The battle for the golden boot award in the 2015 Malawi Super League season is over as it has produced joint top goal scorers namely Innocent Bokosi of Red Lions and Chiukepo Msowoya of Big Bullets.
Both Msowoya and Bokosi bagged 14 goals.
Msowoya had 13 goals before netting one goal in Sunday’s match against Civo United at Civo Stadium in Lilongwe.
The Big Bullets forward was required to score more than a goal against the 2015 Standard Bank Cup champions to overtake Bokosi.
The strikers will now share the Mk100,000 that was put aside for the golden boot award winner.
However, Msowoya and Bokosi failed to match the record set by Moyale Barrack’s Gastin Simkonda who netted 17 goals last season.
Koma a noma mukumva bwanji kumayamikila ma player ama team ena inu mulibe ma player? Nanga anuwo amamenya league iti? Zigoli zawo ndi zingati? Kkkkkkkkkkk
# memory ndi anoma anzako yakula ndinsanje m’malo moti muzikamba za Sulumba 5 goals 28 games mukulimbikira Geneza ngati ndiwa noma akugawirani ndalamazo, mufa ndi nsanje anzanu chikho ndiye tatenga mk15m pompo kuti dii
Bokosi iz better
Nyerere ndi dilu
Next time if there is a tie like this on top goal scorer consider there goal assist as well kkk
Nde mwati zonse zama penalty????? Kkkkkkk
Bola kufera mground.Inu mukafera kuti?
achukepo sangadye okha,bokosi nd big man
wa menya magame ochepa nde top scorer mauleeee boto kut buuuuuuu
wa menya magame ochepa nde top scorer mauleeee boto kut buuuuuuu
wa menya magame ochepa nde top scorer mauleeee boto kut buuuuuuu
Wakalamba nd iweyo memory, panga zako, ngati nd umbeta ufa nawo, ma player a bb sapana mahule.
Ngati Amubera Tengani Akhale Ndi 15 goals koma ref mukhale inu
Kkkkk walandila ndrama zingat??150, 000 neba ndye ukuona ngat amupasa ndrama zambiri eti nanga kuja adakatenga chithumwa kuja akapeleka chiyani ndramayo yachepa potengela ndithawi yomwe imatalikilla ka
Amenyerane Ma Pelnaty! Doro Apezeka.
Madolo samakhala awiri ndiye tnm ikonze tsiku la ma penalties between these two players..zaziiiiiiiiii
Chiukepo win golden boot ndatchulapo za coffin apa?
NebAtu. makomeNt. ako. ndi asanje. malo mogoyang,ana.
Kkkk chiukepo galu kwabasi
Chiukepo zamanyazi zuro kuthamangirj kwa ref kuti amulembe kuti wachinya chigoli kkkk ref ati wopanda mzeru iwe et?ukuwona ngati ndasizina?civo yazibaya yokha iyi hahahaha!chiukepo,fisher akapume akalamba awa azafera graund.
Wasowa zochia iwe et?? Osamalimbana ndi zisilu za Noma bwanji?
Chiukepo wakalamba?…u dnt kno what ure talking abt.
wa nsanje iwee,,chifukwa chake umangomwera tea wa mandimu mowilikiza
Kkkkkk wagwanayobe khalamba wanuyo R150 000 ingamupindulile chiyani nanga mwana adamukhwimila uja kwamakolo ake akapeleka chiyani sikhani zotukwana apa ai player yemwe amandisangalasa ndiuja munamupanga sadaka uja #Daga eish RIP INE NOMA 4LIFE BYEEEE
Munva kuwawa simunati aja ndima Champions…mulira kuti mpeeeeee!
Idiot!
Akunyoza Chiukepo ndiwa nsanje chabe , he always score for club and country siza Sulumba zija.
Memory nkhondo inatha bwererani kwanu ku mozambiq, mukuti sokoneza kwathu kuno. Munthu obwera chipongwe mkati bwanji?
Koma anamveysa chisoni munthu kulilira chigoli…..Chimdala chanuchi ife sichimatiwaza ndiponso amanveka ndimbiri zoipa heavyyy
Kodi agogowa asiyalit mpira
Ati akhwimire wina kaye season ya mawa.
Kkkk
Nanga ndi chani….musathe mau awa akunama. Chiukepo watenga K150,000 . Dzulo kaya Bokosi wanuyo atampase ndani kaya
Ulemu Wanu Guys Super Leag Ya 2015 Idali Yokhungana
Congrats, Wathuwathu Chiukepo
Shared how much?
kkkk ndie kuti amafuna kuba cha no. 15 chija madalawa ? Bokosi he is a gud striker awa zachulukitsa ndi zamapenote kip it up bokosi
ma penalty amangobwera popanda reason ?
Ndye ukut striker ameneyo hahaha dolo ndinzakeyo bas muone eye amupasa 100,000 ingamuthandize chiyani ndye mufuse bokosi kut walandila ndrama ndichani kkkkk muzizisata osamangodya mango ai ok
akuziwa mkona alekanitsa aona kuti enawo analowetsamo juju mpaka chinyengo mkati momwemo kkk
K k k k k ukhomelela ndizigoli zomwe eeee!!!!
Congratulation koma top goal score kumakhala ndi 14 goals mmmh not much good,
Ma game onse omenyedwa top goal scorer kumakhara ndi 14goals basi kkkkk koma chonchi mkumati frames ingafike pati mastriker ake bwembayu
Sudziwa zampira coz he did not feature in all games
Iwe ukufuna unene kuti chani ndikunena zama top goal scorer not kuti zigoli zikuchepa kuti akwanise kuteteza frames ndiye ngati iweyo ukuziwa zampira ukhare ndikuIndikira usanapange respond uzimva chomwe munthu wanena sindinanyoze prayer wa club kharani maso man
Iweso sunamve chomwe muthuyo wayakhula ka vomelezani kumalawi kulibe mastriker sindikutengela term yomwe ndimakwela ai komaso sindigwela term yamakepe ndatchula muthu apa ndye kape wina atukwane tilandana account uwonatso
Kkkkkkkkkk eti man ati sindiziwa pomwe kulibedi ma striker kkkkkk
Honestly ma striker ochinya akuvuta and its a world crisis mateam ngati Chelsea,madrid,liverppol Ac milan akufuna ma striker komano pamsika palibe
Zowonadi ayise ken
Makapewa tikamauza kur ndimbuli zampira samazisata koma kulongolola bas ndudu ndizomwe zikuwapangesa
Kkkkkkkk chingambwe too much
Ife tikuziwa kuti chiukepo d 15 goals cza 14 coz anaugunda mpirawo musamubere plz.
Kkkkk bola winayo
Congratulations to Bokosi and Msowoya for finishing as joint top scorers in the league.
kkkkkkk Bravo Bokosi Ur the best coz ur frnd yo, 7 zake ndi za Ma penalty he is not gd Striker than u.
Kuchinyanso penalty ndi udolo ngati ukachinya penalty sawelengera
penalty is a give away goal…. kuphonya mkufuna ……. star ndiwa ma runs yo…. bravo BOKOSI
Fotsek haters
ku team yanu top goal scorer ali zgoli zngat ? kkkkk or pa #chande osafka ha ha ha
mmmmm chilungamo chake dolo ndi bokosi basi, nanga zama panalty? or ine nthochinya
ukafuse tshabalala zomwe adaona ndi khune wa sundowns pa ma fina
ls a Telkom knockout. ngati zigori za ma penalty samawerengera wav
Ena Akut Chiukepo 15 Goals,bokosi 14 Nde Timve Ziti?
Amukhomerera Chiukepo
Amubera Chiukepo Coz Anaugunda Mpirawo To Disturb The Defender.
Zilibwino red lions moto kut buuu
Zilibwino, Maule Moto Kut Buuu!