An angry mob on Monday in Blantyre burnt to death a man for stealing a handbag and two smart phones.
According to information sourced by this publication, the man stole the handbag which contained money amounting to K40,000 from a lady at Chinyonga bus stop.
Further information sourced reveals the suspect was caught after the victim shouted for help from well-wishers.
The mob then agreed to burn the suspect.
Police later came and took the remains of the deceased to Queen Elizabeth Central Hospital (QECH).
The development comes at a time when the country has registered an increase in cases of mob justice.
However, some organizations have spoken tough against mob justice in Malawi arguing that the country has laws which should be respected.
I support it
work hard osafowoka chitukuko pa tsogolo amalawi
work hard osafowoka chitukuko pa tsogolo amalawi
Stupid dont judge !that’s the duty of police officers to arrest them not burn. Kkkk nanga amatero ?
Malawi watayira yani chikondi komanso mtima wachifundo unali mwaiwe uja kuti lero walimba mtima kuvala uchigawenga now umbanda ngati Iwe ungaweruze motere mulengi adzachitanji
Amupanga bwino, kupititsa ku police amafuna adzikudyela iwe odandaula.
Oh Lord no!, we need awareness on this issue of mob justice, yet j
Sighns of the coming of the son of man
Wrong is wrong yes!! But please my neighbors, do not become heartless like south Africans! That’s why we have police around. Life is precious! And economic
Every sinner is a candidate of heaven! Spiritually speaking, you are planting seeds of killing, that may continue, just as what happens right in Sa, ka small issue, they want to shed blood, not right at all, be ccivilized like us Zambians!
amchita bho. Very ndudu!
Tit for Tat
big up guys show dpp police that they are failures
Kikikikikikiki ehee ine mawu ndilibe another Malawi aboma akulephela kugwila ntchito yawo awotcheni basi banii banii ndekuti
Waaaa!! Mnanaziwambo Ine Kut Amalawi Awa Ayamba Zootcha Wa!! Musiyenimbo Munthu Azaweruza Mulungu Basi!! Waaa!!!
that’s rubbish
Kuotcha ndi kuotcha basi palibe chisoni . Bwanji iyeyo sanachite chisoni kuba ? Dziko lililonse akuba alipo koma amalawi mwaonjeza mabedwe mutha ndithu akuotchani .
Well done BT guys
Good
akamaotchedwa choncho sikuzakhala akuba ku nyasaland.
Its necessary to burn those bastads after investigation otherwise muzatentha munthu osalakwa. Nose amene mukuthamangila kunena kt mbava ziotchedwe muzadabwa muli inu akukuotchan mutanamizilidwa, mark my words all foolish comenters!!
Wakuba ndi mfiti…
End of days
End of days
To what level do people sink when you deliberately take the life of another human being? Let the law take its course. Playing judge and juror does not make you a better person by killing someone! What is this world coming to when A human life means so little. Does the lady whose handbag was stolen feel good about what happened to this person? was that handbag money and phone worth the life of another human being? Precious Jesus have mercy!

Malawi wachangamukadi eti apande malawi wafungo,palibeso njira ina yothetsela umbava kuposa imeneyo,big up.
Malawi wachangamukadi eti apande malawi wafungo,palibeso njira ina yothetsela umbava kuposa imeneyo,big up.
Burning is a good deal
Burning is a good deal
Akuba okuba katundu ndi makape concho ndikuganiza kuwaotcha ndi #DEAL# akunyozesa ntcito ya anzawo omwe akaba mmabank.
Akuba okuba katundu ndi makape concho ndikuganiza kuwaotcha ndi #DEAL# akunyozesa ntcito ya anzawo omwe akaba mmabank.
Vuto ndi police yathu 2 much corruption. Ndiamene akuonjezera umbava pa Malawi pano so the best way iz to burn them
APolice nawonso adatopa amangoyang’ana amvekere mwatichepesela ntchito.
Why should the laws be respected only on mob justice? On gay you remain deaf. Silly !!!
KODI MALAWI UKULOWERA KUTI? IZI NZACHILENDO KUPHA NGATI MUNTHU GALU.SHAME
THOU SHALL NOT KILL
Shall not steal either brother.
This is what makes me think religion has thrived and failed. Holy books make it clear that we shouldn’t judge others and mostly, thy shall not kill, so where do we get an authority to do so? We let those real thieves walk free and give maximum punishment to little criminals like these? Shame to humanity

Shame to humanity indeed
That’s not good kod atakhala achimwene ako,ungave bwanji?
That’s not good kod atakhala achimwene ako,ungave bwanji?
Enanu simunabeledwepo zikazakuchitikilani muzaziwa kuti wakuba ndi mfiti munthu osafunikila pakati pa anthu ozifunila.
Enanu simunabeledwepo zikazakuchitikilani muzaziwa kuti wakuba ndi mfiti munthu osafunikila pakati pa anthu ozifunila.
Chabwino sitimapha, nawonso muwauze asamabe
Chabwino sitimapha, nawonso muwauze asamabe
kill those bombocrat
kill those bombocrat
kill those bombocrat
kill those bombocrat
saiz yabwino
saiz yabwino
Koma kupha munthu moofurumira ndi kulakwa nthawi zambiri amaphedwa ndiosalakwa komaso kumalawi kuli malulo kumwanza anthu anapha azigogo aja momvetsa chisoni Malawi tiku nka kut
Koma kupha munthu moofurumira ndi kulakwa nthawi zambiri amaphedwa ndiosalakwa komaso kumalawi kuli malulo kumwanza anthu anapha azigogo aja momvetsa chisoni Malawi tiku nka kut
OUR COUNTRY IS IN AGONY AND EVERYTHING THERE IS AMESS POLITICS MESS , LAWS MESS AND IDONT HAVE TO BOTHER MYSELF THAT IN OUR OUNTRY SO CALLED THE WARM HEART OF AFRICA THERE LAWS ? IDONT THINK SO ! HOW CAN SOMEONE CUT SOMEBODIES HEAD ? WHERE ARE THE POLICE ? WHERE ARE LAWS ??????
Kodi wakubayo nayenso amadziwanso mulungu mukunena chiyani ndi neba wanu amuchita bwino osamagwira ntchito bwanji
Thiefs must die
Guys kodi Malawi akupita kuti? Kodi mwachita kukhalilatu pampando wakuweluza pamene mwini wake ali pa mpando wachisomo? mwapha munthu koma chonsecho pansi pa mtima mukuziwa kuti munabapo, Ooh! God 4give Malawi
Hybo ohk???
Congrats Guys 4 Job Done Mwna Azawo Atha Kutengerap Phunzro
xenophobia,may God punish everyone who had a hand in such a Satanic act to hell with Malawi and its Law enforcement officialls,you will remain outdated you retards
Zandiwopya zomwe zayamba kuchitika guys
Guys mukutenga lamulo kumanjatu
Anyamata aku BT plz pezani zochita anyamata anzanu kuno ku LLs amatakataka kugulitsa madzi ndi kuotcha mbatata amaopa zimenezi,,, nde anu aku BT mumangoziwa kutchena koma mulibe mane nde mumangokhalila kuba basi…
Nice job
Well done akuonjedza anthu amenewa njira yothana nawo ndikugowapha basi!!!!!!!!!
Ndipo aziotchedwa kumene, ansndibela plazima, raptop, 12 grand ndi iphone yanga…….gyz big up zinthu tuzipeza movutikila iwo asamangotola kulibwino azikatolera kumanda
Guys musaphe mwini wake mlungu azaweluza! Bwanji osamuyitanila apolice? Nthawi zina muzapha munthu woti sanabe angomunamizila
Thats best
Big up keep the fire burning malawiii
Big up keep the fire burning malawiii
Kwabwela kwabhoo guyz akuzolowela akuba matown ndibwino kumapznga chomcho
LORD JESUS CHRIST is coming soon,signs of the last days they will be no love,,,,,,
Eish it’s too much
Oweluza nzake nayeso adzaankha mulandu pamaso pamlungu zoona koba nkuphwanyilana ufulu komaso kubwezeletsana pambuyo koma yehova anati iyendiye mwini cilango ifemonga olengedwa ake palibe olungama kuti aweluze ndipo alakwawo ndiambili koma kusaululika chaona nzako capita mawacilikwaiwe moto ulinda kwatsala tchile kulakwa sikubakokha enaso mudzalakalaka mutakhululukilidwa tsikulina
Mulungu sanati wakuba aphedwe koma adati ophanzake nayenso aphedwe sopano pamenepa oyenela kuphedwa ndani?
Weldon it’s only the way to pansh the thugs.
Mitima ya Kaini pano padzikolapansi ndiye yachuluka tsopano anthu ayamba kuwona kuchedwa chiweluzo cha kwa Mulungu .
Otelowo aphedwe basi, Kut ena atengelepo phuzilo, Chifukwa ndende zinadzadza komaso boma lilibe ndalama zokwanila kudyetsa akaidi, Ndie akamangidwa 3dayz watuluka, Koma akagwidwa aziphedwa pompo! !!!
Nde yake imeneyo man! Aphedwe basi!
Ndakunvan man
Ndakunvan man
Anthu ngati akufuna kuba they must try and steal at the Reserve Bank rather than stealing women’s handbags.Look now the results
Azibusidwa mwina azileka.anthu amenewa alibe chisoni akakupanikiza.
aķufuna video
Big up guyz! Amene akudana ndizomwe zachitikazo nayenso ndimbanva akuopa kuti next time adzaotchedwe ndiyeyo…MUKAPEZA MBAVA IKONG’ONTHENI
Amene wapha munthuyo pomuotcha moto yo ndimene ali oyenera kuphedwa,fufukwa padziko lonse lapansi lino palibe anthu amene angagwirizane kuti munthu akaba aziphedwa ayi,koma ngati wakubayo ngati waba ndi kupha komwe pamenepo akaphedwa wakubayo ndizomveka,komanso kuphako kuzigwirizana ndimalamulo
Azakubere Iweyo Unganene Zimenezo? Calculate Hw U Toil To Find It 4 Its Best & Important Use Ndiye Wina Akatenge 4 Free Claiming He Z Clever?
No comment
Fire Burning no problem akuphwanyisa thupi akubawa next ndiweo mathanyula
#RIP.
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS
Good news
Mphoto latchimo ndi IMFA akapedzeka aphedwe basi
Mmmmmm Malawi is doomed
Ngati mukufuna akuba aziphedwa, yambani mwaotcha the cashgate crew!
Nice 1.Ngakhale Bible limati,’mphotho yauchimo ndi imfa’. omwe akuti sizabwino naonso ndi mbava.
Odula ziwalo ndi oyenera kuwawamba.
Bola odula ziwalo zawathu, osati oba phone.
chilango chili pasi mpopano.
Kuweruza ndi kwa mulungu
Madness
Guys handbag ndi phone mpaka apa….let God be the judge.
Wakuba naye ndi wakuphatu kuteroko akumana akupha okhaokha ma 4ni ndi handbag sanangotola ayi anavutikila kmaso ndalama zokwana 40000 sanatore ankhetsa thukuta
Good judgment just clean up all of them without mercy,fear and fever keep it up fanz
yah keep it up ma angry# mobbers akutionjeza amenewa kwambiri# akuzolowera mwawachita bwino akapita kupolisi akumakalipirako ndalama then #akumabweranso kuzabera anthu mtawunmu #kumangowotcha basi
chisilu chili ndi mwini…give e’m a hard punishment and not burning them..and also pray for those kinds of people
chisilu chili ndi mwing…give e’m a punishment and not burning them..and also pray for those kinds of people
Burn them
Burn them
ellen can u tel m funso loyamba limene amakufunsa ukakumana nawo?
ellen can u tel m funso loyamba limene amakufunsa ukakumana nawo?
Wapata sure
Mmmmmmmm shame
Wapata sure
Kulakwaaaaaaaaaaaa
RIP through bad decisions he has made
Kkkkkk well done I have plenty tires to donate for this cause
nchito za manja awo zawacitira umboni kuotcha basi
Zosezi vuto ndi boma lathu lilibe mphavu koma kunalibeko idzi zongoba chisawawazi kmaso kuphana chochizi, late bingu boma lake munalibe police yogona ngati iyi,
Ndazizidwa Guyz! Ndakumbuka Pa Jon Nthawi Ya Zeno. Osatengera Lamulo Mmanja!
Kulowelela Kwakuba Ndi Ifa Basi Waku Ayenela Kusitha Yekha Akapitiliza Akumana Nazo Kuba Ndi Dpp Kapena Kuti Chipani Ndikosiyana
Koma aku south africa simbava ayi
Good job
Job well done
Yaa mwachitabwino onse akuba aziotchedwa, mphotho yake imeneyo
A malawi,musafike pa moyo wa nyama. Kodi sitimadandaula a malawi anzathu akuphedwa ku South africa? Poti mwampha munthu chifukwa cha hand bag ndi. ma phone,nanga akanakubelani galimoto mukanamutani? Mukazadzindikira kuti kuli mulungu madzasiya.
Ukuoneka kt sunabeledwepo ndichifukwa ukulankhula zimenezi zaziii zakozo zankutu
Sanaberedwedi ameneyu… Sakudziwa mmene zimapwetekera munthu kukubera… Munthu u work hard on sumthn… Wina sanakhetsereko thukuta. Basi nkungochoka kwawoko nkumubera nzake… Adziphedwa kumene akubawa
nyc
Ili Ndi Dziko Muzakumana Nazo Ndipo Uzaleka Kulankhula Zopepelazo.
Munthu wakubatu nayeso ndi wakupha amakutcholera chitseko iwe uli mommo ndikukupha ndikukutengera katundu ndiye kumawasekerela anthu oterewo?
Amakugwililiranso NKukupatsa Matenda
Sunabeledweko ndedzinena nyonyonyoo wakokoyo
Komatu iwe, ndani anakunamiza kuti anthu/amalawi waphedwa ku south africa chifukwa chakuba, awotcheni ndithu anthu oyipawa n nwayeso wakuba ndi wakupha
I WAS ONE OF THE PPLE OMVA CHISONI NDIZIMENEZI AND KUMAPANGA CONDERM, KOMA ZINANDIONEKELA, I’VE NO KIND WORDS FOR AKUBA ONSE- THEY CAUSED EMOTIONAL SUFFERING TO MY RELATIVES AND TO ME AS WELL- WILL NEVER FORGET!!! WAKUBA IS A KILLER
PEMPHELO,ambuye mutitumidzile akuba atatu akafike kunyumba kwa Makumba kuti akawadziwe zintchito zawo,asakasiyile pompo koma kumuchotsa chimbenene,amen!!!
Kuno ku South Africa timaphedwa chifukwa cha njiru za anthu aulesi a kuno not kuba. Achita bwino kuwaotcha anthuo. Anthu timavutika kuti tipeze katundu, wina azizaba, ali iweyo akubela ungamve bwanji?
Kkkkkk, Anthony Kacheche kkk, pemphero loti mpaka ambuye kusekatu kkk
Aixe Makumba,okuba amaphweka akagwidwa,,,Udzakumana naye live nde uzamugwire wekha mkuzaposita nyansi zakozi…if he dies thats gud koz even Bible says award of sin is death.They always deserve it(death)
Kkkkkk kkkkkk mpakana pansi thiiii,gadaaaa @ veronica
Wakolola zomwe adazala.
Well done that’s the best way of dealing with thieves
Tiotche zimenezi..
Atawotchedwa brother wathu tingamve bwanji?
Capital punishment siyabwino. Boma lichitepo kanthu.
KUKHALA NDI CHOMCHO
Ndakunyadilani nonse anyamata pantchito yotamandikayi mawa muzachitileso ena.
Why u use apunishment of god
Why , no reported police?
Uuuummm guys it’s not gud, bwanji mukungowotcha anthu, osamuyitanila a polisi bwanji,,,, those things should stop Malawi.
It’s Obviously this people they take the law into there own hands.which is not gud at all…instead to call da cops…shame
Frank I really dnt understand malawians, munthu kuba poto kapena nkhuku kumuwotcha kumupha
Amenene amapanga zimenezo they r so stupid people..pomwe akuba ma million aja they jst walk free..Koma Iwe nkhuku mpaka kukuwotcha Mmmm my malawi lets wake up
munthu wakuba ndi woopsa kwambiri and people are burning this ppo bcoz akapita ku police akatulukako……mukazakumana Nazo simuzaganizaso kawiri
@Chris i understand u but is only punishment is to kill? there’s no other way that u can deal with??ofcourse yes ndizopwwteka koma to kill is not a best solution…hw can u feel mphwako kuphedwa coz of waba wat u call a smart phone n a bag?
#frank munthu okuba ndimunthu oophsya kupanga kusamala akhoza kukupha,,,, okuba amabwelera zinthu ziwiri atha kukupha or kukubela,,, pofuna kuzipulumutsa dats y amupha,,,kubeledwa ndikowawa udzaziona ukadzakumana ndi okuba

or ali bale wanga sizingandiwawe,,,,phwangayo ndizisangalala akupanga chipongwe anthu ena? ndizintchito zake
or ali bale wanga sizingandiwawe,,,,phwangayo ndizisangalala akupanga chipongwe anthu ena? ndizintchito zake
anthu onsewa akugwira ntchitowa ndi zitsiru? ndi ndani samafuna za ulele???? zinthu zimavuta kupeza man,,, kubeledwa ndikowawa
anthu onsewa akugwira ntchitowa ndi zitsiru? ndi ndani samafuna za ulele???? zinthu zimavuta kupeza man,,, kubeledwa ndikowawa
Makosana tikamalemba macomment wa tiziganizira kuti amene akuwotchedwawa atakhala bambo athu, azichimwene athu, mwachidule azibale athu tingachilandire bwanji??? kumakhala ndi umunthu, moyo wamunthu tisawupeputse chonchi

Malawi 3-0Guinea
Malawi 3-0Guinea
Too bad
Too bad
Zochita kufuna
Zochita kufuna
koma muti mob justice aaaa guys musiyeni mwini moyo akatiweruze yekha
koma muti mob justice aaaa guys musiyeni mwini moyo akatiweruze yekha
Bomaaa ilooo!
Bomaaa ilooo!
After burnig them, you should also EAT them if your conducts to be in line with otherwise judgement belongs to the CREATOR.
Akuti maguy amaotchawa ndi aBeutfy Malawi Trust,Keepin the city clean,mudziotcha zinyalala osati anthu.
Akuti maguy amaotchawa ndi aBeutfy Malawi Trust,Keepin the city clean,mudziotcha zinyalala osati anthu.
Yet if he is caught, he must pay sevenfold, though it costs him all the wealth of his house.Prov6:31..But justice belongs to Yahweh
Yet if he is caught, he must pay sevenfold, though it costs him all the wealth of his house.Prov6:31..But justice belongs to Yahweh
Heeeeeee! Where z Malawi going to? Burning this! Burning that! Burning! Burning!…what z this Malawi?
Heeeeeee! Where z Malawi going to? Burning this! Burning that! Burning! Burning!…what z this Malawi?
While we are strongly saying no to mob justice,and also acknowledge that our country has laws,the question has to be how are the laws applied. This is asign that people are not happy how these laws are enforced,give them hard punishment if caught.
Mob justice is part of african hatred
Mob justice is part of african hatred
chigamulo chabwino ndikudula dzanja lamanzele, akadzabaso dzanja lamanja, akadzabaso mwendo wamanzele kenako wamanja akadzabaso ndiwosanva nkhululukileni.
chigamulo chabwino ndikudula dzanja lamanzele, akadzabaso dzanja lamanja, akadzabaso mwendo wamanzele kenako wamanja akadzabaso ndiwosanva nkhululukileni.
enawo musibwelesa kuno ndisipangila kanyenya my 0999765498
enawo musibwelesa kuno ndisipangila kanyenya my 0999765498
Malawi mmmmm mwaonjeza why why killing
Malawi mmmmm mwaonjeza why why killing
Amuchita bwino
This is unfair punishment! The life of human being is very expensive than anything.lets try other ways. Ungoganiza utakhala iweyo kapena m’bale wanu munakamva bwaaaaanji? Imeneyo si deal.
This is unfair punishment! The life of human being is very expensive than anything.lets try other ways. Ungoganiza utakhala iweyo kapena m’bale wanu munakamva bwaaaaanji? Imeneyo si deal.
t really hurts m’bale wako akamenyedwa olo ali ozunguza, nde wina amuotche eeh nt gud..
t really hurts m’bale wako akamenyedwa olo ali ozunguza, nde wina amuotche eeh nt gud..
ha ha ha kodi inuyo mwavutikila kugula katundu ndiye wina azangokulandani basi????? akuba ndi anthu oopsa kwambiri mukazamuna Nazo muzasiya zanu mukunenazi
Koma #chris sukudziwa mmene moto umawawira chifukwa umadya za mu frige zokhazokha eti?
Wages of de sin is death….
Wages of de sin is death….
CHOT TZIWE NDCHAKUTI, ‘ALIYENSE AZALANGIDWA MONGA MWA NTCHITO ZAKE’ YESU AKUBWERA2 OHO
Nkhani zomaotcha munthu akagwidwa ataba zafika posauzana, but in my opinion thats not good to do so, lets remember that our country has got laws accordingly to every matter, olakwitsitsa siwakuba yekha ayi koma almost tonse, tinangowona kusiyana zochitika zathu, ena achwelewele, andewu, ufiti, and the like…. Mulungu anamusintha Sauli kukhala Paulo, and yet we call Malaw God fearing country…Is it true?
Tikuotchani nonse kaya ndikukumana tikakumane ku hell komweko…..ariiiiii unaberedwako iwe kapena yako ndiyotsolora yomweyi???
Think twice
Ndakuntadirani anyamata nonse amene mwagwira ntchito yotamandikayi pitirizani ndithu. #mumatiyimirira
Very good muzachitileso wina zimenezi akagwidwa
kaya waba kanthu kakang’ono kaya kakakulu iphani basi chifukwa tchimo ndi tchimo basi.
2bad but wages of sin is what?
Ntchito zamanja zamuchitira umboni.
Zikutheka basi wakuba aliyense azatengelapo phunziro iyaa!
Yes ndiye kuti ameneyo sadzaberanso wina osawasiya
Vuto ndi ya police anthuwa akaba kupitanawo kupolice mawa ukakumana naye akudya chap pachiwaya amutulutsa mmalo moti akalandile chigamulo moti apa nkhani ikhala imeneyi akapezeka kutentha basi kkkk
every person has a right to bail and fair trial. People who are rich but hve committed serious offences are out on court bail .People dont talk but when a poor thief steals a laptop nd handbag he is being killed and u blame the police for that .Life is so precious my dear. Learn to forgive others when they commit minor offences.
Please leave judgement in the hands of God.
ha ha iweyo akazakubela then leav judgement to God wamva iwe
Kuleka kupeza chochita basi azibela anthu nde tizingosekelela zimenezo Aotchedwe Basi (y) (y) (y) (y) Mi lyk it 125%
The only way to end umbava nkumawaotcha choncho basi
Kkkkkkkkk
Ur nxt
Its two robbers not one
Mphoto ya uchimo ndi imfa….amenewo ntchito za manja awo zawachitira umboni…& enytym mr president akhala akulengeza kuti shoot to kill ya bwelera.
njila yoyenela kulangila wakuba akagwidwa ndikudula manja osoti kuotcha
Wakumoto Malawi Basi Zosekelera Zimenezi
Ma pupa mamaitha aotchedwe okubawo nteleshede wavuta n akaba samakai user koma kungo imwera vadi aotchedwe basi ndipanga supply ma tire ndi petro mmadela mwanumo big up gyz
Alakwisa Kumupha, Akanangomudula Malisechewa Kk
Ndikokubwera kumeneko 4odays inakwana kkkkkkkkk
Malawi where is that from is murder regalised in malawi ? Why you spared cash gaters life ? RIP!!!!!!!!!hhhhh
guyz am proud of them, that’s agud job let’s burn them untill hashes.
when people were cerebrating kuuka kwa Jesu ndipamene wina akusiya Moyo wake so sad
clean malawi… beautify blantyre
GOOD..!!!
Good iam proud of our security in Malawi. Keep it up
Which security?taking a life which z irreplaceable becoz of a handbag that can be replaced really?
kodi Acash get adakasungidwabe kuootcha amenewo bwanji ndi uwyo amene akumaopseza anthu kuti awaphayo . mtsogoleri omachita kuyerekedwa mkupha
burning em looks to be a harsh punishment to em, but e feeling these guys left you akakubela it sucks big time am e leaving witness i knw how it feels, kuwaotcha si deal koma mwina kungowathyola miyendo
Kuwathyola miyendo kutha kupangisa kuti dziko lathu likhale ndi opunduka ambiri
Kuwathyola miyendo kutha kupangisa kuti dziko lathu likhale ndi opunduka ambiri
Well done Guys keep it up to clean them once they found! Inu amene muti alakwitsa ndiye kuti simudabeledweko zimawawa man inu mwavutikira wina ango utenga osakhetsa thukuta?
What if atakhala mphwako or 1 of yo family member wawotchedwa or wafa ifa yotele hw can u feel??? even boma limati we musnt take the law into our hands..shame
Ameneyo ndimalipiro ake Big! Inewo ndaberedwako that’s why Iknw how painfull it is once Uget robbed. Ndipo anthu akuba alibe chifundo ayi amatha ukupha plus kukubera even wrist watch or ring ngati asowa chokulanda.
@ frank atakhala m ‘phwako umudandaula chifukwa choti ndi m’bale wako kma pasi pantima ukudziwa kt walandila malipilo ake ana oterewa nthawi zina amakhala osanva makolo kuwalangiza osanva
Ndiye the only punishment is to kill?palibe njira ina apart 4rm kupha??
Amuchita bwino…..inu mukutsutsanu simunakumane nazo serious. wakuba amachotsa moyo kapena kukusiyila chilema ngati ukuteteza chinthu chako
Amuchita bwino ameneyo. Aphedwe basi! Munthu wakuba ndioopsa kwambiri
ndipo amuchita bwino Kwambiri
@ frank uzakumane nazo kaye ndiye uzizalankhula mau amenewo
I’ve been stolen from a number of times and i never felt the need to kill the person. How can you think 2 smartphones and a handbag are equal to a human life?
@ Lonjezo me too I’ve passed the same situation for almost 4tyms! In 2003 they broke in my Aunt’s house they nearly kill all of us Iwas there for holiday in erea 36 LLS. Then 2006 Ilost one of my best frnd they killed him cos of TV plus aradio. In 2013 they robbed me R27thousands plus my laptop, computer and they tied me point me agun and leave me on abear tiles untill morning. This year on 9th January they hijacked acar plus took my tablet my Iphone and R6thousand ontop of that they stapped me at 7times Iwas hospitalised for aweek. So what U say my frnd?

Tamusiye amene sakuziwa ,,,,,asakutopese & ds one kumaliro kwake amalira ndi agogo ake enawo mmmmmmmm ayika lero op chinali chizolowezi chake
Tamusiye amene sakuziwa ,,,,,asakutopese & ds one kumaliro kwake amalira ndi agogo ake enawo mmmmmmmm ayika lero op chinali chizolowezi chake
Mceddie Square sorry for your badluck and losing a friend but is that a sufficient reason to take a human life?
Mceddie Square sorry for your badluck and losing a friend but is that a sufficient reason to take a human life?
The prblm is Ucan feel sorry fr them. But them not at all to feel sorry for U cos most of them they used drugs serious my frnd and ihate those thugs alot!
The prblm is Ucan feel sorry fr them. But them not at all to feel sorry for U cos most of them they used drugs serious my frnd and ihate those thugs alot!
Guyz wel done may god bless u all thieves its lyk snake once found kill them stupid devils Amen
Guyz wel done may god bless u all thieves its lyk snake once found kill them stupid devils Amen
Palibe Frank, thats the best solution he deserved it. Iye samadziwa kuti kuba ndi kupha nchimodzimodzi
Lonjezo r u one of them?
wasn’t there any other punishment?
mmmh malawi wafika pena uyu…..
keep it up malawi mwina okuba angachepe malawi ndidziko latendere
Kma Ku Malawi nkhani zootchana zafikapo bwanji kuba shoez awotchedwe bax r.i.p
kkkkkk koma anthu ena…..r.i.p okubawo ha ha ha they won’t have peace I tell u
Eishhhhhh dats very sad Malawi evryda bad newz!!!!
I blame DPP government for all problems in Malawi
mmmh mwangoida dpp.mavuto anayamba kakekale awa b4 dpp…jst go read ur Bible ull get ryt ansz
mmmh mwangoida dpp.mavuto anayamba kakekale awa b4 dpp…jst go read ur Bible ull get ryt ansz
generalization fallacy.
generalization fallacy.
kkkkkkkkkkkl koma A DPP zikuwakhuza cha??? hahahahahaha Malawians they alway blame on the government Smh
Tili mmasiku otsiriza zimene baibulo linalosera zili kukwaniritsidwa 2 Timoteo 3:1-5
Mmmmm uwu ndiye ubulutu zootcha wakuba zinyamba lero ? Kumangoziotsera ubulutu pa ntetete kkkk
DPP woyeeeeeeee
DPP woyeeeeeeee
The judgment will come to u
Cifukwa chakulimba mitima yanu, iphani munthu amene naye wapha munthu, failing whc killing someone just becoz wapezeka ataba simple iterms like those its inhuman..
mphoto yauchimo ndi imfa watsoka yemwe akuothedwa pasipano nd kuzaothedwaso ambuye akabwera
Zamuchitila umboni zintchito zake
akapita ku police amabwerako agalu amenewa… mwina ena mkumaopako khalidwe loipali
kkk mwalowa chiwewe et zlizonse kumangootchana!? ndekut akunsanje aja anasegulila et
i was ther malo amenewo pamapezeka achifwamba
Mwasala ena inuuu
That’s very bad killing someone just bcoz of a hand bag & phones no no no!!
its not very bad why there not find anything to do than to be skoli achita bwino malawi ndi dziko latendere
But the power to judge is not in their hands life is the most expensive thing u can’t afford to biy
yaa its true but chilango chilipasi pno
Ngati uli m’modzi mwa iwo samala m’bale tikuthira paraffin
Aziwochedwa basi koma tsoka kwa iye okwanilitsa malemba
RIP
nkhani yosangalasa
Is that a punishment? A life compared to a handbag/Smartphones(2). mmmmh a Malawi mwalowa chiwewe basi.
its not jst a hand bag.. munthu wakuba ndi munthu oipa amabwera mzambiri more over kutchingira panjira..he could kill her or rape her….achita bwino kumuotcha munthu oipa
sunakumane nazo zimene amachita anthu amenewa panseu
No that’s not the way to teach them a lesson, they’re so many ways than killing them in that way.
Zoopsa izi.But I can’t recommend such Justice tho. Why do we have police? Enanu here u r the next on the line.Anthu azakusokonezani ndi munthu wakuba muzalandila zilango zowawitsa ngati izi f u r not careful.Be simple,smart and conscious.
uzaziwona.
When thief is caught you always complaining bt akatibera u keep quiet y?
sanakumanenawo ameneo
sanakumanenawo ameneo
Thieves deserve very painful punishments according to humility inline with our laws! Some people are usually tempted to steal, a punishments teaches a lesson!! Nzotheka anthu amasintha. Inu simuganiza kodi? kuti nchifukwa ninji boma silidaike lamulo loti “Okuba aphedwe”…. Kupha si yankho lothana ndi mbava!

I agree with you wongani some people the jst born opanda chisoni coz moyo wamunthu u cant compare ndi handbag hmmm thus bad why killing .handband phone zinthu zoti ukhoza kugulaso
I agree with you wongani some people the jst born opanda chisoni coz moyo wamunthu u cant compare ndi handbag hmmm thus bad why killing .handband phone zinthu zoti ukhoza kugulaso
tamakambamkoni zomveka…u said some1 can buy a hand bag n a foni yesss ..so y these pepo ddnt think of buying their own handbags n fones instead of taking some1 elso,??? mutha nose azasowa ubakira mzake
Muthu kupha muthu zake kwa mulungu wanga ndi zoresedwa, malawi wazaza ndi ziwanda relo, police tchito yao ndi chani,
Sunakumane nazo apolice ngati akulephera ntchito kumpititsa lero mawa watuluka munthu wakubatu nayeso ndiwakupha atha kuchotsa moyo wako
Kupha munthu mzako chifukwa choti wachimwa poti wakubera ndi tchimo lalikulu. kodi ndani amene sana chimwepo? Ntchito yoweruza si yathu. timusiyile yehova mulungu ntchito imeneyi yoweruza ochimwa. let us repent please.!!!
Chomwe akulakwa ndichoti akupha, mmalo mopita naye ku police!
Ku police ko akapita mawa akubwerako akukabaso ndiye tizitani nawo anthu amenewa ? Kugula katundutu ndikopweteka mwanva inu
Simunabeledwepo muzamva kuwawa.
Simunabeledwepo muzamva kuwawa.
Munagweredwepo zovuta kamba koti m’bale wanu waphedwa. Muzaziona, moyo wa munthu si za phada! #solution_is_punishment!!

Aphedwe basi tatopa nawo akubawo zikamatero aziwopa agalu awa
Aphedwe basi tatopa nawo akubawo zikamatero aziwopa agalu awa
Akadzabela iweyo u wl nvr say that my friend
Yes ilyk to hear good story lyk thiskkkkkkkkkk
amuchita bwini.dead and gone forever ameneyo
Oo yes zofunikila,amuchita bwino ameneyu
wokuba apse ndithu
Waituluka bwino Easter ameneyo,Yesu anafera pa mtanda,uyu wasankha Moto…
Eya wafera pamoto akukafiraso pamoto ali bho azathu