Reports reaching Malawi24 show that seven prisoners have today escaped from Mangochi Prison.
According to Mangochi prison officer in charge Jonas Chimoto, the prisoners escaped between wee hours of one to two o’clock on Sunday using a channel that they had dug at the toilet.
Chimoto added that the channel led a way out of the prison and they dug it using an old axe and knife.
The seven escapees are believed to have been led by two notorious criminals who are answering murder charges.
The remaining prisoners said they were afraid to to alert the warders on duty since the escapees threatened to kill the remaining prisoners if they dared to shout.
Meanwhile, the police have launched a manhunt for the inmates.
(MORE TO FOLLOW)
kkkkkk muzmanga ndende zolimba!!!
UDzanu idzo ife tinamangidwapo ku zmb
Zoona kupezamwai kuthabasi achina makuluni pachirili amavuta kwambiri
Grace Chinga Coffin
gd move
kukhwima anthu a ku Mangochi
kukhwima anthu a ku Mangochi
Achita bwino athawa akapume nawonso ndi anthu
Gus luck guy’s mulowenso chakumzuzu atijoine kumenyana ndi boma
Good timing,tidyere limodzi MONDOKWA!koma be reformed MWAMVA!kkkkkk.
Shaa zigawenga zovuta azitulusa camma 2am? Tisamale mmacottage plz.
So we have our own Michael Scofield in Mangochi!
So we have our own Michael Scofield in Mangochi!
Prison break
Kmso ziphuphu ndi zomwe za tchuluka
apolice akumalawi ndakutulukila ndinu makape kukuyimbilani 4ni kuno akumba muva kulibe driver kodi simumatha galimoto eeeeti
Koma akayidi athawawa ndiwoti adapha anthu pogwilitsa ntchito zikwanje, m’mawa lino ali kwanuko, ngakhale mukuti achita bwino
Andende amasulidweee!!!,amudima awone kuwala,kundende sikofela,ngati akufa munthu amene ali kunja akuyesayesa kugwila ntchito koma mavuto pwilikiti even njala,ndiye wakundende atani?alimbako?ndiye ngati mpata wapezeka atani?kuthawa kaaaa
Mangachi police anthu ogona mpaka kwathawa anthu oti amakhala nawo limodzi.
Athawa bwanj kuli migwanya
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life, this is what i caused myself, for allowing my fiance make sex to me unsecured without protection, although i never knew he is HIV positive. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the traditional healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS..
azasiya kuthawa kuzayamba ku mumanga amene anaba ndalama ku capital hill
palibe vuto penepo ngati tikuvutika ife ndye bwanj iwo
palibe vuto penepo ngati tikuvutika ife ndye bwanj iwo
I was in prison too pple dont get soft in that fuckin place. They did the right thang
koma malingana ndi ndende za kwathu kuno Zigawenga zingathawedi , ndende yaku Mangochi si nyumba wamba imene ija
koma malingana ndi ndende za kwathu kuno Zigawenga zingathawedi , ndende yaku Mangochi si nyumba wamba imene ija
koma malingana ndi ndende za kwathu kuno Zigawenga zingathawedi , ndende yaku Mangochi si nyumba wamba imene ija
Kuthawa sikupusa
mwamuputa mwanyali ndithu
Good news!!!!!
Akuluakulu let’s not concetrate on their escape bt on who aided them with materials they were using. However busy u might b dont u supervise n check the infrustractures or akamalowa? As u r aware that prison institutions r different from others whereby pipo r punished n find hard,stiff,difficult life to endure. unlike health, education institutions where pple stay free life. Banthu bachimbira awa nivigewenga vyakofyelapo sono mtovwilenge uli kuti maumoyo ghithu na katundu vivikililike???
kodi kumeneku bwanji
anahonga ma guard amenewo kuti atuluke. apa aziti athawa lili bodza za ziiiiiiI
Zachamba eti
Mwathawa ok koma mtima ndinu omangidwa ndithu mukadali mndende
Plison blake amalawi nde ili season chani
koma kumangochi eee zochitika zikuchuluka bwanji,wk singathe osamva china chake chochitika ku mangochi.WHY MANGOCHI!!
They have served so what ????
Sanalakwitse Kunjaku Kuli Njala What Abt Prisn Kulibwn Kumakakumba Mbewa Ku Mozambq Izy Guyz.
Yah pafikapa pafunika mapulani gyz mwachita bwanji akakupezani muziona nokha kkkk nawo apolisi
nonse mukut achita bwno ndinu zitsilu,u dnt knw zomwe mukukamba fools
Sizachilendo ineyo ndili kumalawi mzanga adaba ndalama za aziphunzitsi nthawi imeneyo asanayambe kuwalipira udzera ku bank. Koma atagwidwa adathawako ku mawula in LLZ. Then ndabwera kuno ku RSA anthu adathawaso ku vereeniging preson why? Wakuba nthawi zonse amakhala wa jakapu.
prison break kkkkkk
wapolice m, analandila ndalama za m,kaidiyo
interesting news. .
Its a deal.
Iwe Pofera ,tsopano chikatere? Bwanji enafe wangotipanga mndandanda,kodi ndife tathawako kundende? Kkkkk pofera wakalamba etii?
Apapa bwanji kuthawa kumeneko apolice akuziwapo kanthu.n’chifukwa chake amati agalu osaka,sakani,
kkkkkk Chidren of Rasters’ Escaping disaster.
Kkkk….alonda onse anali pa duty apite ku hearing……alephera ntchito!
changu changu tipezeni ku Zimbabwe tikusungan
Koma ndende zinazi ayi ndithu, mpaka ma prisoner kuthawa…
Apo achita bwino kuthawa ngati woba ndalama za boma amathawa iwo angalephere kuthawa or amati munthu wakuda alibe nzeru amagani moopya muja.
Ndiye Mangochi imeneyo,Mangochi ndi deal
Its thrue akubawo achitabwino bcz
Nayo afuna adye nacho chimanga chankhwimachi
Mwina apita ku admarc abweranso akukagula okha basi
Ine chikhalireni sindinayambepo ndanva kuti ndende ya ku nsanje kapena ya ku lunzu kaya ku kasungu kuti akaidi athawa ayi……koma #mangochi basi ndiye sipamatha mwezi athyola-athyolanso……ngat akuona kuti dzaola osangomanga dzina bwanji???……
Akupangirapo Ndalama.
Kkkkkkkkkkkk koma ndiyetu…….mbuzi za anthu ……..angokhalira kumangovina #beniyo za ntchito ayiwala
Chitsiru iwe osamavina iwe bwanji.
Ooooo kodi zafika potukwanizana????……bola ndikanakhala kuti ndaponda pakhomo pako kapena kuntchula dzina lako ndikanati wayenera kutero koma apa pokha wandionjeza m’bale wanga…….stop it!!!!!
Amon Kumainyadila Ntchito Ndnu Achitsilu
Kkkkkkkkkkkkkkkk tamuuza iweyo
Aaaa Wamva Galu Amenei Nde Uyankhe Ohooo!
kkkkkkk Ndawonanso apa kut munthu wa beni wakwiya. pepani pepani anyamata abeni ntchito yanu timayidziwa kut mkachaso basi
Kkkkkk koma #abeni aku malawi hahahahahaha oooo ntchito ikhale yoguba #pelete eti??.. Kkkkkkkkkkk
Ndipo ku Mangochi last month zinagwidwa zigawenga ndipo nkhani itafufuzidwa zidapezka kut asogoleri ake adali anyamata abeni omwewa. Ndiye ndi momwe zachitikiramu we r not surprised,anyamata abeni omwewo ndiomwe akudziwa game imeneyo.
Kkkkkk……….apapa zangoonetseratu kuti atopa ndi ntchito yawo ndiye sikuti adzingokhalira kumangoguba #pelete kuno nooooo. ..,,,,,, zimafunika onse atachotsedwa ……..mwina tione kuti adzikagubila kuti #beni waoyo
Vuto Ndi Nkala Bongo Mbuzi
Kkkkkkkkkkkkkkkkk……akumabwera ku ntchito ali ndi matsire kkkkkkk
Wavuta Ndi Win Kkkkkk
Kkkkk ndiye wina adzabwere kudzandimanga ine ndidzamuthamangitsa moti sadzandifunanso……….nanga ngat anthu akungothawako ndiye kuti awonako chiyani???……..mwina sakudya kkkkkkkkkkkk
Kkkkkkk
Ayende bwino mbava kumalondera zokhazokha kkkkk nzeru zambava zaboma zinachepera kaba.thawani zanzeru akangokupezani mbava mwaithawayo shaaaaa muli madzi
Prison ya mbola imeneyo komanso #maguardjail ake ogunatha line akuidziwa eee mmene ndimaziwala tindende taku Malawi munthu sungathawe chisawawa kalipokalipo
Nice move guys go far away
Amawachedwetsa afuna azipita ku joni…..
hahahaha kkkkk midyomba yawazika!!!!!!
Atatu ali kuno ku kenya
anthu opusa b like achita bwino kuthawa. these are the same pple who will b breaking ur houses in the middle of the night n killing innocent people .
chichi
Tiuzeni mayina awo mwina tiwadziwa
Wina walandila za manja apa economic cricis pa malawi
no wonder prisoner escape mmafuna akhalire zopusazo no bostic kkkkk nyc move fellaz
Sanathawe koma ma guard alandira ndalama zinyengo zake zadzadza ku malawizi
Komanso ngati anaona ngalande yokumbidwa ndizikwanje iwo amatani kulongosola popewa mavuto onga amenewa.
Guyz or mwathawa koma mulibe ntendere muntima nafeso tidziona nkhani tisanaikepo comment athawawo akuti anapha munthu kodi saphaso ena powopa kuwaulula kuti wathawa ku ndende uja ndiuyu ine ndikuti sanapangebwino komaso ayika moyo wao pa chiswe bcoz the can be killed from police or prison officers
Give them food plz.
ife anakuwululilani zaumfumu wake mamasulidwe kt ankhungu apenyeso amndende amasulidwe!
well done guys
apaaaaaah ndye ziliboh hvy y keeping them
Agwidwa
Mable Maybe Mhedziso, Clementi Cledow Stima, Pollina Mwanza, Hera Chipeta Roberto Mlenje, Petros Gowoka Nyangulu, Eliardoh Mkwanda, Stan Chitex Chitedze, Esther Kapesi, Chikondi Mugabe, Dali Mgabe, Stephano Samson, Leoh Arnold Chilongo, Mcdonald Josiah Nyangani EMINEM
Prizon Brek 7
bola pamenepo
Anthuwo mmasiya mpaka kumakagula bonya kw M’baluku okhawokha ndiye mmati asathawe? Ndiye mukufuna kumatinamiza kuti athawa podzera mgalande yomwe inakumbidwa ndi zikwanje mbali ya ku toilet? Ngakhale muvutike kuwasakasaka simungawapeze coz onsewo anali ndi mapasiport mmakwawo mwakut panopa alowa kale Mozambique lachiwiri atulukira jonzi
Kkkkkkk mmomwemo aise ukunena zoona…..eti mpaka kuwalola azikaona ana mmakwao
Ndende zamasikuano mzachibwana. Anthu anapalamula mlandu owopsya koma kumangowasiya aziyendayenda ndiye asathawe.
kkkkk ooo!! abanduka sangawapeze eeti!!.
Mmmm nde kt mukuziwapo kathu.
@ Brendah kumbali yanji? koma mwayimva mfundo yomwe wapereka wamkulu wa akayidiyo? Ndiyosamveka mkomwe
Kkkkk ayithawa shamba
Ndi dhilu yawo iyi
Ndimomwe amapezera ya kachaso. Ine ndimadabwa ndi anthu ogwira ntchito m’boma,bwanji anthu amenewa amakonda bibida kwambiri?
this just shows the terrible conditions of our prisons,lol
ther here in zambia..!
Self claimed parole
Self claimed parole
9c decision prisoners kp it up
9c decision prisoners kp it up
Gyz ngati mukundimva thawilani ku mozambikikuno
Gyz ngati mukundimva thawilani ku mozambikikuno
Inside job
Sanatawe apita kunyanja kukasambira
Good & Happy prisoner escape
Good & Happy prisoner escape
Akukaonekera kumaliro a chemwaliwa aja
This squad has not even been in the Camp yet. Anyway…. Miracle Money = Miracle Win.
This squad has not even been in the Camp yet. Anyway…. Miracle Money = Miracle Win.
Kkkkkkkkkkk mwacita bwino guyz.
Kkkkkkkkkkk mwacita bwino guyz.