Workers steal millions from National Bank

Advertisement
National Bank of Malawi

Cashgate in Malawi is a deadly disease that is refusing to vanish as it has now seeped through different sectors of society.

National Bank of MalawiThe private sector has not been left out as some employees of National Bank of Malawi (NBM) have become the latest to be caught after swindling their employer of millions of Kwacha.

The bank workers who work at NBM’s Balaka branch are now in police custody  after the bank sent auditors to the branch when NBM management realized that the branch was failing to sustain its services  due to lack of funds.

The auditors found that the employees had stolen K93 million from the branch, a discovery that led to the arrest of a manager and two tellers at the branch.

The suspects are still at Balaka Police but officers refused to comment of the issue because of its sensitivity.

However, rumours suggest the workers wanted to loot more than K100 million from the financial institution before setting the building ablaze to get rid of evidence.

Advertisement

169 Comments

 1. guyz zalakwika koma mudziwe kuti nanunso mungchiteso zomwezo mwina kuposa pamenepo.Enafe timachuluka nzeru zikakhala pa anzathu. Gwero lake ndi umphawi komaso katangale wafala kwabasi.

 2. kkkk Malawi wafika posekesa uyu Oba ma million ndiye mbava kalekale amangidwa koma mbauva zenizeni za cashgate zinaba ma Billion timango aa wakuba akudwala kaye ndiye mlandu waima kaye mpaka apeze kaye bwino. atachira tingomvaso kuti aa munthuyi wanenepa kwambiri ndiye unyolo wasayizi yake tibe.

 3. Aaaaaa zoona amaitha mpakana kubela Bank,kubela dziko,kubela Boma,mmmmmmmm..Makolo anthu amat mwanawe uzivaya ku Geli Coz ukapanda ku Gela uzakha Mbamva.Nde kod anthu amene asewera madinkamuwa mesa ndioGela.Nde ku Xul amaphuzisaxo mmene ungabere et.

 4. CASHGATE IS INSTITUTIONALISED IN ALL SECTORS AND SYSTEMS. SO OUR MONEY IS NOT SAFE ANYMORE. MAYBE WE SHOULD GO BACK TO THE OLD WAYS; KUKUMBIRA PANSI OR KUSUNGA MUMTSUKO…

 5. the bank makes millions and yet ur getting nuts whats the solutions if we want these things to stop banks and any iñstitution has to realiz that its not 1990 anymore life has changed #paywellyouremployees dats the solution

 6. Ineyo November ndinabwera Kwathu Ku Malawi after 7yrs kinda Kubota Ku bank kukasitha ndalama za kunja kupeza bankteller akunena Matengo wina koma bank information numbers is high kundisintha mosika komaso opanda bank exchange slip kumufusa slip akuti alibe printing papers

 7. And those transacting at Liwonde NB should also take great care; you are either paid less or deposits reflecting wrong figures

 8. Kupakula Kkkkk Ndani Samafuna Dola Apolice Muziba Chani? Aphuzitsi Ka Book? Ma Doctor Achina Raa Panado Kuba Ku bank Ckulakwa Week Imodzi Bank Ibweza

 9. Iam not surprised to hear this theft issue for Malawi is addicted to this act of devilsh.When I see a Malawian I see the most crooked person on earth seconded by a Nigerian.Very wonderfully in these two countries there are so many preachers and prophets who claim to be sent by God and its people pretends like sheeps yet are goats.The bible says curses and drought will follow such nations.

 10. Vuto la aMalawi makamaka aChinyamata akalembedwa. Malo molimbika kugwira ntchito mapulani amakhala a Micheni, Madiru, Ngini basi. Zoti kampani ikagwa ulova utipha, tivutika ndi ife tomwe kulibe

 11. Mabvuto akula. National Bank declares billions after tax koma pay it’s worker’s peanuts. After all this the bank never lose, they are covered.

 12. Komatu aphunzitsi ali ndi SIP GATE. K k k k k k. Komanso makope kuwagulitsa basi! K k k k koma akakugwira kamchere kako kathera pompo.

 13. The thieving demons are freely operating in Malawi because even the leadership of this country is full of thieves. This cancer started with the so called A Chair. We Malawians need to repent to God so that he protects us. We need to spare a week for prayer and supplications that God should operate in our midst. Otherwise we are doomed as a nation.

 14. Nsoka kwa nonse okwanilitsa malemba nthawi yomaliza pakut mulungu azalanga ndithu anthu a mtundu wanji osakhutisidwa ndi malipiro anu ndemwapindulanji pamenepo

 15. Nsoka kwa nonse okwanilitsa malemba nthawi yomaliza pakut mulungu azalanga ndithu anthu a mtundu wanji osakhutisidwa ndi malipiro anu ndemwapindulanji pamenepo

 16. Aaaaaaa ine kudabwatu thawi zonse ndingalowe mu bank imeneyo amangoti offline kapena no network kkkkkk munali bzy mukuba eti? Muziona basi

 17. Aaaaaaa ine kudabwatu thawi zonse ndingalowe mu bank imeneyo amangoti offline kapena no network kkkkkk munali bzy mukuba eti? Muziona basi

 18. ine chiyambileni kulowa mu news iyi ya 24 hours yi sinamveko nkhani yokoma yakumalawi kuti mwina pali plan yamwino koma mavuto okaoka eish Malawi why

 19. ine chiyambileni kulowa mu news iyi ya 24 hours yi sinamveko nkhani yokoma yakumalawi kuti mwina pali plan yamwino koma mavuto okaoka eish Malawi why

  1. Koma Mulungu alowerere basi apo bi moyo wathu uli m’madzi.

 20. dzikoli lafikapo abale kodi athu ngati akumba church ndiye mukanene ku Godiko kkkkkkk palibepo chodabwisa apa aliyese akufuna kuchita bwino thawi yake isanakwane

 21. dzikoli lafikapo abale kodi athu ngati akumba church ndiye mukanene ku Godiko kkkkkkk palibepo chodabwisa apa aliyese akufuna kuchita bwino thawi yake isanakwane

 22. Eeeee Malawi,everybody is stealing.I don’t knw who to trust nowadays coz right frm the top leadership of the country up to the bottom evryone is a suspect.What type of ubunthu r we building? This govt is the worst than previous ones.Too much thugs nowadays thats why Banks r withdrawing sponsorships

 23. Basi no more saving money @ the bank. kumangolemeretsa mbava ife kumatipweteka ndi ma service charges daily. Ndanka kukafuna chitini > ndikusegula chitini bank.

  1. Its true there are some unknown deductions which are made by these people!!Kubera mulimi nthawi yonse akuvutika ndi dzuwa.Inu muli pa nthunzi mukuyenda chokhala.

  2. Damiano John, more details will be available in due course but one advantantage of this bank is that there will be no tellers and Branch Manager and heavy security against rats and termites kkkkkk.

 24. copy n paste Ma deal ali pali ponse,imakhala cashgate ukagwidwa. Even maid amatha kusowetsa ya ndiwo evryday,mwezi ukamatha kukhala ndi chithumba kupotsa salary. Tsoka kwa aphunzitsi bcoz they work wth chalk and books!

 25. copy n paste Ma deal ali pali ponse,imakhala cashgate ukagwidwa. Even maid amatha kusowetsa ya ndiwo evryday,mwezi ukamatha kukhala ndi chithumba kupotsa salary. Tsoka kwa aphunzitsi bcoz they work wth chalk and books!

 26. Mbuzi zimenezo mukazikumbire una ku Zomba maximum security zikaolere komko mpaka zikatuluke mphutsi,mlandu wakuba ndalama ndioopsa koopsa akufuna anthu azigona ndi njala iwo akudya?Mbuziiiiiiiiii

 27. Wats going on here n Malawi pple?Till today we are cashgating….. These r last days indeed remember what thee scripture says concerning thee last days: Thee scripture says,we ll 1.love Money 2.Murder 3.war 4.gay en etc hahah God forgive us

 28. Ma deal ali pali ponse,imakhala cashgate ukagwidwa. Even maid amatha kusowetsa ya ndiwo evryday,mwezi ukamatha kukhala ndi chithumba kupotsa salary. Tsoka kwa aphunzitsi bcoz they work wth chalk and books!

  1. Naye Mphunzisi amagolepheresa wana kuti ilowe ma part time. Ma deal ndi pali ponse man. Eish !! Cash yavuta pa Flames.

  2. Naye Mphunzisi amagolepheresa wana kuti ilowe ma part time. Ma deal ndi pali ponse man. Eish !! Cash yavuta pa Flames.

Comments are closed.