudyeren,,doing all this,coz he wants yo votes,
Amalawi Tinazindikira No Development No Vote Kaya ulimuboma Timavotera Ena,mtumbuka Samva Maloza.
That is wat happen when you discover that no development has been done and MP money is good. Its time up….pipo need Change
Kkkkk mukufuna utindyele masuku pamutu choka apa kangwele uko
Fokolo zinu wandale mose akee
A Njiko why indeed wasting your money – Mzuzu City sibwereza MP !!!!!
Kampen ofoila uyu
Tym yosei unalikuti tayamba wadya kae ndalamazo utipeza 2019?mesa umatitengangati makape
Musatitenge Ngt Dzitsilu Dzanu Five Years It Iz Enough Kupanga Cikho Mucikhazkitsa Pano Kfuna Kutikopa Ife Km Samala Mcp Ndi Yomwe Ilowe 2019 Km Uliko Aaaaa Udzaona Ngt Sitikuknda, Utandiakha Cimavuta Ndician Kt Zaka Zosezi Cikha Ngat Cimeneci Cnabwere? Zkomo Pobweretsa Km Ngt Wabwera Kt Udzapeze Mavoti Udzakhumudwa Ubwino Kt Ma Youth Umaganizra Nthaw Ngt Ino. Km Ndikupephen Anthu A Ku Mzuzu Kt Musapusitsdwe Ndiwanthu Ngt Awa Angofuna Ma Voti Anu Zindkran Kt Dzuwa Salozerana Tatopa Nd Boma La Anamapopa, Lompha Alubino, Adanzi La Bodza Losowa Cilungama Conde Ngt Ndalakwa Khulukani Dzwan Kt Cilungamo Cimawawa Ndpo Cimapasura Zikom Kt Mwamva Waktsina Khutu Ndinas, Tsiku La Bwino Kmso Mafuno A Bwino Zkmo
Yikuwakwanira Nthawi Yoti Atinyetse Nalo Bodza 2019 Tisaphonye Dala Tidzachonge Pamene Pali Tambala Anthu Ofuna Kukhutitsa Mimba Yawo Yokha Tatopa Nawo
Hahahhahha Willie Mzumala, it’s personal money not government Ndiye pena it’s good kuyamika or don’t say anything. Taponyani trophy Ya Mphwaka Tione
What is Mk2.0million pa Malawi pano? Iyenso akudziwa amwene. What a useless MP.
Wayisunge waka ndalama yake….palibe zoyamikapo pas
Musatitenge Ngt Dzitsilu Dzanu Five Years It Iz Enough Kupanga Cikho Mucikhazkitsa Pano Kfuna Kutikopa Ife Km Samala Mcp Ndi Yomwe Ilowe 2019 Km Uliko Aaaaa Udzaona Ngt Sitikuknda, Utandiakha Cimavuta Ndician Kt Zaka Zosezi Cikha Ngat Cimeneci Cnabwere? Zkomo Pobweretsa Km Ngt Wabwera Kt Udzapeze Mavoti Udzakhumudwa Ubwino Kt Ma Youth Umaganizra Nthaw Ngt Ino. Km Ndikupephen Anthu A Ku Mzuzu Kt Musapusitsdwe Ndiwanthu Ngt Awa Angofuna Ma Voti Anu Zindkran Kt Dzuwa Salozerana Tatopa Nd Boma La Anamapopa, Lompha Alubino, Adanzi La Bodza Losowa Cilungama Conde Ngt Ndalakwa Khulukani Dzwan Kt Cilungamo Cimawawa Ndpo Cimapasura Zikom Kt Mwamva Waktsina Khutu Ndinas, Tsiku La Bwino Kmso Mafuno A Bwino Zkmo
Only Mk2.0million????? What for?? He thinks people are still not grown up….kikikikiki
It Iz Now Time Kt Tivutike Ndi Anthu Odzikondawa Km Musaiwale Kt Tazindkira Amalawife Tidya Zmezo Anthu Nd Maso Basi
njikho 2019 paurendo ,Vito so iyeyu koma komwe anakarowako Ku DPP ,mcp moto kuti buuuuuuuuuuuuuuuuu
Zoonadi Tafika Nthawi Yot Azitsogoleli Atinyengelere
mwayambapo 2 munali kut nthawi yonseyi
Mzuzu sibweleza MP.
Save ur money Njikho plz.
Time for Bennex Mwamlima is approaching.kkkk
Anyamata sewelani ndipo timudyele ndani angavotelenso njikho…wadya Njinga
Kufuna anthu osauka aja tsopano nothing else kkkkkkk thawi yokopa anthu kuti akuvoteleni mukatelo mudzathawe mukawina
Munali kuti nthawi yonseyi. Takudziwani maso anu ali pa chisankho cha 2019
Kuyamba kuonekano ma constituency ma Mp
Munali kut zaka ziwiri zapitazo? Ndakufunsani man!