Vakabu yayambilanso: anthu 87 atsekeledwa kamba koyenda usiku

Advertisement
Malawi police

Inu amene mumatamika ndi kuyenda usiku kumati Apolisi anasiya Vakabu samalani. Mukagona mu chitokosi tsiku lina.

Malawi police
Vakabu yayambilanso

Apolisi ku Limbe mu boma la Blantyre, lachitatu anatsekela anthu 87 atawakokolola kamba kopezeka akungoyenda nthawi yosayenela.

Malinga ndi Apolisi, mu Limbe munakhala mukuchoka ma Lipoti ambiri oti anthu achitidwa chipongwe.

“Anthu amadandaula kuti alandidwa ma foni, ena abeledwa ndalama ndinso kusompholedwa zikwama,” atelo a Polisi.

Iwo ati pofuna kukhwimitsa chitetezo, Apolisi anaganiza zoyendako mu tauni ya Limbe ndipo anambwandila anthu amene akuwaganizila kuti amachita za chiwembuzi.

“Tinagwila anthu 87 amene amangoyendayenda mtauni nthawi yosayenela.”

Apolisi ati anthuwo anawapeza ndi mafoni ndi katundu wina amene akuganizilidwa kuti ndi wakuba.

Advertisement

127 Comments

  1. NDE yake usiku ndi nthawi yogona mangani inde ndi ntchito yanu inu a #salon amangeni inde tisamasowe ntendele chifukwa chakubawa amangeni basi

  2. Anasiya zija zachisawawa amenewo kalipokalipo ndiye kuti olo akanawapeza masana akanawatengabe, sikuti a police anasiya kuyenda usiku mtawuni.

  3. Vakaba zo.agwira anthu oledzera kumasiya mbava zenizeni. Whats wrong with kuuenda usiku. Akanati bola azimugwila munthu atamuona akuba

  4. Our police are very good at breaking the law….many of us have slept in police cells with no valid reasons

  5. I used to cry everyday thinking I will die of HIV virus. After 6 years of contacting the virus and taking Arvs, I came across an article of an herbal doctor who cured HIV/AIDS. I was terrified and decided to contact the doctor with the number provided.(+2348146005390). I saw other patients the doctor have cured and I got the herb and exactly after a month after I started taking the herb, I went for my monthly test and was completely negative. It was too good to be true that I did series of test in another hospital but the test results came out negative as well. With joy in my heart I share this testimony. If you need help just like me you can contact DR SAVE via email [email protected] or whatsapp him on +2348146005390 thank you once again for your healing.

  6. Ubwino wake kuli ma court,tiona kuti awachita charge bwanji?komanso ndipofunikanso a court awunikirenso tima section tina tingonotingono

  7. Oyenda usiku popanda cholinga xhenicheni agwidwe bas anthu amenewa akukolezera umbava kwambiri mdziko muno amalawi eniake tikukhala mwa mantha dziko lathu lomwe big up apolisi bola musamazilowetse chinyengo so that the sweeping exercise shld be fruitful.

    1. Is it in our constitution? Everyone has a right to walk,stay ,live feel without being disturbed. So I wonder if you say its legally. As far as I know laws u only arrest suspects with evidence not imagination. And that why that unity is asking for cash

  8. Vakabu yomangogwila ife osauka oyenda pansi Koma olemera a magalimo osagwidwa mxiiii… mbava zoopsya zimayenda mmagalimoto popita kuumbava tu

    1. @Loveness Kaunda i don’t know if you would agree with me. During night and odd hours a person moving around by foot is more prone to danger than the one in a vehicle. Rogue and vagabond on the other side of it, provides safety to people like these coz if they are taken to a police station their life is saved from potential danger that is there in the streets.

    2. @Loveness u did not get my point. Munthu oti ali pa galimoto ndi oyenda pansi angapangidwe attack mosavuta ndi uti? And do u think it’s fine kumaimitsa galimoto ili yonse munsewu pa malo oti palibe road block?

  9. i can see the importance of national IDs here……NRB please, speed up the process so that these law inforcers must work and judge a person according to his or her profile………let human rights prevail without freedom stringents

    1. Kkkkk aaaa azibambo amawonjeza kubwela usiku mmakomomu, kuchoka m’bandakucha ana akugona, kuzabwelanso ana akugona?????

  10. vuto ndilakuti malamulo simuwatsata, akamati vakabu inatha sanena lamulo lonse, ngati muli ndi constitution volume II cap 7;01 in law book of malawi section one eighty four sub section c ndi imene inatha koma section A B D ikanagwilabe ntchito ndipo musazinamize kuti kuti rogue and vagabond yatha koma kuti chabe part ya rogue and vagabond yo ndi imene inachotsedwa which means malamulo enawo akugwilabe ntchito and you can be answerable

  11. Guys simudziwa azanu wofuna dalama samangona sumazalema 4 exmple ln SA especialy johanesburg anthu no sleeping amankhala akungulitsa malonda

  12. mmmmmh! ena akukamba za joni koma nkhan ili apa ndiyavakabu zugwirizana nd joni kod? kuno ndkumalawi not kujon zimatinyasa mkamatiuza tisana funse,,,,,

  13. Malawi sasamva.Mukufuna kuti mbava ziziba kenako muzinena apolice sakukuthandizani?.Aliyense oyenda utsiku ndi FISI AKUFUNA KUBA AGWIDWE,Koma ena omwe amakhala akupita kuzipatala,kukapeleka uthenga wa matenda,maliro apolice muzipita nawo komwe akupita kukasimikize.Oweluka mochedwa muzibwelera nawo kuntchitoko muzikafufuza.

    1. Ngati uli munthu osalakwa ololera kubwelera,koma ngati kuli kunama zakuchokera kuntchito yes ndizosatheka.Palitu ena amanena zakuntchito kuli kunama.

  14. Amwene sizoti inatha. Interpret zinthuzi penapake ahh. Anachotsa ka rule komangonyamulana mwa chisawawa kaja. Anthu wo ngati analibe ma ID etc anayenera kunyamulidwa basi

    1. Akuvephi etc. Ngati uli okaikitsa amakupangaso question bhobho and penaso ukakhala disturbed mentally with ‘e use of drugs and alcohol

    2. @Chisomo pali ma guys ena amachita kuoneka after kufunsidwa mafunso usiku wo and amapezeka akuyankha za mbwelera tho sometimes a police amatengera advantage kuti amupange abuse munthu

    1. so the police should sweep the noise? is noise akuba? school me. Or the much noise goes in ppoz houses n start stealing. Coz evn if the police catch thievs there….the noise Wil stl remain

  15. Simunamve bwino inu. Unali msonkhano wama-vendor nawo amati akufuna kumatcha so amakumana kuti awone apanga bwanii. Ndili ndi mwayi sindinapiteko, bwenzi ndili mu chitokosi! 😀 😀 😀

Comments are closed.