‘Just kill me!’ cashgate convict tells court

Advertisement
Leonard Kalonga

A convict in a cashgate case on Tuesday cried in court after being sentenced to five years in jail.

The Lilongwe High Court sentenced the convict, Angela Katengeza, to five years imprisonment for her role in stealing public funds amounting to K105 million in the scam which is commonly known as cashgate.

Leonard Kalonga
Angela Katengeza asked to be killed.

But after she was sentenced by Lilongwe High Court Judge Justice Fiona Mwale, Katengeza cried and told the court she wished she were dead.

“Just kill me, I don’t want to be alive anymore. Just finish me!,” cried Katengeza

Katengeza and former director of tourism Leonard Kalonga were charged with conspiring to use Katengeza’s construction company to siphon public funds.   

Katengeza was found guilty of fraud and money laundering and she has now been jailed while Kalonga is currently awaiting sentencing after pleading guilty to similar charges.

The massive embezzlement of public funds was exposed in 2013 during former President Joyce Banda’s regime.

Advertisement

235 Comments

 1. Malawi awa atiwotchadi ambiri koma bwanji anthunu simukufuna kutimvera chisoni anthu avutikafe? Nkhani daily ikhale yotibera ndalama mulungu akuwona

 2. Koma 5yrs yachepa zedi asaaaas woba njinga or nkhuku mumamupatsa 10yrs koma woba ndalama zankhaninkhani kumupatsa zaka zochepa….mulungu adzakulangani ndithu ma jugde omwe mwapeleka judgement imeneyi…..iyaaaaaa favouritism basi asaaaaa

 3. Koma 5yrs yachepa zedi asaaaas woba njinga or nkhuku mumamupatsa 10yrs koma woba ndalama zankhaninkhani kumupatsa zaka zochepa….mulungu adzakulangani ndithu ma jugde omwe mwapeleka judgement imeneyi…..iyaaaaaa favouritism basi asaaaaa

 4. 5Yrz yachepa chonde ndipempho langa kt maiwa muwaonjezere zaka zoti akakhale mundene , atleast itakhala 15 yrz coz ndi mai osowa chikondi uyu mai oipa.

 5. kill her plz has volunteered herself thus being patriotic. u have set a good example that all cashgate convicts shld be killed.

 6. She robed our tax money and ending up speakig nosence like this?How many good citizens have been dying due to lack of proper madication,that could be bought with that stollen tax money? that is very bad GOD will punish you after saving that small punishment.

 7. Mmm mayi palibe zokuphani apa ife timakukondani kwambiri. Mukatidyele mugayiwa kundende basi kuzolowela ena Kori ndi ma sausage eti uyisova…

  Mwaphetsa anthu mbiri muzipatalamu inu mukhawule basi!

 8. 5 years basiii???? zilibho ifeso tizabako…. the more mount of money u steal the lighter punshment u’ll b given…. less amount u steal heavy punshment u’ll b given…. #by_the _constitution_of_the_republic_of_malawi.

 9. There is evidence that the judge and the convict coluded, so that she behaves in such a way so as to detract pipo from scrutinising her peanut sentence and focus on her cries. And thats exactly what malawians have done. Let us deal with this stupid judge. We have corrupt judged in malawi. lets deal with these judges

 10. kkkkkkkk zikundigiligisha bwanji iyaa bac ndasiya kuba nkhuku ndi mbudzi ndiziba dola zambiri iyaa chilango chake nyatwa ku Capital hill chenjelani nane ndikubwera ndi cash gate 2

 11. Fire goes where there is grass….Samalani mabwana enanu kwakula nkusagwidwa.and one day u will face the music ikangokwana yachifote……..

 12. Thank the Gods for smiling on you. Dont even attempt to appeal. dont cry either. the period iz too short compared to the offence you committed.

 13. A majority of judges in malawi are full of favouritism..,how come wokuba cellphone kumpasa 6yrs but wa cashgate 5yrs..,whats dat????…anakakhala kut wabayo ndiwosauka anakampasa 20yrs…

 14. Foolish woman, you are even lucky because if it was me I would have given 30, because the 5 she is crying of is too lenient, because when it comes to her case, she has a chance of coming out through the presidential pardon some day, that will surely happened

 15. the best way ndikubweza ndalamazo, kukhala ku prison even 50 years is useless, Malawi wont benefit anything. komanso posachedwa timva kuti watuluka pa belo.

 16. Mwamumvela chisoni poti ndimunthu wamayi? Kodi wakuba mamillion mukuti zaka faifi, ndeno oba ng’ombe adzikhalano kundende sabata imodzitu. Koma amphawife tilipamavuto. Mpakana kutimanga zaka seven chifukwa cha mulandu womenyana pofunsana ngongole? Tiona mmene zithele. Mudzandile ujeni ngati mai ameneyi atakhale tizaka faifi tonse amuuzato kundendeko.

 17. Shame there is no justice on earth may this bitches soul burn in hell

 18. Kufa sapempha ngati mchele kwa neba koma amadziwa kuti mulandu wake ukufanana ndi mulandu wabwana a muluzi bwanji iyeyo akupita ku ndende a muluzi ali free muganizileni naye ngati abwana a muluzi,musamatelo ndi dziko lanji losawona anthu osauka, I’ll die here… i don’t need your bad judgment and don’t count me as a Malawian count me as a man from heaven you shit

 19. Musiyeni abale anazoloweratu wofuwofu nanga kundendeko azikakhala pa chani sofa iliko? mmmmmmmmmmmmmmmmmmmmmm mumvereni chisoni ine ndie ndamumvera kale chisoni nanga inuyo anzanga?

 20. Amai amenewa osawapha ndi mfuti ayi chonde koma akamve mene kumakomera kundende.Ikamati 4 oclock atawalowesa kale mkati zimakoma kwabasi sinanga ndalamazo pomadya zimakoma.Ngati ndiwe dolo uchite appeal mulanduwo utulukeko kumeneko

 21. 5 Years Munthu Wakuba Ndalama.Ku Pilizoni,wakupha Albino 17years,kumugwira Munthu Ndimatumba Achamba Mukuti 30 Years. Musieni Amene Akugulitsa Chambayo Iphani Akuba Ndalamazo Ndi Amene Alukumphawo

 22. Akadakhala Kut Sadamugwile Akadakhumba Kuphedwa Uyu? Bwezi Kuli Maumboni2!” Ambue Wandichitila Zazikulu” Ndalama Zakubazo? Mwachita Bwino Mwina Ena Atengelepo Phunziro! Koma Zakazo Zachepa Coz Mlandu Wa Kuba 4n Ndi 3yrs Kaya Mosewalero, Tinene Kut Ameneu Waba Ma 4n Awili?Mmmh!!!!!!!!

 23. F*** !! Wakuba mbuzi Akuti 6 years and uyu waba more than 100 million kwacha Akuti 5 years … Mncweeee !!! Malawi Ndi mbuzi

 24. F*** !! Wakuba mbuzi Akuti 6 years and uyu waba more than 100 million kwacha Akuti 5 years … Mncweeee !!! Malawi Ndi mbuzi

 25. Mbava Ikuti” Mungondipha”mtengeni M’bweletseni Kuno Ku Ndirande Timveke teyala Timuyatse Moto,ena Achitidwe Ngat Uwu Atengelepo Phunziro,magamulidwe Ake Ankhan Akakhala Amenewa Malawi Azakhala Osauka Mpaka Kale,mbava Zikuluzikulu Zikuidwa Kumbuyo Ndi Majaji

 26. Mbava Ikuti” Mungondipha”mtengeni M’bweletseni Kuno Ku Ndirande Timveke teyala Timuyatse Moto,ena Achitidwe Ngat Uwu Atengelepo Phunziro,magamulidwe Ake Ankhan Akakhala Amenewa Malawi Azakhala Osauka Mpaka Kale,mbava Zikuluzikulu Zikuidwa Kumbuyo Ndi Majaji

 27. Ma Million Onsewa Basi Dzaka 5, Kufanana Ndi Okuba Mbuzi, Palibe Chilungamo Apa, Kunamiza Amalawi Uku, Chimodzimodzi Ku Muleka Apa,

 28. Ma Million Onsewa Basi Dzaka 5, Kufanana Ndi Okuba Mbuzi, Palibe Chilungamo Apa, Kunamiza Amalawi Uku, Chimodzimodzi Ku Muleka Apa,

 29. I (Malawi) don’t offer offer death penalty,even the albino killers are hosted,being given free food(once a day). So i cant kill you…or else…kill yourself…bt i would have advised u to be patience…three yrs is not too much.

 30. There is no seriousness. 5 years is just nothing as compared to gravity of the cashgate. Many people would have access to the Govt money she embezzled. this is leniency at its best.In actual sense she will only serve two years. By crying she was expressing excitement. Angella you are lucky juju wakuthandiza

 31. wina kuba Phone ati 8 years in Prisonment with hard labour….uyu anaononga ndalama zankhaninkhani zot zikanatha kuthandiza anthu angapo akufa ndikumzumzika mzipatala umu…koma Malawi suzatheka…chilungamo tikachipeza kwa Ambuye basi tiyeni tingodikila pa tsiku lomaliza….

 32. Oh! Why was she crying while some Malawians lost their lives due to shortage of medicine in hospitals bcoz of her stupid behaviour? She would have just said amen bcoz 5yrs is asimple judgement

 33. the judiciary has shown partiality on this matter.they could have given her 10yrs and above not 5yrs.and that katengeza saying just kill me is nosense.have you forgotten how you killed malawians when you swindled the billions from the government coffers?if malawi is having acute shortage of drugs in hospitals,maize in admarc depots,unemployment levels,etc its due to mismanagement of funds among top government officials including yo idiot katengeza.mxxxx.

 34. Nanga bwanji Osamupha ,zopusa zimenezo moyo wake odzikondawo kumaba ndalama za anthu ovutika kumudzi,dziko silifunika ndi anthu odzikonda ngati amenewa ngofunika afedi .

 35. Anthu inu penapake ndinu mbuzi..zaka five zachulukaso kwambili..anaba dolla zambili nde dollazo akuyenera kumpatsa nazo zaka zochepa kuti azizazigwiritsa ntchito mdziko muno…mwina anazibisa??..nde angazigwilitse ntchito ndani?

 36. It was fake why she didn’t take tamek at the same place?She knew the judgment already.It was just gimmick to fool malawians as if its a shocking news…..

 37. Zachisoni ndithu this katengeza’s case is similarly with Bakili muluzi’s case, but muluzi is walking free katengeza is jail oh shame poor judgment of Malawians courts, always defend those who’re with good profile.hahaha…. poor judge who handle katengeza’s case

 38. Mmmmmmmmmm kkkkk kod cashget ilipobe koma ndetimangidwa ambiri,,,,,,,,zigawan zakazo win afa osadwala muzitinge bwino2

 39. She killed many people in Malawi hospitals bcause she stole the gvnm money, she is stupid, bastard,she must die in Jail.

  1. Then she was involved in the practice.No ways she can be Cashing large somes of Cheques more oftenly without knowing where it is from.Amadya nawo mbuzi ameneyu

  2. Then she was involved in the practice.No ways she can be Cashing large somes of Cheques more oftenly without knowing where it is from.Amadya nawo mbuzi ameneyu

 40. wakuba mondokwa lyf in prison while the cashgate pipo were serving asentence of 5yrs, the judgement its nt enough, amalawi mwatani kodi?

 41. U r luky sister, if it was that regime after Asamunda u could hv die indeed. And 5yrs is not enough according to your crime mw was expecting 10yrs and yrs above in jail with hard labour.

 42. okuba khuku zaka 12, wathyola nyumba zaka 8, dziko kukondela uku Wa cashgate Zaka 5 ndendichimodzmozi ndi nkazi otenga kulela wazaka 5 kuti asatenge mimba.munakawonjezela kuti awowo atengele chitsanzo

 43. Amenewo akuyeneladi kuti aphedwe chifukwa Iwo anapha kale anthu ambiri posolola ndalama zankhaninkhani zomwe panopa boma likutukwanidwa each and everyday kuti palibe chimene likuchita.

 44. No ma’am, we will not kill you. But we will cause you great phain…(assuming a sabbatical of 2 yrs of good behaviour in Maula is painfull!)

 45. who should kill you? kill yourself woman! m’mene akuphedwera abale ndi alongo, iwe wati just kill me? mbuzi akukonderanso apa.

 46. Ngat akufuna imfa mpatseni mfuti aziombere yekha,koma asanatero ayambe wabweza ndalamayo kaye,azipita bwino tilibe naye ntchito abale athu akuvutika mzipatalamu ena anamwalira kamba kosowa mankwala ataba ndalama zaboma ameneyu nde iye azilira ndi 5 years

 47. Just kill her pliz,she stole the money that would have been to buy drugs in public hospitals,coz of her stealing it resulted into no medicine in hospitals and many people died.

  1. Deal with the one that is found for others to learn lessons !!
   God wil tell Himself about that 92 billion,wait nd see bro Ebrahim Jamal ,ife ana kumasilira tea kwa iwowo ,!chosecho ndalama zakuba

  2. Peter Mutharika said on radio after few months in office that he was concerned by 92 billion kwacha that was misled by DPP under his brothers leadership, why must we wait for God to tell us when the blood brother have already admitted? Is 92 billion kwacha a joke?

  3. I dont trust dpp,they stole that money and he is covering it up,when he looses its when a new government would work on it bro Ebrahim Jamal

  4. I dont trust dpp,they stole that money and he is covering it up,when he looses its when a new government would work on it bro Ebrahim Jamal

 48. Akulira cause of five years? Does she know that what she did means malawians will suffer for more than five years? Infact that’s a light judgement she should have been given 80 years

 49. Ku Malawi Former Heart Of Africa Koma Pano Ndi Heart Of Cashgate Zoona Abale Athu Kufa Ndi Cholera Mankhwala Akusowa Inu Angella Mukudya Ndalama Ya A MPhawife? Angokuphanidi Basi

 50. 5 yrs ukuseweza ukanakhara kt sunabe ndikhulupilira ukunaipanga ndalama imeneyo mwachilungamo pa 5yrs yomwe ukakhale osaona amuna ako kukugwiragwirayo

 51. No madam! We do not want you to die but realise that what you did was totally wrong and uncalled for. You need to very thankfull for being given such a lenient sentence. Many others of your kind will follow suit. The millions you embezzled belonged to the poor masses many of which have now died of hunger and lack of medicines and proper medical facilities. One by one, you will slowly but surely go down.

 52. Kodi mukuganiza kuti zinthu zingakhale bwanji patakhala boma limodzi lolamulira dziko lonse lapansi? Masiku ano anthu ambiri ali pa umphawi wadzaoneni, pomwe ena ndi olemera kwambiri. Koma patakhala boma limodzi lolamulira dziko lonse, lingamaonetsetse kuti anthu onse ali ndi zimene amafunikira. Kodi mukuganiza kuti anthu angathe kukhazikitsa boma loterolo?— Werengani Yeremiya 10:23 . Kuyambira kale, maboma akhala akulephera kuthandiza nzika zawo, makamaka anthu osauka. Komanso maboma ena amapondereza anthu awo. (Mlaliki 4:1; 8:9 ) Koma Mulungu Wamphamvuyonse watilonjeza kuti adzakhazikitsa boma limene lidzalowe m’malo mwa maboma onse. Wolamulira wa boma, kapena kuti Ufumu umenewu, adzaonetsetsa kuti nzika zake zonse zili ndi zofunikira.— Werengani Yesaya 11:4; Danieli 2:44 . Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita zotani? Yehova Mulungu wasankha Mfumu yoyenera kulamulira dziko lonse yemwe ndi Mwana wake, Yesu. ( Luka 1:31-33 ) Yesu ali padziko lapansi, ankakonda kuthandiza anthu. Choncho akamadzalamulira dziko lonse adzathandizanso anthu a mitundu yonse.— Werengani Salimo 72:8, 12-14 . Koma kodi anthu onse angafune kuti Yesu akhale Mfumu yawo? Ayi. Komabe, Yehova ndi woleza mtima. (2 Petulo 3:9 ) Iye akupereka kwa anthu oterewa mwayi woti aphunzire zokhudza Yesu n’cholinga choti avomereze kuti adzakhale Mfumu yawo. Posachedwapa, Yesu adzachotsa anthu oipa n’kubweretsa mtendere pa dziko lonse.— Werengani Mika 4:3, 4 . Mavuto ngati nkhondo, njara , matenda ndi Imfa zikutha posachedwa ndipo Yehova Mfumu ya chilengedwe chose apukuta misozi yose maso Mwathu.-Chivumbulutso 21:3,4.

 53. Ndalama yonseyo ndi chimozimozi kupha ma Albino kumeneko tinganenenso kuti iye anapha ambiri zedi nde munthu akupempha imfa mukumukakamiza kundende bwaji?kunali mfuti ku courtko?

  1. Kuteroko anthu omwe akupha albino ndi amenewa,mai woipa mtima ngati ameneyi,kenaka aziti ma President athu akulephera nthito uku mahulewa akumangozilemeletsa okha.

  2. Adwiriri okhaokha awa mamiliyo onsewo munthu mmozi wapha anthu angati ameneyu?nda tax otolera kwa anthu osauka olima tomato ndi kabichi,anthu oipa asatana

  3. kkkkkkk koma gama,,,amene akupha azungu mzika za malawi amene ali mgulu la 17mita in population ndi maboss moti tipovuta kutha kwake mchitidwe umeneu coz zikuoneka kuti zinayambira kumutu pano zili mchiuno xikuthamangira ku myendo

 54. KKKKK, KOMA DZIKO LIMADANA NDI MUNTHU OSAUKA NDITHU UYU AKULILA NDI TIZAKA 5 MPAKA KUPEMPHA IMFA PAMENE WAKUBA MPHIKA AKUMANGIDWA ZA 30, NDIYE UKUPEMPHA IMFA NDIYE KOTHAWILAKOTU USAGANIZE KUKAPUMA KUMENEKO NDIYE DZILANGO DZAKE BOLA ULANGIDWILETU PASI POMPANO. UKO NDIYE KULIDI OZUNZA. BOLA KUNO AKULANGE DZAKA 5 NDIYE ULAPE UKALAPA UBADWE MWATSOPANO KUTI MOYO WINAWO MWINA UKAKHALE MPUMULO.

 55. Munthu akupempha mphtho yake ndi chifukwa chiyani simunamuphe? Mphotho ya uchimo ndi imfa ndiye munthu amadziwa kuti anachimwa powononga misonkho ya anthu osalakwa omwe tsiku ndi tsiku akufa kamba kosowa mankhwala muzipatala za dziko lino.

 56. 5 years yomweo ine ndadandaula kuti akupatsa zaka zochepa,ndalama za amphawi zimenezo ,ine ndikapanga appeal zaka zachepa zomwe ukakhale kundende cashgate pipo anthu oipa inuuu!!!!!!

 57. pa 5yrs wabweza ndalamazo? If not you hv done nothng judges. Akatuluka azazidya bwanj? nd mmakhot momwe katangale eeeee koma Malawi wafkapo… akatuluka muzagawane ndalamazo… Yekha amalira kut bola aphedwe pozindikira kut anabadi zambir now ua sentencing her as little as 5yrs? Law enforcers ua not serius

  1. While oba njinga umva akuti 7 yrs in jail eeeshiii!! dziko likuwawa ili kwa wanthu osaukafe,koma tsiku likuza azayankha Namalenga mafuso anthu ndikulila kwanthu!.

  2. Alibe mulandu.Vuto a Malawi umbuli ndi waukulu kwambiri.Even ma judge sakuziwa mumune dziko likuyendera kunkhani yazachuma..Pa nkhani izi Mulandu ndi Kufuna kupha Mphwiyo basi.Zinazi Mulandu palibe.Ndalama zizizungulira mumanja mwa anthu.Boma ndilo likubera anthu osati anthu akubera boma.

 58. Koma woba mbuzi ndiye 20 years ? Zachamba zimenezo

 59. Osawanyengerela anthu amenewa adidyela ndalama zathu zambiri, ndipo 5yrs yechapa.

 60. mbava zokha zokha 5 pali chani apa.mwagawana gawana mbuzi mada fuck ma jug osaziwa malamuro.mwamphunzira school iti m’kugamura za cash gate 2+2 fsk

 61. Zazi, Okuba Nthiko Mukumuza Azkakhala 20yrs Pamene Mfiti Zokuba Ma Million Mukut 5yrs, Ok, Am Prison Warder At Maula Atipeza Ameneyo, 5yrs Imeneyo Aywona Ngat 90yrs.

 62. Innocent.Saona chomwe chasitsa dzaye kuti jobvu ithyoke munyanga.Black destroying black pple.Racist oppresive colonial courts with western black educated pple who hav mastered western educational ignorance managing the colonial oppresive relics .

 63. kulibe zokupha aisey uone Kaye kiyama anthu afa nzipatala mutaba money agalu inu..ngat mukufuna angokuphani mudikile Kaye museve 5years kenako bhobho

Comments are closed.