The Football Association of Malawi (FAM) has officially announced that Big Bullets will play old town rivals Mighty Wanderers in the Charity Shield cup on 2 April, a week before the start of the 2016 season.
The Fa’s competitions manager Gomezgani Zakazaka made the announcement on Saturday afternoon soon after the end of the association’s Extraordinary General Meeting (EGM) at Mpira Village in Blantyre.
“Innitially, the Super League winner was supposed to play Presidential Cup winner but because we didn’t have that competition, Carlsberg Cup winner will play the league champions,” he said.
Bullets won the Super League whilst Wanderers won the Carlsberg Cup last season. According to Zakazaka, this will mark the begining of the shield cup organised by the Fa which has never been played before when a season is about to kick off.
In England, Barclays English Premier League winner plays an FA Cup winner in a Charity Shield just before kicking off the new season.
kumalawi kuno tikamati kuli ma team ndi Bullets ndi Noma enawo ngongosatilabasi .
kumalawi kuno tikamati kuli ma team ndi Bullets ndi Noma enawo ngongosatilabasi .
Kkkkk amvese kuwawa Neba Fam very guud
Ndi zomwe akufuna anthu amenewo
Sangasankhe ya Ku north ndi Central region nthawi zose bb v noma nzachidziwikire kut FAM matimu ena siwakonda
It will be a every good day in football fraternity, in asfaras ife Manoma & maule is concerned, bt lets avoid ziwawa, kumabwalo amasero, Elijah Wilson, Makula st
Kod ma team ndiawiriwa basi chilichose Noma vs Bb nanga enawa safuna kusewelanawo makondela kwambiri amene muli ku mipandonu.ndine sapota wa bb koma apa mwationjeza coz matimu osewa atengapo chikho last yr 2015 fuso langa kufamuko kod matimu enawa safuna kut nawo azipezako kangachepe.

All yes tidzipeleka m’pata kwa ma-team ang’ono ang’ono wa
All yes tidzipeleka m’pata kwa ma-team ang’ono ang’ono wa
Sukunama mchimwene
bb ndimoto chakachino
bb ndimoto chakachino
http://YouthToEarn.com/?ref=223152
http://YouthToEarn.com/?ref=223152
Civo, wanderes and Bullets shouldve battled for the shield. Koma paja Fam njaku nchalo kumwera kwa ma stadium ama pot holes basi choncho sinanga mmitu yawonso munalowa ma potholeswo. What goes around comes around.
Kkkkkk
Mmmmmhhh…..fam chani chimenechi?! charity shield imakhala F.A. cup champions ndi league winners, in this it should suppose to be bullets against civo
mmmmmmm ithink its not charity cup may be its juliet cup mpaka bb ndi noma?
Musadabwe kuti ‘Y’ NOMA.Ziri concho basi Noma ndi team ya zodabwitsa olo ikaluza anthu samakhulupilira.
Y not Civil?
Civo, noma & bb all won silverware. Why picking noma & bb? FAM could have arranged a match btwn noma & civo to find one to play bb in the shield. FAM have sidelined civo in my view
Game imenyedwera kt?
Game imenyedwera kt?
km ndiye kupupulumatu eee
km ndiye kupupulumatu eee
Have they come to adecision now coz they said there will not be involved in charity shield cup?
Have they come to adecision now coz they said there will not be involved in charity shield cup?
Nkhani ndikufuna kukokera ndalama a FAM bcz matimu awiriwa akakumana amapeza ndalama zambiri
Nkhani ndikufuna kukokera ndalama a FAM bcz matimu awiriwa akakumana amapeza ndalama zambiri
If u are Bullets Supporter please dont accept Good results 4 this Game,this Season is 4 Nomads only believe me.
Are you Gods of football?
No!! but thats the truth.
If u are Bullets Supporter please dont accept Good results 4 this Game,this Season is 4 Nomads only believe me.
Are you Gods of football?
No!! but thats the truth.
tiwotcha matumba achamba onse patsikuli
MAFUNO ABWINO Ka matimu inu.pempho chonde tonsefe ndife amw.tiyeni tisewele mpila wa paubale.
Maule ndi nyatwa 4 eva enawa ndi manyaka basi. Odi ukooooo
Noma 2 chingambwe fc 0
Nanga BB itakana, Chichitike ndi chiyani?
Kkkkkkk its 2 early to start babtising dis jibut wanderers, with their japanese player let BB TEACH HIM malawian foot ball
Wanderers won a silverware, so is civil service United… And Bullets won the super league… And in football the governing body has to decide as whether which teams should play the charity shield by looking at their followers and how much money they will make in the end. U can talk anyhow, but what is done is done!! More over the players will be the ones to play not the supporters, so stop fuming and wait for the day….
You’re absolutely correct
Zipalanenso mamba?
Ziliko
I think its ok tichepese maphokoso amene ayambika before kuyambika kwa premierleague,
Nthawi yakwana makasu a water nyami ayambe kugwila ntchito yaulere nbb isalore tikane
Ndiye axapexere pabullets
oro iwine oro osawina kapena kutenga chikho oro osatenga chikho nganganga kungobadwa kuti ndi wqmanoma basi tikumane mu april
#Kokaaa!tidzawonana tsiku limeneli#nomaaa_4_lyf.
Tamenyanso ma japane MAULE TO EXCEL
wanderers won Calsberg Cup #Moses-Brown. Don’t be too negative about ye Nomads.
Amenye Ayaya fc ndi Civo,game over
That’s your suggestion. FAM is the soccer governing body.
Pezani ina imenye ndi ayaya fc, ife ayi takana
Its only in Malawi where a team without any silverware can participate in the so called “Charity Shield”. Football Administration mdziko lathu lino ili very poor
Vry vry poor indeed.
Mr Chiume R u serius can u please mention the defending champions of all silverwares played in last season.. Otherwise despite poor football adminstation in our country this is not true.
Start following soccer bwana Bullets are defending the super league crown while the nomads are holders of the carlsberg cup
Ife komweko ku Manoma ko
Silver ndi dhilu
ku FAM kuli mbuli,mwatengeranji team ya number 4? Kukondera basi osatenga Civo kapena Mafco bwanji?
Neighbor amenewa mantha?
Umbuli ndi matenda choti mudziwe samatengera ma no ayi koma amafuna ma team omwe angapedzetse ndalama zochuluka ku stadium,
kkkkkkk iwedi ndi mbuli eti? Ku England amatenga team yomwe yawina EPL ndi yomwe yawina FA,mudzidzitsata,osati poti agogo anu amakonda Noma basi nanunso mapazi londolondo mukhaula nazo
according ur statement Fa here was std bank which was by Civo
Kkkkkk japanese vs mafumu a chikopa pa Mw. Tionera limodzi, ine ndi BB 4gud
Mukuwona ngati tikukuwopani? mwaswedwa kawiri last year,tikamati Bullets ndikumtunda simudziwa,chaka chino tikugagadaninsoni,BB 4 LYF
ife tilipheeee! m’mene ipangile FAM mo ndi momwemo.mutipeza.olo tisapange training naa inu simungatinyinye
Ngat ku FAM kuli mbuli bwanji osakawaikako bambo ako akakhale azeru kumeneko bwanji Bullshit wandikwiisa wanva mwato ndikuba chinangwa cha athu et
Ukwiya sunatiiiiiiiiiii
Wonderers 4eva
Wonderers 4eva
Wozindikirawe pita ukayendetse FAM
Wozindikirawe pita ukayendetse FAM
Guys kumvetsa kwanga nkokuti standard bank idasiya nde sangatenge team yomwe idatenga chikho choti chidatha #NOMA forever
Guys kumvetsa kwanga nkokuti standard bank idasiya nde sangatenge team yomwe idatenga chikho choti chidatha #NOMA forever
zili bwino kukayesa zida za season ili mkudzayi
zili bwino kukayesa zida za season ili mkudzayi
charity wa pa number 4 palibe anatenga ka chikho kenakake?
charity wa pa number 4 palibe anatenga ka chikho kenakake?
i love it
i love it
maule adzamwaso wamkaka kip da fire burning
maule adzamwaso wamkaka kip da fire burning
Munsakhe ina mukufuna muxipangira ndalama bullets afam pexan ina yot izamenye ndiayaya fc
Munsakhe ina mukufuna muxipangira ndalama bullets afam pexan ina yot izamenye ndiayaya fc
Kodi muli ndi photo yokhayi?
Kodi muli ndi photo yokhayi?
akumane pa 2 April azakumaneso pa 9 April? tanganizani bwino akulu-akulu.
akumane pa 2 April azakumaneso pa 9 April? tanganizani bwino akulu-akulu.
Wosatenga Civo bwa? mukufunatso muzabe za pagate? poziwa kt bullets ili ndi masapota ambiri,
Wosatenga Civo bwa? mukufunatso muzabe za pagate? poziwa kt bullets ili ndi masapota ambiri,