Former MBC TV Presenter killed by armed robbers

Advertisement
Dexter Kanike
Dexter Kanike
Dexter Kanike slain.

Ex Malawi Broadcasting Corporation (MBC) presenter Dexter Kanike died this morning as he was beaten by unknown robbers at his home in Chirimba, Blantyre, Malawi24 understands.

Kanike presented the flagship Melody Hour music program on the state owned channel.

Reports say his home was ransacked by thugs who stole property in the house before they killed him by hacking, according to reports.

He was taken to hospital where he was pronounced dead.

Advertisement

353 Comments

 1. ifa yanthu ngat awa, boma kapena otsutsa amakhala akudziwapo kanthu. mwakanika kumuteteza alimoyo komo2 posachedwapa tikhala tikumva kut mukufufuza zaifa yake, malawi my country my home! kuphana tsopano sinkhan RIP PALIBE WAMBEU NAFESO TIKUDIKIRA TSIKU LATHU!

 2. May his soul rest in peace, very difficult to forget

 3. They always announce to tip police kwa Munthu ameene akukudabeitsani for your community safety. Pano muli busy kuti Ma Robbers mbwe mbwee! Yet a president sawaona mukuwaonanu you fail to tip police about them. How will your community crime free abale azanga? These people are dangerous, president himself cnt arrest or catch them. You are the ones can help to get rid of robberies and any crime.

 4. Thawi inakwana olo mutati mumufuse okufayo amafuna kuzimangilila ndi maludzi ali kati molingalila ndipa mene pabwela akubawa mwana wa muthu ayenela kufa koma soka okwanilisa malembayo q

 5. Koma this life eishie,,, ma robbers ali mbwee ,, apulezident nawo angofuna kumadya bwino koma ife anthu osauka kumatoleza,,, apolisi nawo ayamba mjuga,, in hospitals no medics,,people with albinism being slaughtered like goats,, kugwililira patsogolo,, why are we killing our fellow malawians,, tu hell with yur regime,,, am concerned nah,, rest well Mr,,, mpake ma Mps akumagona mu parliament cos of yur nonsense speech,,,, go tu hell

 6. This country called Malawi is the same type of wild uncivilized place like SOMALIA

  It’s a dangerous EVIL place that nobody with a brain or heart should visit

  ATTN: FOREIGNERS!!! Stay out of this evil, corrupt, shameless, lazy, JEALOUS place

 7. Rest in peace mzimu wake uwunse mumtendele,ambuye mulandileni mfungatileni,kodi amalawi tikupindula chani tikamamphana ngati khuku?dzikodi likupita kumapeto.

 8. This this why I am in afghanistan learning how to protect myself I don’t trust the police nowadays,and I swear at the end of this case no one will be arrested

 9. Mukamachita like ndi uthenga wachisonwu ndiye kut zakusangalasan?Chochitila like uthenga wa malilo ndichan?Chofunika kungoti,RIP ngat amachita zofuna ambuye Mulungu.

 10. Eish koma zinazi abale,Bring us back to you, LORD!Bring us back! Restore our ancient glory.mlandilen mzimu wawo ndimtendele.

 11. Thus the consequences when the leaders are elected in the name of politics,,,
  Nothing indid to point out by this régime,
  You will hear some one saying its too early to say that,really?
  Igot your point brother Manda
  Munthu amaoneka wanzeru Ali mwana the opposite is true!

 12. Thus the consequences when the leaders are elected in the name of politics,,,
  Nothing indid to point out by this régime,
  You will hear some one saying its too early to say that,really?
  Igot your point brother Manda
  Munthu amaoneka wanzeru Ali mwana the opposite is true!

  1. We ain’t talking abt the population,we r talkn abt security.evn if 90 percent of our population were the police,we wudn’t eliminate crime completly & that’s a fact #Martha I hop u’v eva heard abt the word “example”?

 13. Nde mwati wankulu wapolice boma lamutumiza kunja kokaphunzira za death sentence?? R I P bwana, iwill never try to vote 4 u again(pitala mutharika)

 14. Nde mwati wankulu wapolice boma lamutumiza kunja kokaphunzira za death sentence?? R I P bwana, iwill never try to vote 4 u again(pitala mutharika)

 15. let’s call for God’s intervention what a life in Malawi taking responsible souls, killing innocent souls leaving children helpless,and making them orphans I can’t imagine the situation so sad may God punish evils here on earth.

 16. If these butchermen wanna be captured, treat them just the same as they have done to our former tvm presenter. Otherwise if they will be handled mercifuly; they will do more harmful to innocent souls.

 17. Some are saying, y we are blaming the government, so we should blame whom? You have to know that, those perpetrators they are taking advantage of loosen security which we are having now, panyumba ana akagona ndi njala chifukwa chopanda chakudya, ndiye kuti makolo ndi opanda nzeru

 18. We brimming police because most of them they not doin their wrk, nd most of them they not their for doing their wrk not at all…some like political people those people they are their for wrking in their pocket not to helping people no no……

 19. kuphedwe kwamunthu monga uyu samaphedwa ndimunthu wamba monga ifeyo. koma iwowo akumipandowo akuziwa kuti chachitika ndichiyan. ndiye awagwila bwanji chifukwa ndiakumipandoko. RIP.

 20. kuphedwe kwamunthu monga uyu samaphedwa ndimunthu wamba monga ifeyo. koma iwowo akumipandowo akuziwa kuti chachitika ndichiyan. ndiye awagwila bwanji chifukwa ndiakumipandoko. RIP.

 21. Amalawi Nzanthu Akachitabwino Walakwa Akamavutika Ndikumamuseka Tirinditsaka Sitidzatukuka Tizingo Khalira Kupempha Basi

 22. Amalawi Nzanthu Akachitabwino Walakwa Akamavutika Ndikumamuseka Tirinditsaka Sitidzatukuka Tizingo Khalira Kupempha Basi

 23. Makosa tiyeni tidziyankhula ngati amzeru nkhani iri apa ndiyazathu waphedwayu,sizandale apa kaya ngati zingakhale kt zikukhudza ndale chabwino may be you have information on that ok,palibe zokhudza president apa,kmanso apolice sizingatheke kt adzipezeka kunyumba ya aliyense kmano ndichikhulupiro anthu apanga zimenezowo agwidwa ife kunalibe kma mulungu amawaona,chonde amakhoti kmanso apresident anthu oterowa adziphedwa lamulo lidzigwira ntchito,president adzi saina,zikuonjezatu zimenezi mwava akhoti ndi apresident ndanenatu.

 24. Makosa tiyeni tidziyankhula ngati amzeru nkhani iri apa ndiyazathu waphedwayu,sizandale apa kaya ngati zingakhale kt zikukhudza ndale chabwino may be you have information on that ok,palibe zokhudza president apa,kmanso apolice sizingatheke kt adzipezeka kunyumba ya aliyense kmano ndichikhulupiro anthu apanga zimenezowo agwidwa ife kunalibe kma mulungu amawaona,chonde amakhoti kmanso apresident anthu oterowa adziphedwa lamulo lidzigwira ntchito,president adzi saina,zikuonjezatu zimenezi mwava akhoti ndi apresident ndanenatu.

 25. Nkhani Ilipo Apa Ndiyakut Anthu Tataya Chikondi Takonda Chuma Tayiwala Chilamulo Chamulungu,osati Andale Kapena Apolice Ayi, Kodi Iwowo Pomumpha Munthuyo Mmitima Mwawomo Samaziwa Kut Akulakwa? Ambuye Mukuziwa Ndinu Zonse Tiyika Mmanja Mwanu Mzimu Wa Malemuwa Uwuse Muntendele

 26. Robbers, why? Bola mukamusiya mkungotenga katundu yo. May His Soul Rest In Peace

 27. Ena amati eeee apresident ndi aprofessor amaphunzitsa Obama mbuzi yamunthu ngati imeneyi mumbiri yamalawi malubino sanasakazidwe ngati zililipano mwinaso akuziwapo kanthu mulomweyu daily kuphedwa kugwirira akati agwira anthu ndi cashgate basi mulomwe woyee kubadwa bwino mkwanu bambo u ndiutsogoleri

 28. why murdering innocent people like him?is better to slaughter the one who take this nation for granted & rulling brutally,curruption,segregating

  1. Why all these killings abale? Ma Albino lero Dexter. Why Malawi God? Atleast bwana should consider organising special prayers for our country. Am hurt.

 29. Joel Mkandawire you say this government has failed in terms of security? Tell me anything this government has done better since analowa muboma ?.Don’t skirt around say the truth that, this government has failed. It’s two years now. still nothing to point out. Munthu wa nzeru amawoneka adakali mwana

 30. Amalawi tizakhala osalira mpaka kale,how can munthu wanzeru mzake azika blamer a police kut akulephera kugwira chifukwa munthu waphedwa kwawo. Mukufuna azilondera nyumba za anthu kut kuphana kuthe? Ma neighbors ntchito yawo ndi chani? Bwanji sanaimbire a police? Even ku america anthu amaphedwa koma security is high. Ku south africa security ilinso tight koma everyday anthu akuphedwa. So what special with malawi? A police samagwira munthu b4 criminal,koma zikatero ntchito ali nayo ndiyoti afufuze mpaka anthuwo agwidwe,thus security. Out of 17million population,a police its less than 1million nde mumati azitani kwenikweni? Za ndale tamazisiyani sizikupindulirani.

  1. Jst to add we only have 13,789 police officers only in malawi to protect 16 million people, anzathu a school tachitani masamu mutiuze ratio yake

  2. Jst to add we only have 13,789 police officers only in malawi to protect 16 million people, anzathu a school tachitani masamu mutiuze ratio yake

  3. Thanks,our views will transform someone’s mindset to be a responsible citizen than kumangonyozana zilizonse,zomwe sizingatithandize ngat ife aeni ake a malawi. Kuzindikira ndi mphatso yabwino. Mwandipatsa chimwemwe nonse ndi mfundo zathu zogwirana. Titalimbikira uthengau udzafikira anthunso ambiri

  1. Winanso waphedwa ndi tructor dzulo ku Ilovo, should we blame the government again for not providing security? poor acusations,

  2. Winanso waphedwa ndi tructor dzulo ku Ilovo, should we blame the government again for not providing security? poor acusations,

  1. Ur mind is stupid. Umafuna a police azilondera nyumba iliyonse? Bwanji iyeyo sanalembe mlonda? Lilipo dziko komwe kulibe okuba amene amapha? Bolanso ku malawi,koma ku south africa munthu amaphedwa ndi akuba masana anthu akuonerera koma a police ali mbweee.

  2. Dont show ur stupidity you fool since Peter munthalika become pressident how many innocent people have been killed and beside that witch south africa do u talking about that i dont know?

  3. musaonetse uchitsiru wanu bwana Luku apa and dont run away from the fact, it happens worldwide vuto losayenda mmayikomu komanso kusasata current affairs ndilimeneri and u always blame mtsogoleri, what a shame!!

  4. @ Mr clement sometims umunthu ndiwabwno mwayenda kut inuyo kumene anthu amasekelera anthu akamafa mwachsawawako?? ..kwina kulikose kulakwsa kwa ana m’banja anthu amayang’ana kholo kumene inuyo musamaone zodabwsa anthu tkamaloza chala mtsogoleri coz iye ali ngat kholo lathu ….ndamumva wna akut iwe umafuna azichta kulondera m’makomo mwawo mmmm kulankhula mosakhala bwno kumeneko bwana zitakhala zachtka kwa inu bwanji? …..kunena mosabisa boma ili sakutithandiza kwambr kumbar yachtetezo

  5. @ Mr clement sometims umunthu ndiwabwno mwayenda kut inuyo kumene anthu amasekelera anthu akamafa mwachsawawako?? ..kwina kulikose kulakwsa kwa ana m’banja anthu amayang’ana kholo kumene inuyo musamaone zodabwsa anthu tkamaloza chala mtsogoleri coz iye ali ngat kholo lathu ….ndamumva wna akut iwe umafuna azichta kulondera m’makomo mwawo mmmm kulankhula mosakhala bwno kumeneko bwana zitakhala zachtka kwa inu bwanji? …..kunena mosabisa boma ili sakutithandiza kwambr kumbar yachtetezo

 31. tingodikira kaye paja apresident atumiza mkulu wa apolice kunja kwa dziko lino kukaphunzira mmene angagwirire anthu opha anzawo, chifukwa kulibe wanzeru kapena wamapulani othana ndimchitidwe umenewu, nayenso mkulu wapolice wangokhala paudindowu koma nzeru zothana ndi anthu opha anzawo alibe, bola akudya bwino. Awuse mu mtendere Dexter Kanike

  1. Atsogoleri opusa akuti wapita kunja zoona kuzmbia dziko lazambia liphuzitse dziko lamalawi komaso moreover apresdent ake adaphunzitsapo Obama ili siboma

 32. Amalawi nsanje safuna munthu otukuka chomuphera munthu nchiani kulakwatu amene mwapanga zimenezo musayiwale mwasogoza nzanu nanu lanu likubwera siku palibe wamuyaya RIP

 33. It simply means that this government has totally failed in terms of security, each and every minute people (including the albinos) are being killed…

  1. Vuto ndilakuti news mumangowonera za ku malawi zokha dat is wy ur sain dis,other country 10 ppl r dying each and everyday,koma kwathu kuno kungomva mmodzi wafa eee no security.

  2. Well said Willard Joseph . Ndipo mwachepetsa ine ndaona anthu ophedwa dzulo dzuloli a Malawinso anthu ake zapamseu ndiye osanena.kusadziwa zinthu mkona anthu amangoyankhula mmene atafunile. Security

  3. And nex time they wll blame government for not impregnate their wives….its matter of time people are dying every minute around the world.

  4. Heey wena Evance Charlie that’s true chilichonse akuti boma amaphedwa a police komanso alipantchito yoteteza anthu ndikatundu wao . zina zimaonjeza sindine wa DPP koma zina zimaonjeza

Comments are closed.