Livingstonia University – Ekwendeni Campus is up in flames.
According to reports that Malawi24 has gathered indicate that the inferno has affected the store, IT laboratory, class and deans office.
The University students are currently trying all possible ways to extinguish the fire.
Among notable things that have been burnt by the fire so far include computers.
Police are at the University campus.
The cause of the fire is yet to be established. Reports are indicating that the fire began around 10 am.
This is coming barely within a week after fire gutted Lilongwe main market locally known as Kumpanipani.
Fire extinguishers came late and angry students stoned them away from the University campus.
more to come
bad news sorry
Let it be malaw means flames of fire,,,,moto wake ndiwomwewu bas
Good news
kodi sidazimebe muja munatiuziramu
kodi pa fbpa nkhan inkhale yamoto basi bwaji osaikapo zinthu zina zautsilu basi bomal m`malo moti linthandize anthu amene akugona ndijalawo ayambe zimenezo. amaotcha dala
Sorry For What Happened In Our Coutry,fire,fire Always What’s For?Let Beautfy Our Coutry Instead Of Destroying.
Mmmmmh kma yeah
Malawi… Flames right.
Musamutsutse chonmchi mzanu mwina ndi zowona akunenazo zina zimakhala zandale kufuna kuyipitsirana mbiri bas koma ife a Malawi ndiovutika kale ndiye mavuto kumangosanjana bas ofunika kupeza njira yothetsera mavutowa
Eish Malawi kod akukutani anthuwa zaonjedza tsopano!
so bad dzana timadandaula za cashgate tisanamalize dzulo ndizo timadandaula za zangozi za pasewu lelo mwatiponyera moto Eshiiiii end of de time Malawi wamoto wayakad may God 4give us
bwanji mawulamulilo achina janasi muthalika kumachitika gozizamoto atsogoleliwa koma amapepheradiawa ndakayika iwochomwe amadziwa ndikuba ndalama zamisokhozawanthu basi
On behalf of all people here in Ethiopia. am saying sorry
Zosabwino
Mulungu wanga malawi okoma uja lero wasanduka wa mavuto, anzathu ma a lubino kuphedwa, njala ndiyo anthu kuvutika, lero moto paliponse, Mulungu ngati kuli kutilanga tikhululukireni ndife ana anu, pepani ndithu
just go and help them kuzimitsa
Muotchenso nyanjayo kuti mutchuke ana a njoka inu.
Pitala ameneyo waotcha
the problem Satan is using our title flames of fire back to sender tiziona potchula maina azinthu
Yah agulile zanewn
Politics is rooting too much in our country,we don’t feel excited when one president is doing a wonderful job,we say this will jeopardize our chance of attaining the govt during the next election.Change your mindset politicans and put the nation at heart,pls?
Eeeee !!! kenako timva kut KAMUDZU STADIUM yaphya kenako msewu wa HIGH WAY sinanga mungootcha zina zilizonse mwalusatu ndimaches anuo asatana inu!!!!
Campus yosakongolatu sinyumba yalonda i
Mayi Marawa Watani Mayo Zikoranga Ene,,,
i blive they shud b mcp, bushiri and joice bandas fanz with the mission to turnish the image of gvmnt but know all we r malawians and shud led by one person and govmnt
Iwe ndiwe wabodza wakuwuza ndani zimenezo, kagwere uko ndi boma lakolo, tangonenani zamoto…mukutchula maina aanthu oti kutheka sizikuwakhuzanso nkomwe
Iwe kape eti Bushiri ukumutchulilanji?
Mutharika leadership hmmmmmmm
Pepan
Ndi omwe adaotcha tsika ku lilongwe.boma lititha ili.
Kkkkkkkkkkkkkkkk
SO BOZA.
Muziona
umphawi uli tho,palibe okalowa kumwamba.
Lord have Mercy…
we are out of cashgate now we are on firegate
umbuli wauzimu umapangisa kusaziwa kuti kodi chani chikuchitika…..tym ija ikufika pachimake olo tym yaNowa zinali chimozimozi koma sakaziwa kuti tsiku liti lomwe chimvula chizabwele……moti zimachitika mene zikuchitikilamu..kumamva kuti uku chakuti…mawa zina..pano nde yess welcome kukwanilisidwa kwamaulosi.
shocking!!!!
Ndikupempha aboma kt chonde fufuzani zamotozi ziononga katundu yense wa boma tawakokeni a joyce bandawo pamozi nda bushiriwo ndithu tawafufuzani ameneo atha kuziwapo kanthu zamotou
We need to pray for our nation let’s come together our sin may forgiven
Kodi aMalawi bwanji kukonda kulira ndikudandaula zilizonse,mwatani kodi?Mavuto samatha ndikulira koma amatha ndi mapemphero ndipo mukapemphera Chauta amamva.Anthu achulupiliro chochepa mwatani kodi?
Next week, lake malawi on fire
Ziyasani
OOO!! My god.
One day u gonna hear that state house in Lilongwe on fire coz of ths fuken homosexual u hv accepted
Kkkkkk state house it can be bette they ca fix as soon as posible bt this thing they dont care
Achewa mwayabaso kuotcha ku north?
Please God help our country
:'( very bad :'(
Flames on Fire……. Very Bad
Flames on Fire……. Very Bad
Flames on Fire……. Very Bad
kenako timva kut sanjika paris on fire
Too bad! Why always this? May almighty Allah help our nation
Dis fire thing, somebody has to do something abt it.
Eeee ambuye tichitileni chifundo Malawi akupita kuti yeeeeeeeeee
What? Nooooo don’t burn the north burn your central and south only please
Koma moto umenewu …. Something agween
Asakhale ma cadet awa.I dont trustbthese peopkr.Nda dani a Rev.Nyondo paja ndi aliyense ochokera ku mpoto.
Zachoka kungozi zapansewu zabwela kumoto tsopano eish
WHY??? Why?? Always fire fire fire!!! Eish
Iz It Bcz Of Multiparty? Nanga Kale Zinkachitika? Lets Talk Men.
Satana taku rakwiranjji kuti uzingo ononga dziko la kalawi la uphawi ndikale fees katundu ku kwara kusowa kwa ndalama anthu akungophana
FIRE IS A MAN CREATED HELPFUL SOURCE OF ENERGY . DESTROYS WHEN NOT CAREFULLY TAMED.
Koma malawi kkkkkk dzimu wakamudzu wakwiya
Ine kumeneko ndibwela akachoka akadzapuma akuluwa chifukwa dzandikwana dzimenedzi every day fire
mmm lord hv mercy on us!
Mumphuzapo ndani kusauka kuli tho nde muli busy kuwaula zithu ugalu wanu Malawi .
, not ayoba
U satan what do u nid 4rm us?
Ndiye mukuti mumpuza ndani? Thus political mafia by nzeru zatha.
am a victim of the incdence
We are towards the end of the world.why always fire in schools and markets?thats the power of satanism and power of darknes which is rounding in our country.
Is the world only going to end in Malawi? Why doesnt this happen in other countries if this symbolises the end of the world? The truth is that God is not happy with our nationv under Mthalikas evil leadership. WHY shouldnt u just go straight to the point.
Yes in malawi bcoz am a malawian i cant talk to situations which is happening in nigeria,somalia and other countries
Munthalika Evil? R u sure? Wh r u t say that?kkkkkk u could hv think first mr Desire Simon b4 typing
I don’t see anything to do with muthalika…muthalika is in UK and how can he forgot a lighting candle at ekwenden …..I don’t blame you but I blame your mother who wasted her time conceive a stupid person like you ..
Akupanga zimenezi ndi joyce ndi gulu lake mu satanic kufuna kupasa boma mavuto
Bodza,ndiwe chitsilu etii?
Bodza,ndiwe chitsilu etii?
Palibe nzeru ndi umunthu kumutukwana mnzanu chifukwa cha comment yake
Mbuli izi? hw can u tok bout ur frends mother? r u nt ashamed? anawauza nd ndan kut mayi ako akuthawe ukanali mwana? dats y u dnt c a reason 2 respect a frends mother! my frend this z a free country, w tok wat w want 2
God does not destroy those are works of the evil one!
Mzinda wathu nde utha ndi moto!!!
here in malawi life is hard
not good….
Km ku malawi kay
Wats happening in Malawi ?every week there s fire
Koma MCP yatienjeza
Very bad news
Mwafwa tafwa,phepani.
The gods r angry
sory wanganya tavisuska
Sad news
mmmmmmh nadi????? pepani wanganya
vry bad
Zalowa ndale otsutsa nde akumatuma anthuwa koma choti mudziwe DPP sizachokaso m’boma
Mmmmmmmmm Chibodza Mwakhutakhuta Ndalama Zadziko Osamangodya Bwanji
Aaaaaa siinu nomwe munachotsa amai anja mwati mufuna DPP
Mzatiberaso?
ndiwe mbuzi aise
Nzeru ulibe iwe, kuyankhula ngati opanda mzimu bwanji? Kukamwa tamuoneni
This is not a issue of politics,mphanvu za satana zagwila kwambili dziko lamawi kongot mpovuta kuizindikila ngat suli muuzimu
Oh
DPP ichoke or isachoke m’boma iweyo chako palibe ukhalabe chomwecho while enika akulamulawo mkumalemela ngakhale ana awo school akupita ku united kingdom
ukali wa mulungu pa kusochera kwa ana a israel.mawa mumva kuti nyumba ya president yapya.
Few days ago munayatsa msika wa ku Lilongwe lero tikumva za ku Livingstonia soon in future timvanso za ku Blantyre. Koma ndiye muli pachintchito ana asatana inu.
same like SA universities?
Sorry
Ka Ngimba Fyofi Twe BinaMALAWI?
God have mercy
Chayambitsa ndichan??
Zosadbwits our country s known as flames so flames means fire bt i si khuku za escom zapang iz thy r plying wth switchs
Sheeeeeee
Kodi Dzimamotozi Bwanji ?
Yakwiya ndi mizimu