The Malawi national football team has slipped by 14 places on the latest FIFA rankings released today by the world football governing body.
The Flames were on position 100 last month and have slipped to 114.
This comes weeks after the Flames lost at home 1-nil to Madagascar in the CHAN.
This means that Malawi has become the worst mover on the latest FIFA rankings after dropping by 14 places from 100 to 114.
Whereas Madagascar are the best movers after climbing 9 places up.
Egypt remain the top-ranked African team following the release of the latest FIFA rankings.
With just seven games played during the points timeframe, there was very little movement in the rankings, with no change among the top 70 teams.
Champions of Africa, Cameroon are ranked 33rd and third on the CAF list, while Nigeria’s Super Eagles are 40th, Ghana at 45 and South Africa 64th.
Brazil, Argentina and Germany occupy the top 3 spots overall.
That’s where we belong…!
Ukunama iwe
You must show Walter Nyamilandu to solve that equasion not us
YEHOVA ALOWERERE.
It should be 250 not 114
Anthuwa alibe matupi athazi afunika zamagulu.
If u got nothing to tell us jus keep quiet ashes always makes us sick evene it is on position zero its none of our tuckshop!!!!
Flames sidzamvaaaaa
Thats good, great achievement. Go on boys you will find your selves on position 280 kkkk
Frozen Flames!
Congratulation flames keep it up guys
Osangoithesa bwanji?
Kkkkkk ok thats obvious
flamez siiizamva
Ayi amwene flames siizamva
mapuleya onse ndi mbuli sinzidziwa kusewera mpira
Looking at previous results, this was always expected to happen, but let’s not concentrate on the rankings, let’s concentrate on building the team. I wish them all the best…
Looking at previous results, this was always expected to happen, but let’s not concentrate on the rankings, let’s concentrate on building the team. I wish them all the best…
They deserve it
VUTO LATHU SI MPIRA KOMA KUKONZA CHUMA CHATHU CHIFUKWA TIMADYA CHUMA OSATI MPIRA. Kodi Malawi itawina world cup, chingasinthe ndi chani?
Mbola
Funding Imene Imapita Ku National Team Pa Chaka Bola Muzibwereketsa Alimi, Tizkolora Zambiri,
Poor little malawi
atibela amenewo nanga chitseka kukhomo ndi ndani? mesa ife tinayenera kukhala kumeneko…..awerengetse bhobho
Sulumba angakhale player????
Makape awa
mmmmm flames si team yoti ingawine just appreciate
Akungowononga ndalama za misonkho yathu bola kungothetsa flames
Ndiye zafika pa mwana wakana phala basi
Why? They Shd B Last. When Did The Last Beat An Opponent?
a fifa bodza team iyi amafunika position 268
Makape awa guys….lets just disolve it.
Nanga kuphedwa kwake kumene kuja
Nonsense
Kodi osangosiya kupanga publish nkhani za flames bwanji?
Kkkkkkkkkk koma abale kodi paja timangokwezedwa a position ngakha tiziluza eti kkkkkkkk zizayambisa nkhondo zimenezo one day
makape awa
Kkkk nao ndi mmene amatiikila pa maplimbikilani kuluzako mukhale chitseka khomo
kuli ma team ambili kumbuyo kwathunso mn.
No football in malawi lets conentrate on making children
They will be 200 by next months
kkkkkk km yaaah kamuthemuthe,chakachino kuli kan2
Mmene yafikira flames ikhoza kuchinyidwa kwambiriso ndi djibouti???
mbuli za flamez.
And 114 yachokera pati? Kapena yathu yachimalawi, yokagwirizitsa chithumba azungu Ku Zürich kuti atiganizile, otherwise ikutikhala ndi position 160
Yes losing twice with the same team
…..@….@?&000
Kkkkkkk or kukhala pa 200 I can’t complain
Improve a chimwene
zibwana too much kulibe ochinya zigoli kuno
Anakutembelera kina phiri kuno
Nanga miyendo yake imeneyo angawine? Koma ma hule ndi mowa agalu awa
Kkkkk
Mbuzi
14 places down in a month? soon we’ll be on 210th.
Ngakhale Akanati Yafika Pa 150 Padziko Lonse Zilibe Ntchito Zimenezo
Kuphonya kwake kumeneku tingakhale pa number 1 ???
Flames has done it again chingelezi chili pakamwa
Koma iwe FIFA, frames ikuwotcha ndithu mtheradi. Ungati yatsika ikukwera?
Olo itafika 150 who cares mxiihm!!
Izafika no 1200
MAKAPE OSANTHA MPIRA AWO AKANGOPEZA CHINA CHOCHITA MMAKWAWO
That is devaluation of flames
Kodi coach imeneyo anatengetsa chikho timu yake iti
Komano ifeyo paliso team yomwe tingayimenye?
Lazy boyz
No problem thats our lovely flames does always.
KKKKK Iwo sizikuwakhudza nkomwe aka flames kkj
Aaasaa ndizamenya Malawi basis mwayi ulipo
Eeeeeeeeeeeeee ndizamenye Moira basis ayiiii
No surprise.. A lesson worthy for us and if this pains,, and also if we want to paint our black face white we must act to show we are WE……
you mean pali team yoti ilikumbuyo kwa flames??….please call them flames mwina nkuwinako,ife nkusangalala..aibo!!
We really need to call from 120, draw yokha abale
to be very safe pakufunika ka 140 ngati kalipo….talira mokwana
Timufuse fifayo ngati kalipo
yah,,,other wise eeee,,,,or ka 115 katha kutitswa mtma
eish ask that again. kuteloku alipo ena pa 115? I want to know who are they pls
may be we call # Tonga @ 206 because @ 115 there is Oman….am afraid our hearts would break again….bring Tonga ,flames has to win at least
Zipup your mouths & let the Coach do his work.
Ine ndinalimba mtima kale ndipo ndinavomerezadi kuti chingayipe mbamba chilidi ndimwini.ndiye wina kuima pachulu nkufunsa,kodi kuthesa timuyi chindapusa nzingati? ….
Mbambadi mukufuta chaukalidi
flames manyaka eni eni
Kodi idakali kuwerengedwa….
Very bad we want (Kina) phiri back”
kinah bas enawa mmmmm
Zamanyazi
Anyamata athuwa osanama amayesetsa koma vuto ndila zikhulupiliro aliyense aku yuza zake.Tayeserani kupeza kokhwimisa timu yonse.Abale !!! iya, ngati akulu akulu adatha onse.
Apapa ndiye kuti ife tikuchita bwino. Mwana akakhoza malikisi ambiri ndiye kuti wapambana anzake, amakhala nambala wani. Ndiye Cameroon isamaletu.
Owoo?
kumalawi kuno ndikodalisika kuli mapulofeti ndi asing’anga komanso ndi ambiri kodi onsewa sanga thandize teamyi iyambe kuchitabwino kuti ikamafika mu sept izafike pa 99. chonde ngati muli ndiluso limeneli ithandizeni teamyi, mpira sindado kapena phada
Umakonda zinthu zowononga moyo wako koma suzindikira
Where is your god???
Olo atawayika pomalizila penipeni pa world ranking palibe vuto, sitingadandaule nkomwe, tinazolowera basi!
Thats much better paja Flames siifuna improvments!
Cows
That’s where we belong!
By the end of APM’s tenure, our flames wil be at the bottom most as is the case with poverty level.
Iiii sizikugwirizana flames kuluza yayamba lero??? Kusatha kusewera kwa team munamizire munthu wachete??ayi msambi adha
Kkkk so hw come iye kulamula kut Kamuzu Stadium isatsekedwe against FAM’s decision?
Ambwenumbwenu mtima wa nkhwiziwu muzasiya lit?
Kuda ngat pansi pa machende
Ndiye zosagwilizanatu,,,,therere ndi Nyama apa
Komatu ukanakhala wina nkhani yoti kamuzu stadium isatsekedwe president wayankhula after kumva madandaulo a anthu komanso ma team a bigbullets ndi noma
Sikuti wangozipangira ndiye sindikudziwa kuti zagwirizana pati kusatha kusewera kwa flames ndi utsogoleri wa Mutharika
Wats e connection thea?
Abambo amwela mowa salary kuvaya pa door blaming APM….kkk some people are so obsessed with Peter so much….
Even Muluzi once said,,, munandionapo ndili mu grocery ine? And shallow minded people like u southerners clapped ur hands koz u cudnt see the connection btwn poor economic policies and rising of commodities. If Flames is poorly funded hw do u expect the boys to perform? I guess nw u can see the connection,,,
Basi? ayikondela imeneyi bwanj? imafunika 200
Nt Ft Due 2 Luck Of Fnd 4 Frndlz.
Harvest time, shame!!!
olo itakhala number 15 nde ingatana pot flames kwake nd kuimbitsa ma chior umangova hhhh haa! Kumenyetsa cross bar
osangosiya bwanj mpirawo
I got all swear words against you if you expected anything different. “Frames” siidzamva.
Anatilozayo amathadi!
That’s Flames Doing What It Does Best #Bravo
beaten by a team like Madagascar home and away!no surprise!!!
nzosakaikisa
Flames sucks
Kkkkkkk bwanj osasiya kusewerako nanga mpakana 114 aaaaaa ANATILOZAYO NDI MFITIDI if it is like that
Shame
Boza