At a time when Malawi’s economy continues to stumble, Illovo Sugar Malawi limited has disclosed that its sugar sales in the country have been hit hard to the extent of slipping to 40 percent.
The development has been attributed to incessant rate at which such commodities are being smuggled into the country.
Illovo public relations officer, Ireen Phalula is on record as having told a local daily that such commodities like sugar are largely being imported from neighboring countries like Tanzania, Zambia and Mozambique with import licenses that apply there alone.
“The net effect of this for Illovo as a company, amongst other, is that sales in the current year are down by 40 percent compared to the same time last year. Most of the sugar being smuggled into the country enters the country without Vitamin A fortification, which is a legal requirement for sugar on the Malawi market.” Phalula told local daily this week.
Phalula also said Illovo Malawi provides direct jobs to over 10,000 Malawians and that it indirectly creates even more jobs whose viability is under threat with the smuggling.
Tis comes as economic woes are forcing many companies to change their approach on business and expenditure.
Recently, Peoples Trading Limited announced the closure of 20 out of its 85 shops across the nation due to continued losses.
The Standard Bank also recently announced withdrawal of sponsoring the Standard Bank Knockout Cup, a development the bank tilted to the pace that the country’s economy is taking has made the bank “increasingly challenging” for the bank to generate revenue.
A recent report by international financial experts reveals that the Malawi Kwacha has lost about 35% of its value under the leadership of President Peter Mutharika, pinning it one of the worst currencies in Africa.
The report, published by US Financial aggregator, Bloomberg, shows that Malawi kwacha is just 2 places from the bottom of the Continent’s worst currencies hit by inflation. Slightly trailing the Kwacha is the Angolan currency. The Kwacha’s namesake in Zambia is anchoring the log.
Since his election in May 2014, Mutharika has presided over one of the worst rising inflation in Malawi, a development the report shows as one factors that has lead to “a slump in investor confidence”.
Value of Malawi Kwacha dropped to its record lowest point this month sending a shockwave of price increases on goods and commodities. Bloomberg also reports that Africa’s biggest economies such as South Africa, Ghana and Nigeria are also dancing to the same tune as that of Kwacha.
Kodi vuto ndindalamayanuyi ilibe power mwava awuzeni A pitala ndalama zipezeke mMW
malawi sugar is very expensive,pple in the community cant afford k700.or mutakhala inuyo wina akupanga k700 and wina k300 mungagule nda? ife we believe kuti chakunja chimadula coz of transport cost and othr cost koma kuno ku Malawi zadabwitsaaa
Siyani Kupanga Sugar, Chinangwa Tizimwela Madzi, Bread Tizimwela First Choice Opanda Sugar Amakhala Boo.

siyani kupangako muzipita kwanu
siyani kupangako muzipita kwanu
kkkkkk mwanyanya. ife sugar mpaketi bas jolly jas kk
Price is too high
mawojeza kulibwino kuseka cimeneco.
Sugar wa kunja ku cheaper wathu odula, ndiye chogulira odula nchiyani?
U guys read the inflation rate and the quality of the product properly then comment don’t jus bring in ure usless opinions here
The price of Malawi Sugar is high than Mozambi….suga
agalu amenewa samafunira zabwino anthu akwawo, tiyeni titenge gawo ife achinyamata mwina zingasinthepo. ndikuona kuti akulu akuluwa akalamba, ndiye mumadziwa akulu akulu akatha mano amadya minofu yokha yokha.mafupa amasiyira ana, ndiye chonde achinyamata tiyeni titengepo mbali pazomwe chikuchitikazi
kudula udyo..mukuonjeza kwambiri..
We cant have bread n sugar both expensive like cars…this is so pathetic Malawi
zanyanya sugar yemweyi mpaka k700 sakukwanilanso 1kg tiyamba kuika mchele mu tea bola mmimba mutenthe

Down Down with Illovo Sugar Up up wit Zambian Sugar
Down Down with Illovo Sugar Up up wit Zambian Sugar
Down Down with Illovo Sugar Up up wit Zambian Sugar
Tinayamba kugula sugar wa mozambique, very cheap
mmh lakhulani mukatha mundiuza
Kutsogoloku dzikoli tonse tidzafa tsiku limodzi kkk
Zambian sugar is cheaper and sweeter
next it will be 5%
Sugar kupangidwa ku malawi komaso kumadula kumalawi koma kumakatchipa ku joloza pamene mumachita kumutumiza pama track amatola zachamba eti imwani nokha tea wanu wanchere yo
Iyaaaaa! Mbuzzii za anthu sugar anatha zaka zamma 2000,pano mukupanga mnchere makape sugar mpaka ma supuni five asana kwanebe mu tea iyaaah itseken dzanu,kudulisaso ngati ku field ko imadula ndi tractor mesa ndi manja aanthu omwe muku adulisilao
ok
palibe chifukwa chomalesela shuga wakunja kuti azibwera mmalawi muno apa mukuona nokha nthengo wanuwu aaaaa
Amenewa ofunika ipambane pa 100%
Ku malawi anazolowela kubela osauka kkkkkk sugar, sugar, sugar illovo aaaah imported 4rom Australia kkkkkk
Ayoo ist produced in same country or neighboring country
Ayoo ist produced in same country or neighboring country
koma mchifukwa chan zithu zot zikupangidwa mdziko mommo kumamdula chonchi cement akupagwidwa konkunou koma mntengo wakewo nima lotlon even chimanga chomwechi tikulimachi….kuti uchipeze mnchiletso why malawi?

Akuluakulu tiyeni tipitilizebe kugula sugar wa mozambique yu, akutchipa bwino kobasi
Akuluakulu tiyeni tipitilizebe kugula sugar wa mozambique yu, akutchipa bwino kobasi
Akuluakulu tiyeni tipitilizebe kugula sugar wa mozambique yu, akutchipa bwino kobasi
Illovo why killing us please we blongs to u
Illovo why killing us please we blongs to u
Illovo why killing us please we blongs to u
Mizimbe ndiyatu iyii siiyikuchokera ku uk
Amfiti inu. Mmadulitsa ngati zakunja bwanji? Malo moyika affordable price mmangokweza ngati gold. Ife tikugula wa mbiquee mui sova.
Zachamba eti ndi ndalama yingati sugar tanenani 40 percent 40 percent kanjani?
Ilovo yomweyi ku SA sugar amatchipa.1kg R11.00.pomwe kumalawi ndi K800.or kuyisintha siikwana amwene.kutionelela kwambiri.achita bhooo.
kkkkk pampanjepamenepo komaya munasakahanokha musamalile apa tiyeni uko mesamumkafuna peter ndizimenezo muyisova amalawi kumeneko ine ndiye ndimatumiza 6okg kumpanje suger wakumeneko athuakwathu samamudzuwa machende apeter kodi akufuna zifike paja zinamufikila mb’ale wake uja pajatu zimati chomchi akakhala kwawo amavazakuti bwana fazitu panopa ili kuchipikupanzele kugula suger iena aliku ptc akudikila suger iena pano aliku shoplet suger watha panyapako peter ngati ulindima wu undiyimbile number yanga ili paline pangapomwepo
sugar ochokera ku zambia kumatchipa koma inu mukupangira pompa panchalo nd komaso ku Dwangwa kudula kwambir kungoti chopangidwa ku Malawi mmalawi akuvutika kuchigula
We are buying from mozambique and southern bottlers is next to complaine
oh yes due to high price of sugar people are you using juice powder to replace sugar kkkkkkk
Masiku ano tikungomwa fusion ndi zigomu break fast yatheka tikatero
Masiku ano tikungomwa fusion ndi zigomu break fast yatheka tikatero
b rbvy. dt
b rbvy. dt
Do a survey to find out real reason. Phalula, what you are attributing to as a factor for drop in sales is not true. You have become crazy with your pricing. Sugar in rular areas is sold at more than K800.00. The fact that you employ 10,000+ people will not make Malawians buy your expensive sugar. People will always go for an alternative. Next is Escom who will soon see a drop in number of customers.

Ife Kuno Ku Mj Boarder Timagula Suger Wa Mazambiki, Tinazolowelanso Iyaaa! Kkkkk
Ife Kuno Ku Mj Boarder Timagula Suger Wa Mazambiki, Tinazolowelanso Iyaaa! Kkkkk
ngati kuti mwina mizimbe yakeyoo amachitaa kukumbaa ngati miyala yamumigodi….allaa….tiyambaa kumapangaa tokha mmidzimutu
ngati kuti mwina mizimbe yakeyoo amachitaa kukumbaa ngati miyala yamumigodi….allaa….tiyambaa kumapangaa tokha mmidzimutu
Kkkkkkk kodi mzimwa sugar kapena tea?Malawi kwake kwatha chikhala matenda tikati tiyenawoni kwa sing’anga.
Kkkkkkk kodi mzimwa sugar kapena tea?Malawi kwake kwatha chikhala matenda tikati tiyenawoni kwa sing’anga.
If u dnt wnt to sllng ur suger in dis country pitani muzikagulitsa ku maiko aku uraya ndinu oputsa more over coz mukudziwa kuti Malawi tili mmabvuto anjala then mukumakakweza ntengo wa suger because of wat shatapu!
Kaya okonda tea zikakhala zidakwa ndesizimwa tea zimamwa beer basi, muisova
If u dnt wnt to sllng ur suger in dis country pitani muzikagulitsa ku maiko aku uraya ndinu oputsa more over coz mukudziwa kuti Malawi tili mmabvuto anjala then mukumakakweza ntengo wa suger because of wat shatapu!
Tinazolowela kubeledwa bas ngati akulila atown nanga ku vg dzikhala bwa
Tinazolowela kubeledwa bas ngati akulila atown nanga ku vg dzikhala bwa
Dont give us mpishupishu because of sugar what is sugar ? Ife timadya Zimbe ndipo tinalimbakale mitima
Dont give us mpishupishu because of sugar what is sugar ? Ife timadya Zimbe ndipo tinalimbakale mitima
Mwadulitsa kwambiri anthu sakugula ndiye mukudabwa chani?
Mwadulitsa kwambiri anthu sakugula ndiye mukudabwa chani?
chimanga nde ndi dhilu pano…asitse mitengo kaye.
Hakweeeeeeeeee inu mumati titogula wa pa Zemo pompa kkkkk muisova…
Hakweeeeeeeeee inu mumati titogula wa pa Zemo pompa kkkkk muisova…
10 kg it’s how much
10 kg it’s how much
Musamationese sugar wanuyo apa tinasiya kale ife kumwa tea.bolaso mchele ndiwaphindu ku tundu wanga wachi malawi.tikalima nzimbe pogula matibelaso mitengo koma sugar wanu kumadhulisa
Musamationese sugar wanuyo apa tinasiya kale ife kumwa tea.bolaso mchele ndiwaphindu ku tundu wanga wachi malawi.tikalima nzimbe pogula matibelaso mitengo koma sugar wanu kumadhulisa
ifetu tinasiya wanuyo timagula mosambiq….nde mwati wanuyo wakwela.?
shugaso pano,ife tikudya chakulamba m’mawa.asova asanati.
Kkkkkkkk
Kkkkkkkk
Kkkkkkkk
bwanji man
bwanji man
bwanji man
Kkkkkk, chakulamba mpaka
Kkkkkk, chakulamba mpaka
Kkkkkk, chakulamba mpaka
ndikungo nena tea amalela
ndikungo nena tea amalela
ndikungo nena tea amalela
Ife Tiyi Mayazi,.
DDP ikalowa bwalo ndi choncho….
Musova ….sugar mukatipatse naye busy kudulitsa ngati munthu angadwale atati samwa tiyi? Za tiyi tinasiya.
PITALA AMENEYO MUMUMVASO
sugar is very expensive and people stop using it.thats why your sales are going down
Ok
Heee kaya zanu izo ife ndye juice cola muphala instead of sugar. Kkkkkkkk kma pa Malawi eeee lyf nt simple crying iz evry where may de lord Almighty hear our crying He is only one hu can calm us.
mukhaule sugar wanthaka yathu mpaka seven hundred
My grandma used to cook us sugarless porridge. My mom too, tea is my enemy, we drink kachasu wa mizimbe, no sugar is added. Thobwa without sugar eeish so nice. Moti panopa I dnt kno the price of sugar. Chimidziswagger.org
Nanga akanakhala kut Suger apamga ku USA bwezi ali pa bwanji, tikumachita kukanika kugula Suger koma zimbe zilima tokhala mmmmmmm ilovo ar u Really serious?
Kagulitseni kwa azungu ife tasiyadi kugula sugar wanu mkudulitsa ngat tonse ndife zikhwaya muno. Mapeto ake mwayambanso kudabwa kusonyeza kut simkudziwa kut malawi ndife amphawi eti???
zanu zimenezo ine sindimwa tiyi.
Anyanya mitengo nawonso mapazi awo…sakuona mchere omwe uli ofunikira kwambiri sukudula kkk
Sugar wanyanya kudula pa malawi.kuchita kukhala ngati akuchokela ku UK eishhhhhh
Illovo mumationjeza mxiul
I substituted sugar for msima as breakfast,because sugar is more expensive than five leaves of mpiru
Chicompany chmenech chinayamba kutibhowa kalekale,mot pano tinaiwara zoti ndiyakonkuno kumalawi,angotseka basi
Chicompany chmenech chinayamba kutibhowa kalekale,mot pano tinaiwara zoti ndiyakonkuno kumalawi,angotseka basi
May The Lord Have Mercy On Us.. Tinalakwa Chani Amalawi..!
May The Lord Have Mercy On Us.. Tinalakwa Chani Amalawi..!
Aaaaah koma iwe,busness ya ena ukulira iweyo,chikukukhuza ndi chani? Kkkkkk
sugar wa Mozambique ndi wo cheaper kusiyana ndiwanuyo
sugar wa Mozambique ndi wo cheaper kusiyana ndiwanuyo
Sellati 5kgs 45rand wamalawi tamutaya ife
Sellati 5kgs 45rand wamalawi tamutaya ife
DPP woooooyeeee ………..APM wooooooooooyeeeeeee chala m’mwamba chala m’mwamba lulu luuuuuuuuuu …….
DPP woooooyeeee ………..APM wooooooooooyeeeeeee chala m’mwamba chala m’mwamba lulu luuuuuuuuuu …….
Ngati mwatopa tsekani company yanuyo musatinyase nayo,ameneyo grade 6 pakana k1000? We are all tired with that otherwise we shall…………… With you
Ngati mwatopa tsekani company yanuyo musatinyase nayo,ameneyo grade 6 pakana k1000? We are all tired with that otherwise we shall…………… With you
Drink beer to save money for buying sugar
Drink beer to save money for buying sugar
SUGAR WAKUMALAWI KUDULANGATI CHIMANGA? TIMANGODYA NSIMA IFE BASI
SUGAR WAKUMALAWI KUDULANGATI CHIMANGA? TIMANGODYA NSIMA IFE BASI
amene muli ndi sugar wa maiko ena or mukuziwa uko akupezeka mungotiziwisa basi kuti nafe tizikagura komweko coz nkangosiya ine igwaso ifika pa 60 loadin down fall
amene muli ndi sugar wa maiko ena or mukuziwa uko akupezeka mungotiziwisa basi kuti nafe tizikagura komweko coz nkangosiya ine igwaso ifika pa 60 loadin down fall
Mzimba akumapezeka suger wa Zambia
Rubbish shame to all stakeholders including andale akumalaw fo their contribution ndidyera lawo
shasha ndi #BAKS basi
Rubbish shame to all stakeholders including andale akumalaw fo their contribution ndidyera lawo
shasha ndi #BAKS basi
Kkkkkkk amalakwisa ndiamene amkugulaniwo olo itafika pa k1000 per packet upeza wina mammawa walawilira kukagula mapacket 5 kkkkkk matama basi
Kkkkkkk amalakwisa ndiamene amkugulaniwo olo itafika pa k1000 per packet upeza wina mammawa walawilira kukagula mapacket 5 kkkkkk matama basi
Zafodya bas muzigura nokha zimenezo pano ife timangopwanya nsima nde kudula kumeneko muzigura nokha zimenezo fucken ILLOVO COMPANY SHIT
Zafodya bas muzigura nokha zimenezo pano ife timangopwanya nsima nde kudula kumeneko muzigura nokha zimenezo fucken ILLOVO COMPANY SHIT
sugar akudula ndiye akuona ngati atagule ndani
sugar akudula ndiye akuona ngati atagule ndani
Illovo must fall, we will stop buying your sugar for gud, u know most coz of poverty we are wise enough to find other alternative, Mizimbe titolima tokha iyi koma mtengo wa shuga high ngati zitochoka kunja asa!!!!

Iwe nde eatokota
i wish down with 100% akhale pa ziro no business
i wish down with 100% akhale pa ziro no business
Yoo, the warm heart of Africa, things are getting out of hand in almost every area of our Life, Mr Bigman any plans for better Malawi yet?
Yoo, the warm heart of Africa, things are getting out of hand in almost every area of our Life, Mr Bigman any plans for better Malawi yet?
Kkkkk zako izo ilovo.ine sugar sindiuser wa Ku malawi wachimidziyo.timadya hullets sugar waku southafrica kkkkk
Kkkkk zako izo ilovo.ine sugar sindiuser wa Ku malawi wachimidziyo.timadya hullets sugar waku southafrica kkkkk
We already knew dat n Malawi there z no break fast,so dnt tell us about yo percent
If malawi doesn’t have a morning after a night then u can say there is no breakfast in malawi.and for your own foolishness is sugar used for breakfast only??????

Sugar wathuyi athnk ndi waku califonia coz in real sense sugar xangafike 900 ilovo ur a disgrace to malawians mbava zawanthu atonde achabechabe ximunati ifika 90 percent tieni uko
Sugar wathuyi athnk ndi waku califonia coz in real sense sugar xangafike 900 ilovo ur a disgrace to malawians mbava zawanthu atonde achabechabe ximunati ifika 90 percent tieni uko
Mukutchula sugar lero,kkkkkalibe ulesi amapanga kafukufukuyo.njala imeneyi malonda Ndi nchele
Mukutchula sugar lero,kkkkkalibe ulesi amapanga kafukufukuyo.njala imeneyi malonda Ndi nchele
kaya zanu ife timatumiza wakuno joburg
kaya zanu ife timatumiza wakuno joburg
Tikumanwa juice osungunula ife,mwezi asanathe tikumangosungunula Pang,onoPang,ono,tikumagula K600 basi,1litre kusungunula 10Litres,khalani nayeni suga wanuyo mpaka 1000 kwacha iya
ndife anthanzinso kwambiri

Tiyiso lero akhaulatu abakha amenewa. Kkkkkkk
Sugar is so expensive I use honey instead of it; honey is natural and more healthier than sugar. Mwanyanya a ILLOVO sugar ngati akupangidwa ku Italy pa Nchalo pompa.
Sugar is so expensive I use honey instead of it; honey is natural and more healthier than sugar. Mwanyanya a ILLOVO sugar ngati akupangidwa ku Italy pa Nchalo pompa.
I dont think honey is cheaper than sugar
Sydreck Carter B Where I am it is cheaper than sugar it all depends on where you. the price is not uniform like sugar.
Sydreck Carter B Where I am it is cheaper than sugar it all depends on where you. the price is not uniform like sugar.
Mwanyanya Kumudulitsa Pano Tikumwa Juice Cola
Mwanyanya Kumudulitsa Pano Tikumwa Juice Cola
Sugar kudula ngat wachokera kuulaya fwetseki
Sugar kudula ngat wachokera kuulaya fwetseki
Ameneyu Ndiye Sugar Wadziko Lanji Nanga Wathu Uja Amaoneka Chomchi
Anthu tinatsiya kumwa thiyi kale kale…timadya nsima Break Fast, Lunch & Dinner. Tazolowelanxo apapa. Sugar asamachite kudhula kuposa packet ya salt + half kilo ya beef/pork.
I can understand this as it is fast becoming a luxury for the majority. I too would look for a cheaper alternative to stretch the few MkwS. Praying for the Malawians, they deserve better then this!
thanx
thanx
Welcome
Welcome
tinakadandaula munakati Salt, koma Ife Sugar tinagwilitsa ntchito nthawi ya Amayi Amandazi aja
#PeterMustFall
zinyanya ine ndiye ndazorowera kumwa banks
kudura sugar ngati timachita import? iyaaaaa my rubbish. agwaso pang’ono afike 80 %
mumaonjeza inu chokani okuba inu mumadulisa ngati mizimbe mukuoda kunja olomungotsekaso tizi user waku zambia ocheaper
so sad….timangomva zoti anthu amamwa tea ife tinayiwala
SUGAR izichita Ku dura ngati makhwara akasa…..damn it…bora kukagura Ku Tz or Zambia….than malawi
Help us God
mwanyanya kudulisa, ndayamba kumwa thobwa ine
Kkkkk NDE ukumathira chani thobwalo nzanga naneso ndiyambe hahaha
Kkkkk NDE ukumathira chani thobwalo nzanga naneso ndiyambe hahaha
Phalula, Illovo, escom, pse do some soul searching. Why is it that lacally produced commodities should be more expensive than imported ones? I have in mind sugar, cement, electricity etc. Let me teach you something free of charge. Most of the prices are inflated as they have to accomodate company benefits to employees. Company car, company house, free electricity, six vehicles to a funeral, xmass party/gifts, high salaries. All these costs are borne by the comsumers and most of them are down to earth peasants.By scraping the benefits you could bring down prices and sell more. Even the govt has some places where it pays utility bills for it’s employees who enjoy the services free. And Good Gondwe is sound asleep in the tradition of APM.
A product that is locally made is more expensive than that of foreign..munthu umagula chomwe ungakwanise.lol
your price is too high as if it is not produced in this country.musova!
Sugar winayo ndi wotchipa nde timakwanitsa kugula.
Inunso pezani misika kunja anzathu akakuguleni,kumeneko kuli ndalama. Pano sugar sikwenikweni koma chimanga. Ndemukamakweza muziganiza izo nzakonkuno kumalawi. Musadamdaule if you need more sales then reduce the price otherwise you keep on complaining .