The chief of Malawi prisons has warned all prison warders that they face mutiny charges if they do not return to work immediately.
This is according to a memo made available to Malawi24, released on Sunday, July 16, and signed by prisons chief commissioner Wandika Phiri.
Phiri said the order has come in as the prison’s management is pursuing the issue of salary harmonization between them and the Malawi Police Service.
“You are directed to return to normal duties with immediate effect as management is pursuing the issue of salary harmonization between the Malawi police and the Prison service.
“In review of the foregoing, you are strongly warned that failure to adhere to the directive is tantamount to mutiny and management will not hesitate to immediately take necessary action as stipulated in section 58 of the Prisons Act,” reads part of the memo.
The prison boss has also warned all officers who are not on duty to desist from loitering around prison premises
NDE Malawi wochepayo miyambe kuotcha zootchaotcha….lol
Pitaniiiiii
Ndimaona ngati amalumbira polowa tchitoyitu
Go guys go. Intimidation isn’t a solution to your demands.
Zakudya ndiye osanena amakhala Nazi ndithu chifukwa chake ambiri Ali ndimstupi osalala ndi kunenepa
Abwerere Ku work asasatire aphunzitsi Iwo zina amalandira za ulere monga zovala mphunzitsi bwa sanayambe alandilapo chilichonse chaulere cha personal
Bwanji apolisi atear gas osapitako?
Ngati zavuta basi ife tangokhala kusowa ntchito tilembeni enawo akapeza kwina kuli ma salary okwera nanga ife anthu akuno Ku mudzi ma salary athu azakwera liti ndie nafe tizapanga yathu strike mchaka cha 2019 tizasitha khaza pepani sindinakuvulazeni eeeya
More strikes are done due to poor remuneration.Poverty has over powered us,and gvt seems to be the main source of funds.But why gvt is not taking the issue seriously?Go on the market,soya is sold at K150 1kg,maize K70 1kg,g/nuts K300 1kg sugar K850 1kg increment K200per K1000 is gvt serious?Top gvt officials they cheat service delivery on papers and get million of kwachas yet someone is threatened for truth.MALAWI IS SELFISH.
Let the prison warders open the prison gates and let the prisoners out.
The solution should be harmonizing the salary with immediate effect, not threatening them.
Akulu Mwaluma Bread Wa Ma Slice? Mukufuna Anthuwa Akhale Makasu Anu? Inu Muzitupa Mimba Choncho Iwo Aziwonda? Zowona Azigwira Ntchito Chifukwa Choti Inu Mukuwawopseza? Mulungu Akukukhululukireni. Chifukwa Chani Mukangolowa Satanic Mmakhala Ankhanza Chonchi? Anthuwatu Angofuna Ma Salaries Awo Azifanana Ndi Achitetezo Anzawo. Sopano Inu Mukubwera Ndikuwopseza WHY???
Akulu Mwaluma Bread Wa Ma Slice? Mukufuna Anthuwa Akhale Makasu Anu? Inu Muzitupa Mimba Choncho Iwo Aziwonda? Zowona Azigwira Ntchito Chifukwa Choti Inu Mukuwawopseza? Mulungu Akukukhululukireni. Chifukwa Chani Mukangolowa Satanic Mmakhala Ankhanza Chonchi? Anthuwatu Angofuna Ma Salaries Awo Azifanana Ndi Achitetezo Anzawo. Sopano Inu Mukubwera Ndikuwopseza WHY???
Muwapase masiku ngati akanike kuwonjezela ndalamazo basi ali ku ndendewo asegulileni azipita mmakwawo nanu muzipita muzikalima basi nkhani yathela pompo sinanga akukuonani ngati ndinu osafunika?
U are the one who caused this mess in the first place,because u don’t listen. Stop threatening them with laws. The same laws which you have also broken
Tsholazz Wizzy P Popo
Go a sepafala ko Malawi
Ba siame batho bao
Ka eng ne mr?
Strike
Chelete ntatez….they are paid lower than police n army
Must we follow suit
Gilbert Barcos Tswiri
Kkkkk in the name of military slogan ! The way of a soldier, highly respected,poorly paid,do first complain later
Tikumana pagate bwana…matayala 10 apezeka kale oyambira mawa
Wafikira mmavuto…… Ndidamva ana nthawi inayake akuyimba kuti ng’ombe…………..sikoka…….
Please let prisoners go out we miss them.
Police department is not Prison department, zochitika zimakhala zosiyana, department iliyonse imakhala ndi zofuna zake, ma risks amakhala osiyana e.g. a police ambiri akumafa kapena kuvulala pogwira ntchito yao pomwe posiyanitsa ndi anzake, training imasiyana kwambiri, ku nkhondo amene amapita ndi a MDF ndi a police ndi zina zambiri. Zonse zili ma act osiyana Army, police, prison. Zofuna za a police ndi zofuna a prison ndivzosiya. The best way ndi kukambirana ndi boma pa zomwe a prison akufuna osatengera za department ina mkumati ndife amodzi ayi ndinu osiyana za copy and paste ayi. Chitsanzo china ndi choti anzanu atati apange strike ngati a police in just 3 hours mukhoza kuona mmene dziko lingakhalire koma ena Apanga strike masiku ambiri chuma, business, security, ndi zina zikuyenda bwino showing kusiyana pakati pa ma department inu. Don’t act like uncivilized people
So your comparison do you mean other departments are more important than others?? Am not understanding you well
fact man,mwathoka ngamo@kumbu
Mr Nsomba chomwe simukumva nd cian apa?? Sulungwe wakamba momveka bwino kut zochitika nd zosiana mu ma depatmentmu ndipo nd apolice angat aphedwa ( to be more specific PMF) kusonyeza kut ntchito nd ya risk,,, sananyoze kut ena nd ofunika koma ma previlage anaenea kukhala osiyana ,,,
Ofcourse ma Department ndiwosiyana. Mwati strike yama prison warders zithuzikuyenda bwino??kodi atati awatsegulire akayidi mukuwona ngati zikhala mmene inu mukuwonera?
mwathoka truth man
Koma nde zaonjeza strike
Police department is not Prison department, zochitika zimakhala zosiyana, department ili
Kkkkkkkkkk Asilikali kunyanyala ntchito ? Zoopsa
Iwe anenele ~sakukondwa nayoo
salary yawoyo ~sakukondwa nayo
Why are you intimidating them instead of paying attention to their problems? Will that going to iron out the problems? Kumayamba mwaziganizira muli inu kaye,them too are human beings just like you and me,they also wish to have what you have and do what you do wosangowopsezana apa ngati dziko lino ndilanu nokha NO!
Pangani zomwezo , asakuopyezeni .
no mutiny here. in a mutiny, the offices would have been closed, the senior officers arrested/killed by junior officers. none of these happened, were on a peaceful strike. bwanji ma khansala anatsekela ma DC kunja aja sanaimbidwe mulandu? bwanji ma cadet anamenya wa police sanaimbidwe mulandu. mungokonza zolakwikazo basi
Refusing to obey a person in authority (military) is called mutiny. and anyone involved (mutineer) may be subjected to relevant charges, in ths case the prison act.
meaning repressive conditions to be adheard to?Well, NOT in a democracy. complaints started long way back but no response. This was their only way out, the authorities were banking on what you have said, but everything has a limit. Govt even had to listen to pensioners, PENSIONERS who are no longer working, why not them warders?
Prison service is one of the security agencies in the country. There is no way the army can be on strike too is prison service. So others are saying there is intimidation but with ignorance. Let’s suppose the army and police are on strike, what will happen?
We know that there are not allowed to strike. You are missing something. These people are not taken serious and their department has no way to get bribe. Police will never ask for increment but they increase salary by receiving bribe. E.g at home no soap, food, school fees, then a hard criminal throw 200000 just to let him go. Its obvious the police will get that money and go home. But teachers, these prison guard can’t get bribe and they will breath the fire
I wish we had heard from government side why disparity in salaries among these 3 departments,otherwise not justifiable no wonder warders are protesting because wrong decisions made today will be difficult to be reversed in future, in civil service for many time we have been assured of salary harmonization but they are failing.
Very pathetic indeed! I believe there are some more important sections than others
Prison Warders becoming more like Prisoners. How does a normal person block a responsible Minister from entering the Premises to hear & discuss their grievances?. Malawi looks to now being a Nation of brainless People.
Apatseni zofuna zawo akaidi mwayi wanu just make a plan
Kkkkkkkkkkkkkkk koma a Malawi akuwaopseza,mmmmm zigawenga zitulukatu mkatimo Tawapatseni basi.ena akuthizimulidwa ndi zigawengazo mkatimo bwanji osanvera kulilako? Hehehehehehe eish!!!!!
Apaseni zawo. Mavuto pamalawi nawoso awakulira
LUTEPO OUT, KASAMBALA OUT IN THE NAME OV STRIKE….
Kkkkkkkkkk ziliko
” our wisdom begin to ellapse at a time when righteousness intertwines with negligence- Malcolm X”
the best the prison boss can do is to threaten ….?….are you taking advantage that the prison stuffs striking are of levels of education to an extent of citing “section 54&58″….,of the prison act ……serious ……?
when the judiciary was on strike y dint we not cite section 94(c) of the judiciary act… ?
ooh yes wen teachers were on strike why dint we not cite section 32(1) of the tum act”?……i think we lacking wisdom thus y negligence in the whole matter seem to criss cross with yo righteousness. ….think twice…..
Inu ndi mfulu yakhulani zakukhosi kwanu akoza amenewa aaaa akulu sangangokuwa amenewa atopanazo asa mwalakwanji Ambuye akumenyerani nkhondo imeneyi zitheka ndipo zithekadi
Mpaka kuopsyezana
Abwana amvetsetseni anthuwo musathamangire kuwaopsewAbwana amvetsetseni anthuwo akudandaula zoona musathamangire kuwaopseza sakulakwitsa akawakonzera abwerera mawamawali.
no pay no food n work
apaseni chabe ma kopala awo
kupereka threat kuti mudziwaberebe et kkkkkk koma my Malawi eeeeee
Solve the problem not intimidation
Thats why timakuuzani ntchito koma ya uphunzitsi. One day strike Boma lidakakhala lakonza kale zolakwika zonse 🙂
inu simungayelekeze kuthawisa ma prisoners mukuziwa kale kuti ndi mbola hahaha 🙂
Apatseni anthu zomwe akufuna zo sizoti muwapatse ma mutiny anuwo bwana….kusunga mbava tu simasewera ai
wogwira ntchto ku prison sikt iyeso ndi prisoner iyayi,adzkhala chete pamene zinthu sizikuenda bwno? pamene apolice josephy nkasa adawamenyera nkhondo,nanga ku prison awamenyera ndi ndani? gys osafooka mukapusa muzidya machange omweo muona.zinthu zadulatu mumisikamu,ndie mukapusa zanuzimenezo….
kodi nthawi ya mavoti yaandikila
KKKK ASOVA BAS
Anthu awa alibe mwambo munaona apolice akuchita strike m’zachilendo izi
Ana akufuna ma grades akwere, is that mutiny?
Aka ndikoyamba kumva kuti msilikali wapanga strike chibadwileni changa. Chikhala kuti zinachitikako bwenzi titazionela kale pa ma movie ndithu. Eeee mpaka kuotcha ma tyre ndiwe ma civilian ife tiotcha chani?
Pepani boss mwina mongokonza i think ku prison ku kakhala kachiwiri,I hope inali 2004 or 5 kunalinso strike ma issue ake anali omwewanso msanga msanga anapanga harmonise ma salary ndipo zinatha bwino bwino.
It was in 2004, with Bingu, but it was just a single day, the following day salaries were harmonised,
Mutiny is a criminal conspiracy among a group of people (typically members of the military or the crew of any ship, even if they are civilians) to openly oppose, change, or overthrow a lawful authority to which they are subject.
In prison Act: if one found guilty of such charge, is either fined or to serve 2 yrs imprisonment with bard labour in default.. thanks
Cite ur source bro! thats plagiarism
Sec 58 of the Prison Act brother, go & search
Sec.58 its abt unfair dismissal
Simau a msogoleri awa. Ali sure kuti anthuwa onse atasiya ntchito sipakhala vuto? My fellow concerned officers, don’t take this threat. Akulankhulayu amalandila zindalama zochuluka zedi, kaya amdyesa chi banzi ameneyo achisanza ndi phuma but don’t quite your strike till you got what you want
Nayenso thupi lake watsala ma bar owerengeka ndiye aziwopsyeza mzika za dziko
kkkkk mpaka pamenepo
Do not forget that criminals are at the mercy of these people whom you are intimidating!
Ngati simutipatsa tikhala tikuotcha mateyalawa basi
Apaseni zomwe akufuna mapeto ake eshhh!!!!!! Prison break,,,
Apatseni zawo basi…
Aaa tipitire mantha?
Amuthimbwitsa nacho chibazii!!!!
Malawi sudzatukuka ndkupondereza kwakoko. moto osowa wokuzmitsra ukukudkra kumwamba
Nthawi ija yokawona ku Ntendele iyii,
Mutiny charges ya chani,ingowayankhani madandawulo awo
I said it here
That’s wrong. Stop intimidation and threatening. To me it seems something’s is wrong here. Instead of solving the problem you threaten. What about teachers. Are you going to threaten as well. That why the problem gets worse. Swallow your pride and face the problem and sort it out.
Bro its not intimidation but thats the rules in any millitay forces.
I understand that police, army, and prison guards are law enforcement and government security. But if the issues raised always fall on deaf ears. That leaves with no option but to break the law. Since the law was set by people then I don’t see it strange. But don’t forgot that they have been crying but being ignored now they strike you say law really
That’s why in Africa we will keep fighting each other for small matters that can be solved easily and fast. We always look on one side of the situation. Its time we look from different angles. I understand but the dangers that can cause. But because they are not allowed to strike then no concerns must be heard from them. Everywhere in the world people take advantage of Malawians because the say they understand quick. If you go to RSA just mention Malawi you will be first choice. Because you don’t complain even you see that this is unacceptable and with bad conditions. Employment must favour both employees and employer. Not one side no that not good
Stop comparing Security departments with Teaching department. These are two different departments with different rules brother. Military forces doesn’t go on strike, where in the world have you ever heard this has happened????? Svhool me
Wachuluka ndiumbuli adakakhala akudziwa malamulo sibwezi atapanga zimenezi
Dali Gazaman Bakuwa I am aware of that government security don’t strike. But as far I know where in the world have you ever heard that when you security raise any issue you ignore. Is that a way you solve issues. Everywhere you go no strike for these people but when they raise issue the government discuss it and come up with solutions. But they are striking because they are left without option. If this matter was attended then we should be not debating here. But due to ignoring that’s why thing are turning the way are now. This is first time in history in the world. Zimbabwe is suffering but the police, army,prison guard are looked after to avoid situation like this. So are they going to eat law?
Blocking the minister from entering the prison premise is what will solve the problem? Charging them with Mutiny will it be wrong? How about sending their chief to submit their concerns, wasn’t it a good idea?
Dali Gazaman Bakuwa that shows that this matter is old. As far as I know. You Dont strike without table discussion. That show they have send their problems before but it was just falling on deaf ears. Take it like it sad you trying to solve this problem but no one takes you for granted because you have no right to strike. Trying bwana ndiganizireni nyumba zazitini zodotha komanso malipiro ndizinthu mnene zizilili umu chonde bwana ndimvereni. Then your boss know that you don’t strike and ignore you. Then what next strike and know you say they are not allowed to strike. A lion to eat grass its not a choice but n meat available no choice no option. Its simple take it like if it was you in a situation like this
you have already said in your first comment ,,break the law”” i know u know what it means to break the law,,,which means if they get punished u won’t be surprised,,, laws were made by people of course but when u break the same laws which were made by ur fellow human beings there is something u will get that is punish
Kkkkkkkk at 53 kuopyezana. Just raise the salary. Zomwezi mpaka ma meetings. Some ministers will be in these same prison. Xikoli ndilozungulira. Mukawapeza mukuwanyozawa
No need for mutiny here……they have a right to strike..even Army can go on strike
The issue is police and prison petitioned the very same ministry to transform their salary structure, when it comes for the pay day, police get the answer, while prison remain intact, the prison juniors asked their bosses what will be the way forward, their bosses answered them let’s wait for the ministry, so juniors refused to be nothing.
The problem in Malawi is people enjoy suffering and failure of someone. How do you feel to see these people suffering when they keeps criminal away from your family. For sure if this department they was a way to get bribes trust me they won’t be complaining like this. That why we see all department that get bribes will strike and cry but no straight answer. Look Africa at large police don’t stress they just increase their salary thru bribes. It’s only these few department that is not easy to get bribe.
Paja amathira teargas away bwanji osawathira tione ngati sipanunkha
Thats true dzikoli ndilozunguliradi ngati mpira…..posachedwapa mukapezana konko mutasanduka white white….bwno nazotu !!
Komabe jst address their grievances other wise… Ndipamene muwone kufunikila kwa asikali ogwira ntchto mundende.. Madandaulo awo ndiomveka
Don’t comment delete
thus military act has no porous disciplinary stand….musova
he he he..
he he he..
ndaseka
ndaseka
Asova
Zoopyezana zilipobe? Eeeeeee
ukaopyeze ana ako mbuzi?sindigwira mpaka ndalama zanthu tilandile?its our tax pay not your money
ameneyu ndi nyani ndithu..poti zawo zikuenda…to hell chief
Mwayamba kuopyesa akutanini kumtundako
eeeeee
UKALI NGATI ZIKUCHOKA MUMATUMBA MWAWO
wadya chibanZi
Sitipitabeeeeeeeeeeeeeee
Dont intimidate them, tangowapasani zofuna zawozo basi azikagwira ntchito.
zafika pamenepa.