Ruling Democratic Progressive Party (DPP) General Secretary Eckleni Kudontoni has died in a terrible road accident this morning, Malawi24 can report.
According to reports, he died after his Toyota Fortuner’s tyres developed a fault causing the vehicle to roll over several times.
It is said the accident happened at Bua in Kasungu. He was traveling from Kasungu to Karonga.
Sources say he died on the spot.
As this report was posted, the DPP was yet to make a statement on the matter.
MORE TO COME.
Think B4 u tolk about this because one day ndi iwe ndi ine sorry REST IN PEACE R I P
Thank you
may his soul rest in peace
Akapumule mumtendere may God receiv his soul
mkulu anali wamwano uyu
Koma guys tiyeni tizikhala ndichisoni atakhala abambo kapena nchimwene wako ungave bwanji umasamala poyakhula kuno ndikunja kumayanja lichero
Zosayenda ause mtendere
RIP MR Kudontoni
A Malawi tiyeni tiziopa Mulungu muchowonadi osati kumangokamba pa kamwa ayi,,,, tisanyoze mtembo coz ifenso mmawa ndi mtembo ,, dziko la malawi anthu ake sitimakondana thats why tikumaphana pofuna kt tizidyelera bwino za dziko lapansi ,,, koma zonse tikupangazi Mulungu akatiponya ku moto coz kwa Mulungu kulibe lawyer,, kuli kuimika kt chilungamo chisaoneke ayi,,,
See you soon
Zosakhala bwino tataya munthu wofunika Ku chipani zimu wawo uuse mu mtendere
Rest In Peace Sec.
R.I.P mr kudonton
May soul rest in peace
Umoyo wamunthu umakutilidwa ndi zinthu ziwiri: ubwino ndi kuipa. Omwe amaona ubwino pa munthuyu ndi omwe akukhetsa misonzi pomwe amene amaona kuipa kwa munthuyu ndi omwe akunena za kukhosi kwao. Posatengera ubwino kapena kuipa may i say RIP!
Ee! Koma Anthu Mumatokota Pa Network Pano, Mmmmmm…
Kodi ifayi yamupita pati petela
Mmmmmmmm ifa iwe bwanji ukanatenga Peter yu please
xry ifa ndikanyama komwe kalingat ebola akuluwa anali munthu olimba mtima
Ndilibe problem kaya wina azifa kaya adwale mkono ine ndilibe PULOBULEMU. KKKKK
mulongosi mulongosi iiiiiii
maike G jinard inuo mutu mwanu mwazaza mamina ndipo mulibe umuthu mwava maliro ndi maliro zopusa mwalembazi musazalembeso iwe ndie ndani kutuwa sanachite kufuna olo iweo lero ukhoza kufa mulungu atafuna ukumva guys mukamalata zopusa ine zimandikwana naliro omwewa paka mwapeza khani ana agalu.
R l p sec
Rest in everlasting peace bwana…We shall always miss you!
Koma achaskwera ndi mai apume kutukwanidwa
I witnes dis,so sad indeed r.i.p
We will miss u RIP
Why do u let politics ruin chikondi chapaubale,,,,,politics lacks Christ
Very good example inu a DPP Mumaiwala kuti muzafa,kulalata,kuba ndi kupha mulibe nzanu bola ngati munakumbuka sacrament la kulapa
There z no way a normal human being can rejoice over another somebody’s death. Ask urself kuti where wil u end. I dont think kuti Mulungu angakondwe nazo zimezi. Ili ndidziko. R I P. Sec
Ause muntendere
RIP hon kudontoni
Ndiye mwati chakwera ndi amene ukudziwa za imfa yaku dontoni
Nde mwati o Ekelesi Kidontoni onakwe bulu ulendu wokatembelera onthu o Mulungu o Chakwera? Ha, zoona bulu kumkwapula kuti omange kowasi osadziwa kuti pa Buwa paima mnjero ndi lipanga lokuthwa konsekonse? Balam!
wasala pamtumbo pitala, aksngogweseraaaaa zenjemo athu akwiya iyaaa tatopanaye ife
u r wasting your time if u think Peter will go so soon, maybe you will be the first one before him cos dat man has got more than nine lives
You don’t know nothing u. Peter olo atafapalibe yemwe sangakondwe aliyese kufa kwa pitala azasangalala coz of hw reading coutry,
Mmmmm komandiyengozi zikuchuruka
Uyudi adzipita walalatakokwana nde mukamati rip ndikudabwa tichenjere kulimoto kukanthuko!then he is nxt i dnt know hu me u
zachisoni
So bad
They have started killing each other
very sad
Nothing to say full of sorrow ,GS rip.
Yemwe Chibadwile Sanachimwepo Ayambe Kulalatila Mtembo Wa Kudonton.
He will reap what he sow
Its an ill propaganda!…RIP hon.
Ngozi zachuluka why? sasan walowererapo kwambiri RIP Bambo,
Inna lilahie wainna ilayhie rajauunie mzimu wawo uunse mumtendele
KAPUMENI BABA KUME KUMENE MWAPITAKO KULIBE KUBA
MHSRIP.Dos Hu R Tolkng Xa Mbola Wll C Wat DPP Wll Do In 2019.DPP Woyeeeeeee!!!!!
Anali wa phuma kwambiri kuitenga DPP ngat yake. Beta akanakhala APM
R.I.P MR KUDONTONI
Mmmmm nothing to say RIP
Will miss you my brother
Pepani aku banja, pepani aku mpingo, pepani achipani, pepani anafedwa nonse. Akudonton mzimu wanu uwuse mu mtendere wa ambuye.
Munyoza mtembo bwanji,anakuberani chani,muleka kumalimbana ndi chair Lady wa cashgate mmamuopa eti,anali a MP achipani cha UDF poyamba,ife tinkawakonda,Ambuye waakondetsa,kuweruza kuli kwa mwini wake,nawe lako likadzakwana uzaweruzidwa
NANGA IWEYO?
Tonsefe iwe udzatsala?
So sad
Tatiyeni tingolila malilo akulakulu eish koma abale palibe chitipindulile ngakhale titukwane bwanji.
BREAKING NEWS: The ruling Democratic Progressive Party (DPP) Secretary General Ecklen Kudontoni has died after being involved in an accident enroute to Kasungu from Lilongwe. DPP spokesperson Francis Kasaila said Kudontoni was involved in an accident around Bua area and his body has been taken to Kamuzu Central Hospital. The cause of the accident is not yet known.But unconfirmed eyewitness reports indicate that the front tyre of his Toyota Fortuner vehicle burst before it rolled.
Pepani akubanja la akudontoni tikuziwa muli pachitsoni chachikuli pangodzi yomwe yakugwerani. Yang’anani kwa yehova mwini zonse ndiyemwe amathondoza wotsweka mntima.
AMEN
The country has lob st another politician gone soon before 2019 rip
AKudontoni tikusowani kuchipani,zoona 2019 tizatengenso boma inu kulibe?Mpaka tizakumanenso mupume mumtendere.
May his soul rest in peace.
…Ooowoh kani kodi mudzi munu muli zovuta. ayi sorry!
Wapaulendo saopa agalu ukaopa kumene upitako!
Ifa inakati izipepha choyamba tikanatumiza awowo. Anyway mwasangalala padziko pano ndi ndalama zamisokho kwatsala mukupitako
May his soul rest in peace ,he was agood man.
Zamaliro ndizomwe mukukambazi zikusemphana before you talk its better to think twic palibe yemwe amapempha imfa
shaaa! anayamba ndale asanakonzeke!!! zimafuna kukhwimatu izi, akanamufusa kaye john tembo, anyway rest in pussy!!
Nde mudzikalalatirana ndi satana. Kulalata ngati moyo wako uli Ltd.
RIP(Rise If Possible)
BIGEST sory to family, Biger to DPP and big sory to de nation may his soul rest in P.
Zovuta
so sad R I P
Aikidwa mpingo wa dpp?
sorry
ma members ena a DPP mtengelepo mphunziro makamaka iwe pitala kumaliro supita kumangokhalira kugula magalimoto ndalama zake zomwezi za anthu iwe umangothapako oooohooooo!…siku ndi limodzi
abwana nde mwandifikapotu kkkkk
kkkkkkkk! ..ndiope chani ine ?mbava izi
ok tamva inu amuyayanu
ayi ine si wa muyaya koma ndimadya thukuta langa lenileni
osati kumabera anthu osauka
very sad.RIP
Zitayeni bas.
Sorry R.I.P
Benard saidi osamatero.
Imfa ndiyowawa…imaphweka ikakhara kwa ena
Zoona Ine Ndikudabwa Kuti Ma Comment Amenewa Mnga Pepani Kapena Anachalira.
Ine ndingova chisoni zapasewu ndizimene zimakhalila Osamasekana motoumapita kwasala tchile.
Ah zowona koma
amati chisilu chili ndi mwini maliro sasekana muzaziona chikazakugwelani dziwani kuti munthuyu ali ndi abale ndi ana so dont talk too much
Anali wandale ndiye anthu ayenela kulankhula basi….sorry!!!
wandale si munthu koma chisilu,alive or dead,
maliro ndi ndale ndizinthu ziwiri zosiyana ziwa kuti pali achibale ena akuwona zomwe zikulembedwazi samala ndimayakhulidwe poti suziwa chobwela mmawa
Wandala akafa amanyozeka bcoz sionse omwe amamukonda
enanu mukuyankhula mopusa ngati ndinu zitsulo, or chitsulo chimachita zimbiri
Kkkkkkkkkkk
myhsrp
R I P.
Im only here to read the comments
ulibhoo kudontoniiiiiiiiiiiii
Very Sad!!! Loosing One Of The Few Young, Talented Public Orators! MHSRIP!!
tosefe tifa ndithu
Hoo sory Shaa!! nde kutukwana kuja mkumafaso????
R I P .
ameneyo wasamuka kachitatu katsala kawili
Going in peaces.mbala sizifa bwino.
Very bad may his soul rest in peace
Atidyera kwambiri ayende makola
No word, RIP
MMmmmmmm waisiya K20000
Wat happen
Sadi
Eya pang’ono ndi pang’ono nonse a DPP mukacheza ndi man bingu
zosachita kufusa izi ndipang’ono pamenepo zazikulu zichtikabe dikilan muzigwila
Ithink ukudziwa zambiri za izi
Kod Chimakhala Vyamba Chan?
kkkk was ala pitala naye akupita basi,
kkkk guys u hav t b serious #kudonton must rest in everlastng sanity
Ben Phiri Is Ths True?
Ana Apansi Pa Nyanja Sasoweka Zoyankhula Zawo, Remember dat “Moto Umapita Komwe Kwatsala Ntchire ” Get Ready.
yaaaaaa thats true imfa sichinthu choseweretsa sure
M.H.S.R.I.P
This politician’s if their doing their political they don’t think they can suddenly death like this but imfa sikusankha ilibe time kodomton samaembekezela angafele pa msewu phumziro kwa osalafe mzimu wake ukause mumtendele ngati mkwamtendele
Mmm kukanakhala kotheka ambuye mukanailora tisinthiseko tikupatseni uyuyu uyu koma basi conco tipanga bwanjiii MHSRIP
A’m crying deepdown my heart…..
May your soul rest in peace.
Iam really touched.
The boundary between death and life is just like a thread.
Mwayamba kufa athu akuba ndalama zamisokho, odzikundikira nokha mwasiyana nawo ntendere wapadziko kafikeni bwino
Man siboo kulankhula choncho Allah akukhululukile
mnyumba mwakwawo simunafike maliro dikila kaye uzaone momwe zimwapwetekela
Hahaha kundipweteka kwachiani athu adpp inu mumasakelera zopusanzo aziba sokho watha ine ndidzisowa magetsi kuchipatala ndizikalipira??? Ndiye ukufuna asafe iwe annie?? Kapena iwe siudzafa ingokoza mtima wako aise osati uzipanga against ine,
Kodi iwe ukhalangati ndiwe yekha ukudula nsonkho bwanji ?
Ngati adpp nu mumamva kuwawako??? Mesa makolo anu amakupatsani
eti a dpp wo samava nawo kuwawa chifukwa iwo akudyerera
Ngati arephera kumangitsa chipatala kumchinji uku mpaka muthu wamba ngati ine kumangitsa ekha komano kuthamangira kukadura liboni basi kkkkkkkkkiest
Anthu okuba misokho yaife akupita 1 by 1. Tsogolani kumotoko
Paja anati azithana ndi onyoza pitala,,nde wayamba iyeyo kutha
Iiii!Timvere chisoni kuti chani?Anthu onse amene akufawa timvere chisoni iyeyekha?Taluza anthu,iyeyu ndindani?
andale asamafune kut tixiwavera chisoni
andale asamafune kut tixiwavera chisoni
andale asamafune kut tixiwavera chisoni
andale asamafune kut tixiwavera chisoni
Rip ena akupanga like tione uzapange like bambo ako !
RIP
Ena azidandaula koma maso alipa tsogolo ufuna udindo wakewo.
Very sad news…. RIP…
Sibwino kunyoza nzako pathu sipa dziko , mwatibela zambili kauseni ndi ntendele ngati kuli kotheka
Kkkkkkkkkk kwene paravingativi chiyike vikuchika
Rip koma afera ndale awa too much talkative
Eish ngakhre ndiza maliro l cn say rip bt mmmmmh dx guyz talktive haevy kulakhura kwanu mmm wakumuto uwu??
Zikufunika kukhala ndima IGWE mmanyumbamu coz politics + witchcraft =death of politicians ..o in o RIP
ndekuti man wa adalibe igwe eti?? nde amachedwa. kkk
Iwowatu mwina anamuchotsa ntchito!
mmm nw this is strange achinyamata akuva koma nkhalmba zili phwiiii mumandoo..aaah tooo sad.may his soul rest pieace
R I P
So Sad Any Way It’s How God Made To Be Mhsrip
Yoooo Rip
Why black hero die young?
What a Secretary General wiv lost, Rest In peace Kudontoni
MHSRIP
Rest in peace
tikapezena msogolo
So pain but why malawi my God
May the good Lord keep his soul in eternal peace
R.I.P
Avaye bho
Tonse tidzafa ndikongodikira tsiku koma andalewa atsiyeni azifa. RIP
R I P mr secretary Gernal,we will miss u.
Zomvetsa Chisoni Komabe nthawi yakwana Abasi awuse mumtendere.
Sad
R I P very sad
eish!! R I P
kodi imfa ngati imeneyi ikutathauzanji ya ngozi koma zili bwino m’bomamo kufa koipa uko sikumoto koma rip
R I P
R.I.P
So sad….may his soul rest in peace
So sad RIP
Rest in Peace general
Mmmmhu
– 1 problem …..
Aaa Akudothi!Sory Malawi,Sorry DPP,Sorry Mr President. R I P MR Kudothi.
R.I.P
Sad to hear but we shall meet in paradise if nt shall gehenna no one will escape from death
Uuuu too bad sleep well
Sad, RIP
Too bad, may his soul rest in eternal peace.
sorry R.I.P
This 2016 eeeesh ayi… am speechless! …Watilanda Grace Chinga, Izeki, Zakaria, Mbendera, Mtafu, Chakuamba, Wame taika dzanazanalii lero ndi Hon.Kudontoni! mmmm..Kwathu si padziko koma ngodala okhawo amwalira ali mwa Ambuye coz zinazonse nchabe…. R.I.P
Politics is full of lies,jealous and even killings.I doubt if politicians really dies repentants.
Doubtful indeed
Ishiii, Bad News , Iwil Mis Him
Pachoka Mzako Pali Malo R.I.P Man.
Very sad RIP
Napepe……ambwiye
Mwakumananso kumeneko
mmmmmh rest in peace
mmmmmh rest in peace
Mmmmhu
Mmmmm! Sorry kalikonse kamoyo kanzalawa imfa RIP
thats true
2ru
Road accdent shaa.RIP
Rest in peace ,Nde mukapexa big wapta kumeneku unlike kwa Late Nana.
Akuyenela kupita peter is our father ku chipani as we r a family meanin to sy peter yo wataya mwana wake ndekusapezeka kwake ukhoza kukhala mwikho
kkkk zija nde mbwelele za munthu!!!
RIP
sorry
Ause mumtendere
Sad
Rip
R I P
R l P
RIP sad