Cashgate in Malawi is a deadly disease that is refusing to vanish as it has now seeped through different sectors of society.
The private sector has not been left out as some employees of National Bank of Malawi (NBM) have become the latest to be caught after swindling their employer of millions of Kwacha.
The bank workers who work at NBM’s Balaka branch are now in police custody after the bank sent auditors to the branch when NBM management realized that the branch was failing to sustain its services due to lack of funds.
The auditors found that the employees had stolen K93 million from the branch, a discovery that led to the arrest of a manager and two tellers at the branch.
The suspects are still at Balaka Police but officers refused to comment of the issue because of its sensitivity.
However, rumours suggest the workers wanted to loot more than K100 million from the financial institution before setting the building ablaze to get rid of evidence.
Kudya pomwe aimangilila
Kudya pomwe aimangilila
It’s not stealing they have taken there benefits.
guyz zalakwika koma mudziwe kuti nanunso mungchiteso zomwezo mwina kuposa pamenepo.Enafe timachuluka nzeru zikakhala pa anzathu. Gwero lake ndi umphawi komaso katangale wafala kwabasi.
kkkk Malawi wafika posekesa uyu Oba ma million ndiye mbava kalekale amangidwa koma mbauva zenizeni za cashgate zinaba ma Billion timango aa wakuba akudwala kaye ndiye mlandu waima kaye mpaka apeze kaye bwino. atachira tingomvaso kuti aa munthuyi wanenepa kwambiri ndiye unyolo wasayizi yake tibe.
Kwa ine no coment viva Dpp Viva!!!!!!
Kkkkkkkk
ngati kuli mbava zoopsa opanda mfuti ndi ma auditors…anayambitsa course imeneyi anali mbava yotheratu
Hey ! Nawawo bt vis malawians. Koma nde tilemela2
Ife tingoti phee tiwone
Ndizoona national bank ndiyakuba zedi
Jb spirit. Outtttttttttttt!!!!!!!!
Aaaaaa zoona amaitha mpakana kubela Bank,kubela dziko,kubela Boma,mmmmmmmm..Makolo anthu amat mwanawe uzivaya ku Geli Coz ukapanda ku Gela uzakha Mbamva.Nde kod anthu amene asewera madinkamuwa mesa ndioGela.Nde ku Xul amaphuzisaxo mmene ungabere et.
CASHGATE IS INSTITUTIONALISED IN ALL SECTORS AND SYSTEMS. SO OUR MONEY IS NOT SAFE ANYMORE. MAYBE WE SHOULD GO BACK TO THE OLD WAYS; KUKUMBIRA PANSI OR KUSUNGA MUMTSUKO…
Umphawi wake umenewu munthu atani?
Ok dzikupitirabe
the bank makes millions and yet ur getting nuts whats the solutions if we want these things to stop banks and any iñstitution has to realiz that its not 1990 anymore life has changed #paywellyouremployees dats the solution
Zosadabwitsa ndi mmene dziko lathu likuyendera. Malawi wanukha.
Nde mwati zimachita kusenzedwa madengumadengu? Shaaaaah
Ineyo November ndinabwera Kwathu Ku Malawi after 7yrs kinda Kubota Ku bank kukasitha ndalama za kunja kupeza bankteller akunena Matengo wina koma bank information numbers is high kundisintha mosika komaso opanda bank exchange slip kumufusa slip akuti alibe printing papers
Unprofessional.
this is muder case. ayenera nawoso aphedwe.
#Malawi ilipamavuto azachuma kale akungowonjela mavuto enanso
#Malawi ilipamavuto azachuma kale akungowonjela mavuto enanso
It’s a wake-up call to NBM staff to audit their branches nationally
It’s a wake-up call to NBM staff to audit their branches nationally
They are educated people
Angokambilana nawo asawamange sakuyiona njala?
And those transacting at Liwonde NB should also take great care; you are either paid less or deposits reflecting wrong figures
Nothing new
Bank cashgate,eish!!.
mbuzi imadya pamene ayimangilila
Kupakula Kkkkk Ndani Samafuna Dola Apolice Muziba Chani? Aphuzitsi Ka Book? Ma Doctor Achina Raa Panado Kuba Ku bank Ckulakwa Week Imodzi Bank Ibweza
Iam not surprised to hear this theft issue for Malawi is addicted to this act of devilsh.When I see a Malawian I see the most crooked person on earth seconded by a Nigerian.Very wonderfully in these two countries there are so many preachers and prophets who claim to be sent by God and its people pretends like sheeps yet are goats.The bible says curses and drought will follow such nations.
Njala yavutadi pa Malawi
Imadya pamene aimangilila
Atinamiza pang’ono ndi bank manager ndi teller mmodzi osati awiri, ife tilikonko
Ba dira masepa batho ba teng.go batla ba ya toronkong.
Vuto la aMalawi makamaka aChinyamata akalembedwa. Malo molimbika kugwira ntchito mapulani amakhala a Micheni, Madiru, Ngini basi. Zoti kampani ikagwa ulova utipha, tivutika ndi ife tomwe kulibe
Mabvuto akula. National Bank declares billions after tax koma pay it’s worker’s peanuts. After all this the bank never lose, they are covered.
Asiyeni ameneo akufuna alemele mwansanga.
State of anarchy and moral decadence
These are the kind of people that digging Malawi on the ground…the enemies of progress! Gosh! arrest them all
Komatu aphunzitsi ali ndi SIP GATE. K k k k k k. Komanso makope kuwagulitsa basi! K k k k koma akakugwira kamchere kako kathera pompo.
The thieving demons are freely operating in Malawi because even the leadership of this country is full of thieves. This cancer started with the so called A Chair. We Malawians need to repent to God so that he protects us. We need to spare a week for prayer and supplications that God should operate in our midst. Otherwise we are doomed as a nation.
May the Lord intervene.
Cashgate ili paliponse. Mumangenso aja adaba ndalama xa boma aja xausiru eti.
Cashgate ili paliponse. Mumangenso aja adaba ndalama xa boma aja xausiru eti.
It’s a pity
It’s a pity
Doller nkumangoika mu Jombo basi
Wandiwaza wamva
Doller nkumangoika mu Jombo basi
Imeneyo nde malawi kuba basi
Imeneyo nde malawi kuba basi
Aaaaa koma njala ili kumpanje ena mkumaba ndalama zochuluka chonchi basi cashgate sidzatha dziko lathu
Aaaaa koma njala ili kumpanje ena mkumaba ndalama zochuluka chonchi basi cashgate sidzatha dziko lathu
dziko wanu ndalama wanga anthu atopanaxo
dziko wanu ndalama wanga anthu atopanaxo
Nsoka kwa nonse okwanilitsa malemba nthawi yomaliza pakut mulungu azalanga ndithu anthu a mtundu wanji osakhutisidwa ndi malipiro anu ndemwapindulanji pamenepo
Nsoka kwa nonse okwanilitsa malemba nthawi yomaliza pakut mulungu azalanga ndithu anthu a mtundu wanji osakhutisidwa ndi malipiro anu ndemwapindulanji pamenepo
Betakachitin kamathandiza nanga zimezi
Betakachitin kamathandiza nanga zimezi
Awonjeza pakana ma millions pamene amalawi ena akugona ndi njala komanso kumfa ndi njala
Awonjeza pakana ma millions pamene amalawi ena akugona ndi njala komanso kumfa ndi njala
Aaaaaaa ine kudabwatu thawi zonse ndingalowe mu bank imeneyo amangoti offline kapena no network kkkkkk munali bzy mukuba eti? Muziona basi
Aaaaaaa ine kudabwatu thawi zonse ndingalowe mu bank imeneyo amangoti offline kapena no network kkkkkk munali bzy mukuba eti? Muziona basi
Umva 5yrs choncho umbanda ndi umbava ungathedi,kubandula 21yrs imprisonmnt ena sangayerekeze,koma akatero wamuninkha kale judge ndi 1mita ,ungomva 6 wiks kwinako aziyendera kkk mw walero
Umva 5yrs choncho umbanda ndi umbava ungathedi,kubandula 21yrs imprisonmnt ena sangayerekeze,koma akatero wamuninkha kale judge ndi 1mita ,ungomva 6 wiks kwinako aziyendera kkk mw walero
imadya pomwe ayimangirila
laston kamaliza,tikatenge kajakatu tikadyele
laston kamaliza,tikatenge kajakatu tikadyele
Aphady alijonz ndlama zawo amasungtsa konko,mbolatu pano akudalila kkk.
Short cuts are always wrong cuts.
Short cuts are always wrong cuts.
that ìs the way we gonna leave just because our leaders are gready .
that ìs the way we gonna leave just because our leaders are gready .
Phillip Prince Bamusi Halord Chikoti
Phillip Prince Bamusi Halord Chikoti
ine chiyambileni kulowa mu news iyi ya 24 hours yi sinamveko nkhani yokoma yakumalawi kuti mwina pali plan yamwino koma mavuto okaoka eish Malawi why
ine chiyambileni kulowa mu news iyi ya 24 hours yi sinamveko nkhani yokoma yakumalawi kuti mwina pali plan yamwino koma mavuto okaoka eish Malawi why
Koma Mulungu alowerere basi apo bi moyo wathu uli m’madzi.
Mpakana kunyamula mu Dengu kkkk
Mpakana kunyamula mu Dengu kkkk
Pano anthu anatulukila kuti kuba nkwabwino .
Makamaka zagulu Kapena boma.
Pano anthu anatulukila kuti kuba nkwabwino .
Makamaka zagulu Kapena boma.
Just arrest them
Just arrest them
Awachita bwino
Awachita bwino
agalu awa 15 grand yanga up to now sakundibweZera nakapanga complain up to now, iiiii God is watching ndthu
agalu awa 15 grand yanga up to now sakundibweZera nakapanga complain up to now, iiiii God is watching ndthu
that’s what happen when u r paying your employees peanuts!
that’s what happen when u r paying your employees peanuts!
dzikoli lafikapo abale kodi athu ngati akumba church ndiye mukanene ku Godiko kkkkkkk palibepo chodabwisa apa aliyese akufuna kuchita bwino thawi yake isanakwane
dzikoli lafikapo abale kodi athu ngati akumba church ndiye mukanene ku Godiko kkkkkkk palibepo chodabwisa apa aliyese akufuna kuchita bwino thawi yake isanakwane
Tonse ndiakuba koma ukagwidwa umagidwe basi amagidwe akanganyawo
Tonse ndiakuba koma ukagwidwa umagidwe basi amagidwe akanganyawo
Sami Venkatesan
Sami Venkatesan
Zaheer Bheda
Zaheer Bheda
Kkkkk
Kkkkk
Sizachilendo ndiye kumalawi kumeneko.
Sizachilendo ndiye kumalawi kumeneko.
Aaaaa aaa ok? Iwowo kusolola nkukhalabe pomwepo? Ameneo nde achionatu kkkkk
Eeeee Malawi,everybody is stealing.I don’t knw who to trust nowadays coz right frm the top leadership of the country up to the bottom evryone is a suspect.What type of ubunthu r we building? This govt is the worst than previous ones.Too much thugs nowadays thats why Banks r withdrawing sponsorships
Kumpanje sikuzathekanso
Let them go ife tikaloweko
Sanabe angobweleka zimenezo abweza next week friday 6:30 PM. what do u think?
To work in a bank does not mean you have money/cash in your pocket!i see!
bank getyo !!kunyasalandi kwabeba
Why arresting them mmesa pa dzana mumati imadya pamene ayimangilira kkkkkkkkk not just saying
Why u can’t Steal mr president
Basi no more saving money @ the bank. kumangolemeretsa mbava ife kumatipweteka ndi ma service charges daily. Ndanka kukafuna chitini > ndikusegula chitini bank.
chitini bank kkkkkkkkk
chitini bank kkkkkkkkk
Its true there are some unknown deductions which are made by these people!!Kubera mulimi nthawi yonse akuvutika ndi dzuwa.Inu muli pa nthunzi mukuyenda chokhala.
[email protected] account tidzitsegula ndi zingati?
Damiano John, more details will be available in due course but one advantantage of this bank is that there will be no tellers and Branch Manager and heavy security against rats and termites kkkkkk.
Kubank masiku wano sikofunikadi kumasunga namtindi wa ndalama kumangolandirilapo basi
Kubank masiku wano sikofunikadi kumasunga namtindi wa ndalama kumangolandirilapo basi
WATCHERA KUMWENZI Nkhanga Zaona
i find it difficult to believe what this page writes
copy n paste Ma deal ali pali ponse,imakhala cashgate ukagwidwa. Even maid amatha kusowetsa ya ndiwo evryday,mwezi ukamatha kukhala ndi chithumba kupotsa salary. Tsoka kwa aphunzitsi bcoz they work wth chalk and books!
Bank Gate…

Eeh Aphulatu amenewo koma musawasiye chonchotu.mwaiyambitsa isathetu chaka mukufufuza…
Ndimadabwatu kumati ndalama ya panga report mu fon kuti akazanga atenga koma asanatenge mumaba eti zina zija mundibwezerenso mbava iny
Dziko limayenda bwino ndi CASH GATE! Just know guyz.
Mbuzi zimenezo mukazikumbire una ku Zomba maximum security zikaolere komko mpaka zikatuluke mphutsi,mlandu wakuba ndalama ndioopsa koopsa akufuna anthu azigona ndi njala iwo akudya?Mbuziiiiiiiiii
Anthu amzeru amabela bank not munthu mzako
Zavuta pa Nyasaland zasolobana wachiona ndani akatamuke system.
kkkkkkk bankgate
Wats going on here n Malawi pple?Till today we are cashgating….. These r last days indeed remember what thee scripture says concerning thee last days: Thee scripture says,we ll 1.love Money 2.Murder 3.war 4.gay en etc hahah God forgive us
Without justifying their actions this is just a pointer to what a bad economy can do to a country.
Imadya pomwe aimangilira mwambiwu ndidaumva mkale
Yah amalawi amenewo.
good,mwina ife tkapeze maganyu kwao….
Ma deal ali pali ponse,imakhala cashgate ukagwidwa. Even maid amatha kusowetsa ya ndiwo evryday,mwezi ukamatha kukhala ndi chithumba kupotsa salary. Tsoka kwa aphunzitsi bcoz they work wth chalk and books!
Chalk ndi dhilu
kkkk ok chalk ndilu?
Kkkkkkk azingoba chalk chomwecho basi
Kunyenga ana basi
Iiiiih bomba limenelo
Iiiiih bomba limenelo
Naye Mphunzisi amagolepheresa wana kuti ilowe ma part time. Ma deal ndi pali ponse man. Eish !! Cash yavuta pa Flames.
Naye Mphunzisi amagolepheresa wana kuti ilowe ma part time. Ma deal ndi pali ponse man. Eish !! Cash yavuta pa Flames.
kkkk koma adha ujeni uyu inuso mumaganiza mwakuya bwanji kkk muli bho ma teacher ndi chalk basi
kkkk koma adha ujeni uyu inuso mumaganiza mwakuya bwanji kkk muli bho ma teacher ndi chalk basi
Ngati uli mphunzitsi, ukuyenela kudziwa kuti ukunama. Kapangeni upgrade kuti muwone kusintha!
Ngati uli mphunzitsi, ukuyenela kudziwa kuti ukunama. Kapangeni upgrade kuti muwone kusintha!
akuba likuni masikwano
maphunzitsinso amalowetsa ana mwachinyengo kywalemba xul
Koma mwandiwaza kikikiki ntchito yopanda unform kikiki
Mapazi anu mavewmda inu patjaxa panu ponunkhpo zikugwirizama apa pj pa pj kamwa panu
Kkkkkkkk nde ukumunena ndani zosamvekazo,ukufuna utatukwana koma ukukanikanso kulemba. Usova!
I joined teaching to serve not 4 money and i paid for the course
kkkkkkk jst passing
Dzimvere mtolo
Dzimvere mtolo
Ndani mphunzitsi anakapemha kukhomo kwanu kapena kwa mai anu? Nonsense!
Ndani mphunzitsi anakapemha kukhomo kwanu kapena kwa mai anu? Nonsense!
Wakulu mwakwiya, anthu sadziwa kuti dolo la opambana lagonera mwa aphunzitsi!
Wakulu mwakwiya, anthu sadziwa kuti dolo la opambana lagonera mwa aphunzitsi!
National GATE
where, when & how much?