Breaking : Livingstonia – Ekwendeni campus on fire

Advertisement

Livingstonia University – Ekwendeni Campus is up in flames.

According to reports that Malawi24 has gathered indicate that the inferno has affected the store, IT laboratory, class and deans office.

on fire.
on fire.

The University students are currently trying all possible ways to extinguish the fire.

Among notable things that have been burnt by the fire so far include computers.

Police are at the University campus.

The cause of the fire is yet to be established. Reports are indicating that the fire began around 10 am.

This is coming barely within a week after fire gutted Lilongwe main market locally known as Kumpanipani.

Fire extinguishers came late and angry students stoned them away from the University campus.

more to come

Advertisement

116 Comments

 1. kodi pa fbpa nkhan inkhale yamoto basi bwaji osaikapo zinthu zina zautsilu basi bomal m`malo moti linthandize anthu amene akugona ndijalawo ayambe zimenezo. amaotcha dala

 2. Musamutsutse chonmchi mzanu mwina ndi zowona akunenazo zina zimakhala zandale kufuna kuyipitsirana mbiri bas koma ife a Malawi ndiovutika kale ndiye mavuto kumangosanjana bas ofunika kupeza njira yothetsera mavutowa

 3. so bad dzana timadandaula za cashgate tisanamalize dzulo ndizo timadandaula za zangozi za pasewu lelo mwatiponyera moto Eshiiiii end of de time Malawi wamoto wayakad may God 4give us

 4. bwanji mawulamulilo achina janasi muthalika kumachitika gozizamoto atsogoleliwa koma amapepheradiawa ndakayika iwochomwe amadziwa ndikuba ndalama zamisokhozawanthu basi

 5. Mulungu wanga malawi okoma uja lero wasanduka wa mavuto, anzathu ma a lubino kuphedwa, njala ndiyo anthu kuvutika, lero moto paliponse, Mulungu ngati kuli kutilanga tikhululukireni ndife ana anu, pepani ndithu

 6. Politics is rooting too much in our country,we don’t feel excited when one president is doing a wonderful job,we say this will jeopardize our chance of attaining the govt during the next election.Change your mindset politicans and put the nation at heart,pls?

 7. Eeeee !!! kenako timva kut KAMUDZU STADIUM yaphya kenako msewu wa HIGH WAY sinanga mungootcha zina zilizonse mwalusatu ndimaches anuo asatana inu!!!!

 8. i blive they shud b mcp, bushiri and joice bandas fanz with the mission to turnish the image of gvmnt but know all we r malawians and shud led by one person and govmnt

  1. Iwe ndiwe wabodza wakuwuza ndani zimenezo, kagwere uko ndi boma lakolo, tangonenani zamoto…mukutchula maina aanthu oti kutheka sizikuwakhuzanso nkomwe

 9. umbuli wauzimu umapangisa kusaziwa kuti kodi chani chikuchitika…..tym ija ikufika pachimake olo tym yaNowa zinali chimozimozi koma sakaziwa kuti tsiku liti lomwe chimvula chizabwele……moti zimachitika mene zikuchitikilamu..kumamva kuti uku chakuti…mawa zina..pano nde yess welcome kukwanilisidwa kwamaulosi.

 10. Ndikupempha aboma kt chonde fufuzani zamotozi ziononga katundu yense wa boma tawakokeni a joyce bandawo pamozi nda bushiriwo ndithu tawafufuzani ameneo atha kuziwapo kanthu zamotou

 11. Kodi aMalawi bwanji kukonda kulira ndikudandaula zilizonse,mwatani kodi?Mavuto samatha ndikulira koma amatha ndi mapemphero ndipo mukapemphera Chauta amamva.Anthu achulupiliro chochepa mwatani kodi?

 12. Satana taku rakwiranjji kuti uzingo ononga dziko la kalawi la uphawi ndikale fees katundu ku kwara kusowa kwa ndalama anthu akungophana

 13. Koma malawi kkkkkk dzimu wakamudzu wakwiya
  Ine kumeneko ndibwela akachoka akadzapuma akuluwa chifukwa dzandikwana dzimenedzi every day fire

 14. We are towards the end of the world.why always fire in schools and markets?thats the power of satanism and power of darknes which is rounding in our country.

  1. Is the world only going to end in Malawi? Why doesnt this happen in other countries if this symbolises the end of the world? The truth is that God is not happy with our nationv under Mthalikas evil leadership. WHY shouldnt u just go straight to the point.

  2. I don’t see anything to do with muthalika…muthalika is in UK and how can he forgot a lighting candle at ekwenden …..I don’t blame you but I blame your mother who wasted her time conceive a stupid person like you ..

  3. Mbuli izi? hw can u tok bout ur frends mother? r u nt ashamed? anawauza nd ndan kut mayi ako akuthawe ukanali mwana? dats y u dnt c a reason 2 respect a frends mother! my frend this z a free country, w tok wat w want 2

  1. This is not a issue of politics,mphanvu za satana zagwila kwambili dziko lamawi kongot mpovuta kuizindikila ngat suli muuzimu

  2. DPP ichoke or isachoke m’boma iweyo chako palibe ukhalabe chomwecho while enika akulamulawo mkumalemela ngakhale ana awo school akupita ku united kingdom

 15. Few days ago munayatsa msika wa ku Lilongwe lero tikumva za ku Livingstonia soon in future timvanso za ku Blantyre. Koma ndiye muli pachintchito ana asatana inu.

Comments are closed.