Malawi continues to offer refuge to stranded Mozambican nationals who are fleeing conflict in their country.
The Mozambicans are staying at the newly established Kapise ll camp in Mwanza district as fighting has intensified in their country’s Tete Province.
The current trickling in of refugees follows another pour in of more than 700 people into Malawi in July after RENAMO fighters had carried out two attacks in Tete province, and refugees say they continue to flee atrocities and killings by militias.
However, Kapise II is already home to more than 2,500 refugees and the current situation will likely worsen living conditions at the camp.
According to media reports, the refugees are facing difficult weather conditions due to lack of shelter and they need food, water, sanitation, and social support.
Some of that social support will have to be provided by villagers who live near the camp but they are worried about the refugee influx.
“We are staying with these people in the village, yes, but we are living in fear because we believe that in time they will completely run out of food, they will start stealing from us in our homes,” says William Mitiwe, the headman at Kapise ll village.
The villagers also fear some of the refugees might have run with weapons that can be used against them.
Mozambican authorities reportedly said those fleeing into Malawi are either thugs or lazy people. But refugee Jaleo Bernaldo denies this.
“They cannot say we are lazy people who are leaving Mozambique for free things at a refugee camp in Malawi. Here at the camp there are all sorts of people, including children, adults and the aged,” says Bernaldo. “Do they mean they are the ones who have been feeding us all this time?”
Malawi government authorities say they are trying to work with their Mozambican counterparts on how best to address the issue.
Meanwhile, international bodies are helping out. Doctors Without Borders is providing medical help.
The United Nations has provided some tents and has established a children’s counselling centre, where children also sing songs to help relieve them of trauma due to running away from home.
Malawi previously hosted Mozambicans who fled a 16-year civil war between 1977 and 1992. The current conflict between government soldiers and opposition RENAMO forces followed a disputed election early last year.
Let them stay,,,, we r the 1
Welcome the people of Africa we are one
Osasunga amenewa chifukwa amatithamangisa amenewa kwawo tikamadusa amafuna mamitikashi koma ife tili ndi makwacha
That’s good we are all God kids
M’Malawi amakonda anthu akunja…these guys amatizunza kwawo.Paja a Lhomwe munachokera konko,asungeni abale anu.
M’Malawi amakonda anthu akunja…these guys amatizunza kwawo.Paja a Lhomwe munachokera konko,asungeni abale anu.
M’Malawi amakonda anthu akunja…these guys amatizunza kwawo.Paja a Lhomwe munachokera konko,asungeni abale anu.
Azipita kwao amenewa anthu oipa kwambili
Iwe Mozambique usayesedala kudzandiyandikira !! kungokugwira while here in Malawi eeeeeeeesh ndikugwira ukapolo uja waaaanyooooo!! ndipo ulakalakanso kuthawiranso kwanu komweko phwanga!!!!!! wandizuza mokwana!!!!
They abuse us wen we go to there country en they dnt show respect so does it mean kut ife ndi asamaliya a chiufundo tu hell wth yu
Shw!
koma guys amalawi ndi chani?kupusa kapena chifundo?anthu oipa awa,,samationa ngati anthu amaiwala kuti akayamba kumenya first option kothawira ndi kwathu,,guys tikamakumana nao tiziwasecha nafenso,,asatizolowere
Zmene ndnapeza malawi nd dziko latulo + anthu akeso not dziko lamtendele azivaya asova komweko.
aMalawi ndife opusa thawi zonse, we alwaz welcome strangers kaya maybe bcoz of poverty??? Tonseee Mbuzi
Thanks Chicco Adriva Pilitu for your likeness on my comment.
No problems kuno Xeno njee
Nzako akapsa ndevu zimile,,,,,, mawa ndiife Tanzania ikamazatitsira wangitao moto. U better mind Ur comment Guys
ndife amodzi
Kod nkhondo idakali maona ngt zakale2 mh tawalandila amenewa koma njala kuno acibale akufa ndinjala kundende uko nde kay awa tiadyexa cani kay
please if there is a help give them dot point as they are guilty bUt its their caused them to be needy as such.
they dont even recognise malawians as neighboures
anthu ankhaza amenewa kwapitila kapena kudusa mziko lawo. kwaamene mumayenda you can witness this
Ndipo ine kuti ndingopeza mwa m’modzi wa moxo m’dziko lathulo ndingamuonetse zeno,anthu ameneaja nthawi iliyonse ndikamabwela komaso kupita kutheba amativutitsa kwambiri,panopa kuteleku ndikamadzabwela adzandivutitsa
Lets welcome them although there r clazy people, to much kutibela m’ma border mwao tikamadusa. Ndiye ukhonze pansi pa mtengo umva wakonzela president m’mutu anyway tiyeni tiwalandile we r one image from one God.
Warm heart of Africa
Ur most welcome feei free,dnt overcome bad 2 bad bt bad 2 gud God lv us be blessed
Boma lawo likuti anthu omwe akulowa muno ndi zigawenga kapena anthu aulesi chabe. This just shows that there stupid government ain’t appreciating what we are doing for their people. Bwanji tiwagogomese azivaya?
I have been with these mozambicans for a while but all they know are bad manners and ill treating malawians since malawi is peaciful nation let them hide and provide all that requires never do tit for tat so that if they have senses they should learn something from us malawians but dont let them behave like animals here in malawi they should learn how to respect human diginity with positive mind as we do if they will fail to live in hamony with the locals they will be unwelcomed too actually too much liniency sometimes is not good all they have to do is to coply with our rules and respect them………!!
Although we know Mozambicans to be bad people in general, let’s still help them for the sake of ‘loving thy neighbor as you love thy self’. Just remind them that we do burn thieves here.
Thanks Tchona Wanyerere Kalipande for your likeness on my comment.
Guys anthu amene amativuta mdziko mwao siamene akuthawa nkhondo lerowa akanakhala asilikali ndikanati asapatsidwe gawo kma amene tikuwatsungawa zimenezo sidzikuwakhudza, tionepo bwno pamenepa
Alandilidwe basi nkhondo ikusausa kwabasi.mumene akuvutikila ana ndi azimayi.sinthawi yosalana iyiii
Gyz ndikuonapo atsikana pamenepo tiyen tipange limodzi limodzo tiakwatile kuti dzik lathu liwathandize anthu ocepa ok
Alandilidwe koma azimai samalani…sizoti akamazapita kwawo azakhale atasiya tiana mbwembwembwe kuno ai..ndikuwadziwa anthu awa pobeleka chitute weniweni
Kkkkkk man mpaka chitute? Ai ndithu
Malawi ndidziko la mtendele ndipo la chifundo koma maiko enawa akuzuza anthu ochokela Ku malawi kodi iweyo malawi umatengambo mbaliyanji pa anthu ako omwe akuzuzudwa kumaiko RNA?
Send them back
Kodi ife tidzakhala achisoni mpaka liti?
Anthu amenewa kwawo alibe mkhalidwe pofunika adzibwelela kwawo.
Thanks Geofly Mpanga Banda for your likeness on my comment.
Lol in time coming azatilandira kwawo ikayamba ndi Tanzania.
Koma matsenga awo omasanduka afisi mkumaluma amalawi chonde tisazione, komaso chonde asecheni palipose asalowe ndi akasinja kut azithyolela zitseko ndikumaba katundu. Pomaliza akumbutseni kut timaotcha munthu akapezeka ataba choncho asunge mwambo
zachamba zimenezo
Asungeni ngakhale anandichita nkhaza
Well done Malawi but the world must support them too
Zowona ndine m,modzi eni mzmbque ndizowona ngakhale anuwakefe timazuzika ngati alendo moti tikalowa m,malawi timapanga zinthu momasuka komabe tisungeni anthu owopa mulungu inu
Si anthu awa njoka izi kwao amanyada kwambiri agalu awa kudutsa miseu yakwao ali ndi zimalamulo ngati sanavutikepo
Akuno ku Malawi ndiye kumapitanso kumeneko ati kuma farm kkk
Thanks Zigere Zindoga for your likeness on my comment.
Kkkkkkkkk mpaka akumbe chimbudzi ndi mpeni
Kkkkkkkkk mpaka akumbe chimbudzi ndi mpeni
Guyz akutikaniza kusegula Port athU aWo paNo mukuwalandila apaseni ma termZ ,…
Guyz akutikaniza kusegula Port athU aWo paNo mukuwalandila apaseni ma termZ ,…
I CANT BELIEVE THEY ALSO NEED HELP , THE WAY THEY TREAT US WHEN PASSING THEIR BORDER POSTS
I CANT BELIEVE THEY ALSO NEED HELP , THE WAY THEY TREAT US WHEN PASSING THEIR BORDER POSTS
vuto ndasilikali osati anthu wamba. Asoiyeni akhale momasuka
vuto ndasilikali osati anthu wamba. Asoiyeni akhale momasuka
Anthu oipa amenewo atayeni palipose
Anthu oipa amenewo atayeni palipose
Alandilidwe basi mamozambicano ndi anthu abwino bwino.kwawo kuno timakhala ngati tili ku Malawi alibe chipongwe ndi munthu.
Alandilidwe basi mamozambicano ndi anthu abwino bwino.kwawo kuno timakhala ngati tili ku Malawi alibe chipongwe ndi munthu.
Ndiye musamati mumakonda mulungu nanga nebayu simukumukonda bwanji anthu inu
Mutafusa akut kwawokuno kwatan chfukwa kuno kulbe kapena amenewo akuthengo km muno kulbe nkhondo kkkkkkkkkkk mmmmmm ayooooooo
Kodi muzadyetsa chiani anthu amenewo? Pamene chisowa ife eni ake dziko
mmmmmmm! athamangiseni kumeneko ndi anthu ankhanza awoo! zisiru izo ine sindiwafuna agalu amenewoo! achokeretu
Palibeeeeee! Musiyeni Malawi asunge anthuwo!! Kubwezera mkwamwini wake YEHOVA.
Asiyen akhale koma amawanzunza aMalawi akawapeza mdzko lawo amat yalowera kut ibwerere kapena iforame ikumbe chimbuzi ndi mpeni
Kkkkkkkkk kukumba chimbudzi ndi mpeni mpaka?
Kkkkkkkkk kukumba chimbudzi ndi mpeni mpaka?
Eya zmacitika and anthu akhala akuuzdwa kut atero. Ndi a nkhanza amanewa
abwere basi enafe tipeze mabanja
Tikanena za moyo wakhanza anthu awa ndiye eniwake komabe asungidwe mulungu azatidalitsa amalawife
Athu oipa osawa sunga samaganiza kuti tikhoza kuwathandiza
Malawi ndi dolo!Kuteloko ikuzembera thandizo kuchokera ku UNHCR!…Kuyiwonera patali…
Kkkkk komaaaa mwaiwunikila?
We know that mozambicans,hates malawians but malawians does not hate them.We always welcome any individual despite,colour of skin,race,religion or nationality knowing that, we all belong to one creater(JEHOVA GOD).
Welcome
bola asayambiste nkhondo
bola asayambiste nkhondo
aweteni ana anjokawo akakhazizika mudzaona zomwe adzakupangeni
Welcome all of u
asiyeni basi alowe
Tonse ndi amodzi basi , ine ndilibe nao problem abwere basi kaya onse bwera mnyumba mwanga ali olandilidwa
Anthuwa nkhalidwe lawo koma ndi lankhanza kwambiri ukangofika kwawo
‘The Warm Heart o Africa’
Koma anthu a moshco, alibe umunthu kwawo, amatizunza
Bwinoni ndi anthu amenewa. Ngankhanza ndithu. Ku Nsanje anawaletsa kukalima minda, moti sakhalitsana bwino, chikhalireni amaoloka ku Malawi kukathandizidwa mankhwala kuchipatala.
nafenso tiiyambisa pompano tiswanapo zikuchitika za mageyizi
Alandireni koma asiye kutizunza mminsewu ya kwawoi, makamaka pa chamano boarder ndi pa tete bridge.komaxo zoti tikapempha madzi akumwa asiye kutipatsa othira mchere .
Koma amenowa kwawo,ok aliolandilidwa mudziko lonyadilisa ndi mtendere!
Lets welcome them as we are all blacks
M’mmm “guyz no comment !!
We are one
Despite the inflow of riffles, well let’s welcome them.
Koma a Malawife aaaaaaah ifenso ndiye kaya! Inu Ziko la mozambik likukaniza njira yoti sitima ifike pa Doko la Bingu! Inu ndiye mukuwavomeranso amenewa kuti azitithera ma resources athu??? Nkhondoyo taiyambisa ndi ifeyo kodi??? Anthu amenewa amatipanga chikuwawe siomawasekelera amenewa ayi
usamakhale ndi mtima ngati wa afalitsi konda mzako ngakhale atakuchimwira mukonde mphotho its just in near future.. God sees
Aaaaah za zea! Masiku omaliza kulibe konda mzako monga uzikondera kkkkkkkk! Thus y a Malawi tizakhala anthu osalira mpakana kale kale! Iwe usanamepo apa! Masiku ano chasala ndi konda Ndalama monga m’mene uzikondera!! Mukanakhala anthu achilungamo mukanapita mukawalalikire a Mabungwe amene alolera kuti inu a Malawi muvomereze mathanyula chifukwa chokonda Ndalama! Usataye nthawi yako ndi kuti undilalikire ine wamva?? Cz Masiku ano chakula ndi chinyengo!! Ikakhala nkhani ya ma refugeese yi isakuwawe awowo ndi maganizo aine nawenso uli ndi ufulu ongonena maganizo ako not kundilalikira
asungeni basi ifeso ikayambika ndi tanzania tidzathawira kwawoko
Malawi dziko la anthu opempheradi komaso okonda mtendere.. Dziko la Mozambique anthu akuzunzika kuti adutse kupita ku Zimbabwe or RSA.. Kumawalipiritsa anthu ma R50 ena R100.. Ena akachitikanso tsoka akumamenyedwa ndi Asilikali awo.. Ndiye mukamati akuthawira ku Malawi aaaaa God Bless Malawi..
lf we are failing to pick up 1 bag ov maize do u think we can manage to pick up 100 bags?Mmmmm masovedwe commmm!!
What Malawi Gvt is doing is like playing with Lions or snakes l know these people they don’t have manners at all Villages near them at total mess believe you me. l have stayed with these people around the boarder anthu amenewa amazunza kwambiri and sayamika you caint walk or travel in their land freely without them tip off their authorities to abuse or detained u. My four years of stay with these people lived in hell. because of our parents and ancestors let them stay
Amenewo ndiye mawu koma poti amalawi ife ndi anthu achisoni tiyeni tiwalore akhale
Maka akayamba zawo zosanduka afisi zija atizuzatu abit khaphwirani amenewa heavy.
Afisi mwatenganso ulendo uno???
Asunguni kkkkh koma ndi fans yausiru ukamadusa mu seu mwao…ukamakaikisa stamp mu passport amakuuza kut uvule chipewa…..
azipita kwao ndikuti zandiyipira ,,nnaona akuwakwapula amalawi pa dzobwe chifukwa choti anapanga overstay ku rsa zosagwilizana ,azipita ndikuti
Hahahaaahaha!koma Big
big ndalamula choncho ine hahahahaha
Let them in,. but they have to learn about life this time as Africans n neighbors,, we don’t have to be hard to forgive, let God bless Malawi as a peaceful nation
Eish am abit nervous how to go back home through there roads these Makambaraza are hard and heartless…..imagine just to pass through there boarders what they ask is 1,000 Americano dollar( kkkk yet they dont knw its value)and you wonder why since i got all documents right.But never mind dont punish them back they are still our brothers and sisster…..keep them though its not first time,pray for peace in there country and more freedom and peace in our country so that we can keep them in time of bullets like ths.
Ngati kuli anthu oipa ndie amenewa anthu ankhaza kwawo azipita
okay. welcome malawi, km mumwele ndi chakunya chanu musapatse mavuto ena president tikulila mavuto anjala sono mukutawa kwanu mukufuna mumalize ndla zakumalawi pa mundimbela ndalama zanga ena pamene ndi kapita
I want one girl of them to marry her my..0718455448 plz help me to find (18..22)
Alandileni koma muwauze malire okhalila kuziko lanthu ndianthu amwano.Komaso azikhala mwatendele osatikuitanisa chisokonezo aiiiiiiiiiii
Anthu ankhanza awa tikamadutsa kwao mxiew kmaso amatibela pa nyamapanda boalder
alandireni ndi msangala poti mawa ndife chakuza mawa sichiziwika.
Kkkkk poti choipa sabwezera but honest they are heartless pple they dont think of tomorrow
Poti Malawi ndiwachifundo ndi anthu obwera,,,, km akanakhara kuti amafikira nkhomo ndi nkhomo ine ndikanawakana coz awa pa chimano border amavta heavy
Atisegulile Port ya Nsanje Tiwasungila anThu awo or Elss apite ku mwamba or -ku hell ‘..
Atisegulile Port ya Nsanje Tiwasungila anThu awo or Elss apite ku mwamba or -ku hell ‘..
kkkkkkkkkk bwanji aduridwe makosi dziko lino that’s y timangoponderezedwa kkkk
anthu a khaza kwambili awa tikapita kwawo nanji akava kuti ndmumalawi eshiii
ntchito yabwino yofunika kuigwira ndiimeneyi,,,,So Help Us Lord.
M’malo moti muthandize anthu anu akufa ndi njala ndalama mukukathela ma tchangani ozolowela nkhondo kwawo iwowo angalandile ndani ndinkhaza zawodzo!!!!!!..
Pliz welcome them and share whatever u have with them,i love you nd i know what it means to be a foreigner !
Malawi akutukwanidwa leloyu kutj overpopulated nkhani yake ndi anthu amwnewa nkhondo ikatha safuna kubwerera kwawo mxiieew! Olo kuwathamangitsa kuwaudza kuti Malawi naye alibe chakudya komanso ali pamavuto adzaoneneni iunkhani ya chuma… Anationapo ife tikumenyana? Koma akuona ngati ife tilibe pulobulemu? Nooo timakana zimenezi zoti tizizazumzika m’mayiko a eni ake. Nkhondo yawoyo ikazatha asazakhare kuno azakumbukire kwawo asathe malo kuno…
alande mabanja aanthu komanso cholera nd mphere
Koma chisoni chinaphesa nkhwali anthu amenewa ndiwovuta ngakhale kungodusa mdziko lawo kupita ku Zimbabwe kapena ku Jon amatizunza mpaka kuti bela ndiye zitakhala kuti zativuta kwathuko mkuthawira kwawoku angatisamale???
True bra..ndiwovuta kwambiri
Ndinkhandwe zimenezi
nthawi zina tisamangolola zilizonse, anthu amenewa osalephera ena akulowanso ndi mfuti mdziko muno as a result securitywise, we not safe.
nthawi zina tisamangolola zilizonse, anthu amenewa osalephera ena akulowanso ndi mfuti mdziko muno as a result securitywise, we not safe.
Abwelere kwao si anthu abwino awa
Ndisamve kuti mwawathamangisa tiyambapo
I hate the Mozambicans, very self-centered people, heartless,full of hatred.These people have got no mercy,they don’t take fellow people as humans. It’s a shame that they are seeking refuge there.When we are going to South Africa or coming back home,they treat us as animals not human beings.
Aloleni akhale nafe, koma akazayamba ufiti ndiye azizapita.
Ntchito yabwino imeneyo osabwezera choipa kwa wochita choipa. Anakhomelera doko lansanje. Amalawi tiope Mulungu azatitukula
Asungeni ndi #Abale #Athu
War In Mozambique Again?
Asungeni ngakhale amanyada kwawo komaso Auzen kut mvula inavuta chaka chatha tilibe chakudya
Welcome them but they musn’t kusiya bana, nkhondo ikasila kwao
A2 oyipa odzikonda
Tingowakhulukira
Mistakes has no master, ndi abale ndi alongo tiyeni tiwalandile m’mene tinawalandilira maburundi chifukwa mphamvu ya Mulungu siinama, welcome to malawi the warm heart of africa no xenophobia here stay with peace
Takulandilani koma musazolowele nafe tilindi mavuto
Welcome them poti enafe ku Mozambique kuli abale athu. Bt they shd not bring ISIS chonde, kaMalawi kathuka nkonokola kale atha kungokamalizapo
Cool guys abwelera kumudzi soon coz is just friendly war
Kodi nkhondo yayambikanso?
mmmn this is bad hey, now mozambique do thing like s a, zeophobic
Pankhani ya nkhondo ngati mwai wapezeka mkupulumuka chonchi mmmmmm yamikani Mulungu ndikuwauza kt azikhala ndi mtendere wawo kuno mku Malawi welcome.
Aloleni akhare koma muwauze kut tilibe chakudya
Kuli njala kuno ndiponso ndiwovuta mdziko lawo
Kodi khondo ili kuti? Cz ife tikumapita ndikubwerako
Komatu anthu amenewa alibe ubale kwawo amatizunza
aloleni azikhala nawoso ndi anthu ngati Ife tomwe osamazikonda bwanji nkhaza iya
Ndaniso wanena kuti akukanidwa?
Makape awa amazikonda athamangiseni tikalowa dziko lawo amatizunza
koma kwao kuvuta anganya amenewa
?
Thanks to hear that form you ,so we should be all alert about that ,prefect
Khondo ikatha sabwerera kwao
Anthu osalora kupondelezedwa alowa kale ntchire siife ayi kutibera osalowa ntchire
Moscow yayambikanso?Ifenso ibadwe basi tishosho Tz simadelera paja!!
timenyane friendly nd Tz bax
kkkkkkk u r clazy…
kkkkkkk u r clazy…
kkkkkkk u r clazy…
Let them stay please it’s our brothers and sisters , to look Poorer we’re same
Asungeni palibe vuto,,,Koma, Kunyada anthu awa tikamadutsa miseu yakwawo anthu achipongwe kwabasi..
Zoona chipongwe too much ma boarders awo.
Zoona chipongwe too much ma boarders awo.
athu amatama ukawapeza kwao awa azipita bax
mpake ine andifusa akuti mwini wake wa passport yanga Ali kuti ine ndati its me akuti nanga bwanji sunavale zovala zili pa passport cholinga a ndichose ndalama
Mmmmm #George..zimene amapanga anthu amenewa sindimatha kuzimvetsa kuimitsa ullendo akuti aone galimo ngati sikutaya oil kupa kuti uwadettsela mseu wawo.#Nyirend,anthu amenewa akamakupanga search amakhala ngati akupeza kale ndi Vuto
Athu ankhaza kwabasi takhala masiku 5tilikubwezedwa pa bridge limene lili ma roadblock awiwri. Koma poti ndife antendere asungeni basi.
kikikikikikikkiki,#James,Ndizomwe amapangatu…akakupeza ndivuto samafunaso ndalama ya kwawo akuti Rand basi .kikii
Awatu afera zaweni, even mu boarder akwathumu alimo akhalidwe oterowo, umayamba kusupa pa mwanza pomwepa, nde amenewo akhululukireni basi alowe.
Anthu oipa amenewa ,komabe asungeni mwina tsopano azindikira ,
Alandileni mwachikondi kuti adziwe ndife anthu amtendere. Ngakhale ndikudusa mudziko lawo ulendo wa ku SA ananditsitsa mgalimoto kukandilimisa mmunda kamba koti ndinalibe R3000.
ndipo amwene simunama a2 oipa kooopsa. amapanga nkhaza ngati kuti tifuna tipephe Malo pomwe ulendo wanthu umakhala wautali.
#Esie,Somba ikaola imodzi zose zimaipa.Komabe sitikuwakana.#Osman tikhala nawo awa muja tinakhalira ndi wena aja mma 1990s
Kikikikikiki…#Gomiwah…anthu achabe awa.#Tsegula sindimadziwa maganizo awo amakhala wotani?
Mumtsinje wazambezi malo okhalamo ngambiri…apite kumeneko isaaa
Kikikikiki….#Siphelille,musatero tiyeni tasunge basi
Kma ndiwanthu ozikonda bad kuposanso anthu akomwe ukupitako sindikuziwa kt mdaliso ukadakhala mziko mwao ndibwemzi amalawi akuphedwa angat per night kapena kt zinthu zikanakhala bwanji?
Tikanakhala kuti ndi ifeyokuti tikufuna Malo kwawo Sibwezi atalora awa..#Simeon
bola kumawasecha bwinobwino asanalowe enawo ndi zigawenga zotheratu
#Mr Chisinga,tiri pamavuto anthu awa akangokhalitsa muona ayamba kuonetsa khallidwe lawo angati momwe amatichitila muja tikamadutsa mu Dziko lawo akuthawalo..
Apatseni malo okhala koma phwanya nde adzinamize, anthu akhadza koopsa
Apatseni malo okhala koma phwanya nde adzinamize, anthu akhadza koopsa
nothing to say!# malawi
zi anthu zakhaza kwambili nanji akava kut ndmalawi eshiii or apolice awo asawone #plet ya galimoto ya malawi sikukakamila kwake
Amenewo awabweze kwa kwawo coz last week apolice anayimisa galimoto yomwe munali amalawi amwe abwela kuno ku south africa ndikuwamenya anthu kenako kuwalanda ndalama.one of them ndi bale wanga so faz imeneyo ndiyoipa izipita kwawo.
Koma naweso ukukhala kwaweni sichoncho?
Amene anawamenya abalewakowo siamene ali ku refugees camp, muziyamba maganiza musanayankhule bwana,
Iwe somba ikaola imodz zonse nde kut zoola
Uyu sanalakwe ayi, wanena bwino zedi. Anthu aku Mozambiki kunyasa too much amakhala ngati sitinawalere kwa nthawi yayitali kuno. M’malo mophunzitsana kukhala a ulemu iwo amatipangira nkhanza ku dziko lawo la nkhondolo. Iya abwerere lkwao konko
So those people who as going to south Africa which way are their using ?
Exactly my thought.
Same route man em in tete but no threats at all only dat the fight is takng place at renamo’s camp in jango very far frm city
Asiyeni akhale nafe
why not sending them back ? these people r selfish
Dont say that
At least u are better than those ones down south,