Angry mob burns man in Blantyre

Advertisement
Blantyre Mob Justice
Blantyre Mob Justice
Torched.

An angry mob on Monday in Blantyre burnt to death a man for stealing a handbag and two smart phones.

According to information sourced by this publication, the man stole the handbag which contained money amounting to K40,000 from a lady at Chinyonga bus stop.

Further information sourced reveals the suspect was caught after the victim shouted for help from well-wishers.

The mob then agreed to burn the suspect.

Police later came and took the remains of the deceased to Queen Elizabeth Central Hospital (QECH).

The development comes at a time when the country has registered an increase in cases of mob justice.
However, some organizations have spoken tough against mob justice in Malawi arguing that the country has laws which should be respected.

Advertisement

326 Comments

 1. Malawi watayira yani chikondi komanso mtima wachifundo unali mwaiwe uja kuti lero walimba mtima kuvala uchigawenga now umbanda ngati Iwe ungaweruze motere mulengi adzachitanji

 2. Wrong is wrong yes!! But please my neighbors, do not become heartless like south Africans! That’s why we have police around. Life is precious! And economic
  Every sinner is a candidate of heaven! Spiritually speaking, you are planting seeds of killing, that may continue, just as what happens right in Sa, ka small issue, they want to shed blood, not right at all, be ccivilized like us Zambians!

 3. Waaaa!! Mnanaziwambo Ine Kut Amalawi Awa Ayamba Zootcha Wa!! Musiyenimbo Munthu Azaweruza Mulungu Basi!! Waaa!!!

 4. Kuotcha ndi kuotcha basi palibe chisoni . Bwanji iyeyo sanachite chisoni kuba ? Dziko lililonse akuba alipo koma amalawi mwaonjeza mabedwe mutha ndithu akuotchani .

 5. Its necessary to burn those bastads after investigation otherwise muzatentha munthu osalakwa. Nose amene mukuthamangila kunena kt mbava ziotchedwe muzadabwa muli inu akukuotchan mutanamizilidwa, mark my words all foolish comenters!!

 6. To what level do people sink when you deliberately take the life of another human being? Let the law take its course. Playing judge and juror does not make you a better person by killing someone! What is this world coming to when A human life means so little. Does the lady whose handbag was stolen feel good about what happened to this person? was that handbag money and phone worth the life of another human being? Precious Jesus have mercy!

 7. To what level do people sink when you deliberately take the life of another human being? Let the law take its course. Playing judge and juror does not make you a better person by killing someone! What is this world coming to when A human life means so little. Does the lady whose handbag was stolen feel good about what happened to this person? was that handbag money and phone worth the life of another human being? Precious Jesus have mercy!

 8. Vuto ndi police yathu 2 much corruption. Ndiamene akuonjezera umbava pa Malawi pano so the best way iz to burn them

 9. Why should the laws be respected only on mob justice? On gay you remain deaf. Silly !!!

 10. This is what makes me think religion has thrived and failed. Holy books make it clear that we shouldn’t judge others and mostly, thy shall not kill, so where do we get an authority to do so? We let those real thieves walk free and give maximum punishment to little criminals like these? Shame to humanity

 11. This is what makes me think religion has thrived and failed. Holy books make it clear that we shouldn’t judge others and mostly, thy shall not kill, so where do we get an authority to do so? We let those real thieves walk free and give maximum punishment to little criminals like these? Shame to humanity

 12. Koma kupha munthu moofurumira ndi kulakwa nthawi zambiri amaphedwa ndiosalakwa komaso kumalawi kuli malulo kumwanza anthu anapha azigogo aja momvetsa chisoni Malawi tiku nka kut

 13. Koma kupha munthu moofurumira ndi kulakwa nthawi zambiri amaphedwa ndiosalakwa komaso kumalawi kuli malulo kumwanza anthu anapha azigogo aja momvetsa chisoni Malawi tiku nka kut

 14. OUR COUNTRY IS IN AGONY AND EVERYTHING THERE IS AMESS POLITICS MESS , LAWS MESS AND IDONT HAVE TO BOTHER MYSELF THAT IN OUR OUNTRY SO CALLED THE WARM HEART OF AFRICA THERE LAWS ? IDONT THINK SO ! HOW CAN SOMEONE CUT SOMEBODIES HEAD ? WHERE ARE THE POLICE ? WHERE ARE LAWS ??????

 15. Guys kodi Malawi akupita kuti? Kodi mwachita kukhalilatu pampando wakuweluza pamene mwini wake ali pa mpando wachisomo? mwapha munthu koma chonsecho pansi pa mtima mukuziwa kuti munabapo, Ooh! God 4give Malawi

 16. xenophobia,may God punish everyone who had a hand in such a Satanic act to hell with Malawi and its Law enforcement officialls,you will remain outdated you retards

 17. Anyamata aku BT plz pezani zochita anyamata anzanu kuno ku LLs amatakataka kugulitsa madzi ndi kuotcha mbatata amaopa zimenezi,,, nde anu aku BT mumangoziwa kutchena koma mulibe mane nde mumangokhalila kuba basi…

 18. Ndipo aziotchedwa kumene, ansndibela plazima, raptop, 12 grand ndi iphone yanga…….gyz big up zinthu tuzipeza movutikila iwo asamangotola kulibwino azikatolera kumanda

 19. Oweluza nzake nayeso adzaankha mulandu pamaso pamlungu zoona koba nkuphwanyilana ufulu komaso kubwezeletsana pambuyo koma yehova anati iyendiye mwini cilango ifemonga olengedwa ake palibe olungama kuti aweluze ndipo alakwawo ndiambili koma kusaululika chaona nzako capita mawacilikwaiwe moto ulinda kwatsala tchile kulakwa sikubakokha enaso mudzalakalaka mutakhululukilidwa tsikulina

 20. Mitima ya Kaini pano padzikolapansi ndiye yachuluka tsopano anthu ayamba kuwona kuchedwa chiweluzo cha kwa Mulungu .

 21. Otelowo aphedwe basi, Kut ena atengelepo phuzilo, Chifukwa ndende zinadzadza komaso boma lilibe ndalama zokwanila kudyetsa akaidi, Ndie akamangidwa 3dayz watuluka, Koma akagwidwa aziphedwa pompo! !!!

 22. Anthu ngati akufuna kuba they must try and steal at the Reserve Bank rather than stealing women’s handbags.Look now the results

 23. Big up guyz! Amene akudana ndizomwe zachitikazo nayenso ndimbanva akuopa kuti next time adzaotchedwe ndiyeyo…MUKAPEZA MBAVA IKONG’ONTHENI

 24. Amene wapha munthuyo pomuotcha moto yo ndimene ali oyenera kuphedwa,fufukwa padziko lonse lapansi lino palibe anthu amene angagwirizane kuti munthu akaba aziphedwa ayi,koma ngati wakubayo ngati waba ndi kupha komwe pamenepo akaphedwa wakubayo ndizomveka,komanso kuphako kuzigwirizana ndimalamulo

  1. Azakubere Iweyo Unganene Zimenezo? Calculate Hw U Toil To Find It 4 Its Best & Important Use Ndiye Wina Akatenge 4 Free Claiming He Z Clever?

 25. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS

 26. Wakuba naye ndi wakuphatu kuteroko akumana akupha okhaokha ma 4ni ndi handbag sanangotola ayi anavutikila kmaso ndalama zokwana 40000 sanatore ankhetsa thukuta

 27. yah keep it up ma angry# mobbers akutionjeza amenewa kwambiri# akuzolowera mwawachita bwino akapita kupolisi akumakalipirako ndalama then #akumabweranso kuzabera anthu mtawunmu #kumangowotcha basi

 28. chisilu chili ndi mwini…give e’m a hard punishment and not burning them..and also pray for those kinds of people

 29. chisilu chili ndi mwing…give e’m a punishment and not burning them..and also pray for those kinds of people

 30. Zosezi vuto ndi boma lathu lilibe mphavu koma kunalibeko idzi zongoba chisawawazi kmaso kuphana chochizi, late bingu boma lake munalibe police yogona ngati iyi,

 31. Kulowelela Kwakuba Ndi Ifa Basi Waku Ayenela Kusitha Yekha Akapitiliza Akumana Nazo Kuba Ndi Dpp Kapena Kuti Chipani Ndikosiyana

 32. A malawi,musafike pa moyo wa nyama. Kodi sitimadandaula a malawi anzathu akuphedwa ku South africa? Poti mwampha munthu chifukwa cha hand bag ndi. ma phone,nanga akanakubelani galimoto mukanamutani? Mukazadzindikira kuti kuli mulungu madzasiya.

  1. Sanaberedwedi ameneyu… Sakudziwa mmene zimapwetekera munthu kukubera… Munthu u work hard on sumthn… Wina sanakhetsereko thukuta. Basi nkungochoka kwawoko nkumubera nzake… Adziphedwa kumene akubawa

  2. Munthu wakubatu nayeso ndi wakupha amakutcholera chitseko iwe uli mommo ndikukupha ndikukutengera katundu ndiye kumawasekerela anthu oterewo?

  3. Komatu iwe, ndani anakunamiza kuti anthu/amalawi waphedwa ku south africa chifukwa chakuba, awotcheni ndithu anthu oyipawa n nwayeso wakuba ndi wakupha

  4. I WAS ONE OF THE PPLE OMVA CHISONI NDIZIMENEZI AND KUMAPANGA CONDERM, KOMA ZINANDIONEKELA, I’VE NO KIND WORDS FOR AKUBA ONSE- THEY CAUSED EMOTIONAL SUFFERING TO MY RELATIVES AND TO ME AS WELL- WILL NEVER FORGET!!! WAKUBA IS A KILLER

  5. PEMPHELO,ambuye mutitumidzile akuba atatu akafike kunyumba kwa Makumba kuti akawadziwe zintchito zawo,asakasiyile pompo koma kumuchotsa chimbenene,amen!!!

  6. Kuno ku South Africa timaphedwa chifukwa cha njiru za anthu aulesi a kuno not kuba. Achita bwino kuwaotcha anthuo. Anthu timavutika kuti tipeze katundu, wina azizaba, ali iweyo akubela ungamve bwanji?

  7. Aixe Makumba,okuba amaphweka akagwidwa,,,Udzakumana naye live nde uzamugwire wekha mkuzaposita nyansi zakozi…if he dies thats gud koz even Bible says award of sin is death.They always deserve it(death)

 33. Uuuummm guys it’s not gud, bwanji mukungowotcha anthu, osamuyitanila a polisi bwanji,,,, those things should stop Malawi.

  1. It’s Obviously this people they take the law into there own hands.which is not gud at all…instead to call da cops…shame

  2. Amenene amapanga zimenezo they r so stupid people..pomwe akuba ma million aja they jst walk free..Koma Iwe nkhuku mpaka kukuwotcha Mmmm my malawi lets wake up

  3. munthu wakuba ndi woopsa kwambiri and people are burning this ppo bcoz akapita ku police akatulukako……mukazakumana Nazo simuzaganizaso kawiri

  4. @Chris i understand u but is only punishment is to kill? there’s no other way that u can deal with??ofcourse yes ndizopwwteka koma to kill is not a best solution…hw can u feel mphwako kuphedwa coz of waba wat u call a smart phone n a bag?

  5. #frank munthu okuba ndimunthu oophsya kupanga kusamala akhoza kukupha,,,, okuba amabwelera zinthu ziwiri atha kukupha or kukubela,,, pofuna kuzipulumutsa dats y amupha,,,kubeledwa ndikowawa udzaziona ukadzakumana ndi okuba

  6. #frank munthu okuba ndimunthu oophsya kupanga kusamala akhoza kukupha,,,, okuba amabwelera zinthu ziwiri atha kukupha or kukubela,,, pofuna kuzipulumutsa dats y amupha,,,kubeledwa ndikowawa udzaziona ukadzakumana ndi okuba

 34. Makosana tikamalemba macomment wa tiziganizira kuti amene akuwotchedwawa atakhala bambo athu, azichimwene athu, mwachidule azibale athu tingachilandire bwanji??? kumakhala ndi umunthu, moyo wamunthu tisawupeputse chonchi

 35. Makosana tikamalemba macomment wa tiziganizira kuti amene akuwotchedwawa atakhala bambo athu, azichimwene athu, mwachidule azibale athu tingachilandire bwanji??? kumakhala ndi umunthu, moyo wamunthu tisawupeputse chonchi

 36. After burnig them, you should also EAT them if your conducts to be in line with otherwise judgement belongs to the CREATOR.

 37. While we are strongly saying no to mob justice,and also acknowledge that our country has laws,the question has to be how are the laws applied. This is asign that people are not happy how these laws are enforced,give them hard punishment if caught.

 38. chigamulo chabwino ndikudula dzanja lamanzele, akadzabaso dzanja lamanja, akadzabaso mwendo wamanzele kenako wamanja akadzabaso ndiwosanva nkhululukileni.

 39. chigamulo chabwino ndikudula dzanja lamanzele, akadzabaso dzanja lamanja, akadzabaso mwendo wamanzele kenako wamanja akadzabaso ndiwosanva nkhululukileni.

 40. This is unfair punishment! The life of human being is very expensive than anything.lets try other ways. Ungoganiza utakhala iweyo kapena m’bale wanu munakamva bwaaaaanji? Imeneyo si deal.

 41. This is unfair punishment! The life of human being is very expensive than anything.lets try other ways. Ungoganiza utakhala iweyo kapena m’bale wanu munakamva bwaaaaanji? Imeneyo si deal.

  1. ha ha ha kodi inuyo mwavutikila kugula katundu ndiye wina azangokulandani basi????? akuba ndi anthu oopsa kwambiri mukazamuna Nazo muzasiya zanu mukunenazi

 42. CHOT TZIWE NDCHAKUTI, ‘ALIYENSE AZALANGIDWA MONGA MWA NTCHITO ZAKE’ YESU AKUBWERA2 OHO

 43. Nkhani zomaotcha munthu akagwidwa ataba zafika posauzana, but in my opinion thats not good to do so, lets remember that our country has got laws accordingly to every matter, olakwitsitsa siwakuba yekha ayi koma almost tonse, tinangowona kusiyana zochitika zathu, ena achwelewele, andewu, ufiti, and the like…. Mulungu anamusintha Sauli kukhala Paulo, and yet we call Malaw God fearing country…Is it true?

 44. Vuto ndi ya police anthuwa akaba kupitanawo kupolice mawa ukakumana naye akudya chap pachiwaya amutulutsa mmalo moti akalandile chigamulo moti apa nkhani ikhala imeneyi akapezeka kutentha basi kkkk

  1. every person has a right to bail and fair trial. People who are rich but hve committed serious offences are out on court bail .People dont talk but when a poor thief steals a laptop nd handbag he is being killed and u blame the police for that .Life is so precious my dear. Learn to forgive others when they commit minor offences.

 45. Mphoto ya uchimo ndi imfa….amenewo ntchito za manja awo zawachitira umboni…& enytym mr president akhala akulengeza kuti shoot to kill ya bwelera.

 46. Malawi where is that from is murder regalised in malawi ? Why you spared cash gaters life ? RIP!!!!!!!!!hhhhh

 47. kodi Acash get adakasungidwabe kuootcha amenewo bwanji ndi uwyo amene akumaopseza anthu kuti awaphayo . mtsogoleri omachita kuyerekedwa mkupha

 48. burning em looks to be a harsh punishment to em, but e feeling these guys left you akakubela it sucks big time am e leaving witness i knw how it feels, kuwaotcha si deal koma mwina kungowathyola miyendo

 49. Well done Guys keep it up to clean them once they found! Inu amene muti alakwitsa ndiye kuti simudabeledweko zimawawa man inu mwavutikira wina ango utenga osakhetsa thukuta?

  1. What if atakhala mphwako or 1 of yo family member wawotchedwa or wafa ifa yotele hw can u feel??? even boma limati we musnt take the law into our hands..shame

  2. Ameneyo ndimalipiro ake Big! Inewo ndaberedwako that’s why Iknw how painfull it is once Uget robbed. Ndipo anthu akuba alibe chifundo ayi amatha ukupha plus kukubera even wrist watch or ring ngati asowa chokulanda.

  3. @ frank atakhala m ‘phwako umudandaula chifukwa choti ndi m’bale wako kma pasi pantima ukudziwa kt walandila malipilo ake ana oterewa nthawi zina amakhala osanva makolo kuwalangiza osanva

  4. I’ve been stolen from a number of times and i never felt the need to kill the person. How can you think 2 smartphones and a handbag are equal to a human life?

  5. @ Lonjezo me too I’ve passed the same situation for almost 4tyms! In 2003 they broke in my Aunt’s house they nearly kill all of us Iwas there for holiday in erea 36 LLS. Then 2006 Ilost one of my best frnd they killed him cos of TV plus aradio. In 2013 they robbed me R27thousands plus my laptop, computer and they tied me point me agun and leave me on abear tiles untill morning. This year on 9th January they hijacked acar plus took my tablet my Iphone and R6thousand ontop of that they stapped me at 7times Iwas hospitalised for aweek. So what U say my frnd?

  6. @ Lonjezo me too I’ve passed the same situation for almost 4tyms! In 2003 they broke in my Aunt’s house they nearly kill all of us Iwas there for holiday in erea 36 LLS. Then 2006 Ilost one of my best frnd they killed him cos of TV plus aradio. In 2013 they robbed me R27thousands plus my laptop, computer and they tied me point me agun and leave me on abear tiles untill morning. This year on 9th January they hijacked acar plus took my tablet my Iphone and R6thousand ontop of that they stapped me at 7times Iwas hospitalised for aweek. So what U say my frnd?

  7. The prblm is Ucan feel sorry fr them. But them not at all to feel sorry for U cos most of them they used drugs serious my frnd and ihate those thugs alot!

  8. The prblm is Ucan feel sorry fr them. But them not at all to feel sorry for U cos most of them they used drugs serious my frnd and ihate those thugs alot!

 50. Cifukwa chakulimba mitima yanu, iphani munthu amene naye wapha munthu, failing whc killing someone just becoz wapezeka ataba simple iterms like those its inhuman..

  1. mphoto yauchimo ndi imfa watsoka yemwe akuothedwa pasipano nd kuzaothedwaso ambuye akabwera

  1. its not jst a hand bag.. munthu wakuba ndi munthu oipa amabwera mzambiri more over kutchingira panjira..he could kill her or rape her….achita bwino kumuotcha munthu oipa

  2. Zoopsa izi.But I can’t recommend such Justice tho. Why do we have police? Enanu here u r the next on the line.Anthu azakusokonezani ndi munthu wakuba muzalandila zilango zowawitsa ngati izi f u r not careful.Be simple,smart and conscious.

  3. Thieves deserve very painful punishments according to humility inline with our laws! Some people are usually tempted to steal, a punishments teaches a lesson!! Nzotheka anthu amasintha. Inu simuganiza kodi? kuti nchifukwa ninji boma silidaike lamulo loti “Okuba aphedwe”…. Kupha si yankho lothana ndi mbava!

  4. Thieves deserve very painful punishments according to humility inline with our laws! Some people are usually tempted to steal, a punishments teaches a lesson!! Nzotheka anthu amasintha. Inu simuganiza kodi? kuti nchifukwa ninji boma silidaike lamulo loti “Okuba aphedwe”…. Kupha si yankho lothana ndi mbava!

  5. I agree with you wongani some people the jst born opanda chisoni coz moyo wamunthu u cant compare ndi handbag hmmm thus bad why killing .handband phone zinthu zoti ukhoza kugulaso

  6. I agree with you wongani some people the jst born opanda chisoni coz moyo wamunthu u cant compare ndi handbag hmmm thus bad why killing .handband phone zinthu zoti ukhoza kugulaso

  7. tamakambamkoni zomveka…u said some1 can buy a hand bag n a foni yesss ..so y these pepo ddnt think of buying their own handbags n fones instead of taking some1 elso,??? mutha nose azasowa ubakira mzake

  8. Sunakumane nazo apolice ngati akulephera ntchito kumpititsa lero mawa watuluka munthu wakubatu nayeso ndiwakupha atha kuchotsa moyo wako

  9. Kupha munthu mzako chifukwa choti wachimwa poti wakubera ndi tchimo lalikulu. kodi ndani amene sana chimwepo? Ntchito yoweruza si yathu. timusiyile yehova mulungu ntchito imeneyi yoweruza ochimwa. let us repent please.!!!

Comments are closed.