Angolan man stabs Malawian woman 17 times in UK

Advertisement
knife-blood

In what is being dubbed as a horror attack, a Malawian woman believed to be in her early 20s was reportedly stabbed 17 times by a sharp knife by her Angolan husband after a dispute broke up between them.

The lady, a mother of three has been identified as one Lizzie Namukhopwa while the husband who is said to be in the hands of police is by the name, Antonio Francisco Neto, aged 45.

knife-bloodAccording to reports, the lady was stabbed in the family’s house in Teingnmouth Avenue in Collyhurst.

Manchester Police found the Malawian woman with wounds to her torso, hands and legs at her house on Wednesday, following an abandoned 999 call to an address in Teignmouth Avenue, Collyhurst, at around 11.15pm, international media reports.

At the moment, Namukhopwa is in hospital undergoing surgery.

“She was taken to hospital, where she underwent surgery for 17 stab wounds to her torso and legs. She is now in a stable condition in hospital.”

According to Press Association report in Lancaster Evening Post , Detective Chief Inspector Andy Cunliffe of North Manchester division said: “We have a team of detectives investigating this incident and we have made an arrest.

 

MORE TO FOLLOW.

 

Advertisement

146 Comments

 1. Koma how can you people say such negative things without having all the facts.Imagine if this was your sister and someone was saying those things.She was in a relationship with this man and he was the father of all her kids.Chili kwa nzako.
  Those of us who know the story tili phee

 2. Let this sound itself as a warning to those of you who have sexual desire with foreigners. Afterall, there r so many Malawians all over the world. Why not choosing one to marry? Umafuna kutchuka kuti wakwatiwa ndi Angola? Ndizimenezo, akanangokupheratu than stabbing you 17 times.

 3. Let this sound itself as a warning to those of you who have sexual desire with foreigners. Afterall, there r so many Malawians all over the world. Why not choosing one to marry? Umafuna kutchuka kuti wakwatiwa ndi Angola? Ndizimenezo, akanangokupheratu than stabbing you 17 times.

 4. Let this sound itself as a warning to those of you who have sexual desire with foreigners. Afterall, there r so many Malawians all over the world. Why not choosing one to marry? Umafuna kutchuka kuti wakwatiwa ndi Angola? Ndizimenezo, akanangokupheratu than stabbing you 17 times.

 5. This beautiful young well behaved girl your all talking bout here, was not poor and she did not marry this man for money but love and they had three kids together , she didn’t chose to be hurt by somebody she called her husband and father of her three kids, domestic violence does not pick whether your Angolan Malawian British Irish Zambia , instead of supporting your Malawian blood your busy talking trash bout innocent girl you barely know nothing about, instead raise awareness, end domestic violence, support the victims no matter what country from, end violence

 6. This is very bad.I don’t think there’s humanity in the man

 7. NDaKoDWA!!!!! popenza zachitikira kumeneko kuuraya!!! muchira, 17times amoyoooo kukadakhala kuno kuno kwa apitala iiiii chemwali bas kunali kumaiya 370 amabukhu akamuzu!!!! get well soon ccta

 8. Malawian ladies be careful even here in SA they losing they lives bcoz of love of money , the love of money is a root kind of evil , so we can say Malawi is poor nation ,but we are better even than most of south Africans u can go to rural areas in SA u will cry , no water , prostitute for money,so my fell Malawians let’s be proud of ur country

 9. Ndiye Mmalawi Ndikumudziwa Ine Ameneyu..Even 25 Times Stabbing Sangasithe Amukhonza Ine Ndikukanda Ndi Umbeta Zxachamba

 10. decision based on mkwiyo..its always the case..after hospital go and bailout your lovely husband.

 11. Sad but Malawians women and foreign husbands eish!!!
  Our women ought to be careful with who they get married to within and without!!!!

  Get well soon and hoping this bastard of a guy gets more years in gaol

 12. But I don’t understand akazi akwanthu ku Malawi, munthu angakwatire ndi mwamuna waku Angola. Amuna aku Angola adakale ndi magazi mumaso mwawo. Sorry for her but kumafusa zinazi

 13. Sorry for her!
  We should,on the one hand,blame neither her husband nor herself because we don’t know what actually caused the dispute.On the other hand,her husband had to take it easy until getting the right solution.My fellow Malawians,I beg you feel sorry and abashed for a situation like this because people out there ruminate that it’s because of poverty here in Malawi.

 14. yes we saw them here and they will never say I got married ,umva ndinamusiya amandivutisa olo amakonda kuredzela hahahaha lady from Malawi, pomwe mwamuna wake anamwalira,Sadzathekaso lady from Mpanje

 15. Mukutisiya ife mabatchala ,ku malawi kuno kutsatila amuna akunja ndye nd zimenezo muzibayidwa choncho.

 16. Sisters think before you get married with thugs you call sweethearts, they wil indeed finish you off. I do not see how an angolan man would be a good husband. Get well soon though

 17. Anyanya kukana amphawi anzawo koma kutsatira chuma komanso eeeh in her twenties bt three children and four granddaughters hahahahahaha magranddaughterswotu ndi amtsogolomo ndangowonjezera pomudziwa mkaziyu khalidwe lake

  1. Ndithu mmene ndikuoneramo mwinanso daughter mmodzi azapangidwa chipongwe paja history repeats,nanga inu kukhala ngati amuna kwathu kuno anatha kukakwatiwa ndi anthu oti anatichita chipongwe titapita kwawo komanso dzina limene lija ndakaika ngati ali wakumalawi pajatu pakatipa ma refugee amapeza ma passport akuno

 18. Nayenso mtsikana anaonjezatu, early 20s against 45, ndi zija zomati bambo akafuna kuvala kumutulusa kaye mkazi ali “tikufuna tivalireko kuno.”

 19. Ndinanena ine kuti; ma Angolan, ma Congolise ma Taifa agwirizana zowononga malawiii! Lero si izi. Komatu wa mkulu ali pompo

 20. Anthu Musamayankhule Choncho.Kutheka Ana Ali Nawowo Anali Ndi Bongololo Wina Wa Ku Malawi Kuno Mkumangomunamiza Apo Ayi Kumuzunza Ndiye Ngati Anakumana Ndi Waku Angola Wa Serious Akanatani??Sicholinga Cha Mzimai Aliyense Kuti Azibereka Ana A Mamuna Osiyanasiyana.Kuzunzidwa Kapena Kuthesa Ukwati Koma Zimangochitika And Anthu Pokwatirana Sakwatirana Kuti Azaphane Pena Kuvulazana.Akumatiotcha Matako,kumatudula Manja,kumatityola Mafupawa Ndi Amuna Akunja???Ngati Muli Pa Banja Labwino Just Thank God Mwai Siofanana And You Have To Know Kuti Others Out There Are Struggling To Get What You Have.Kusegula Miyendokonso Ambiri Amene Tili Okwatiwanso Ndi Amene Talowa Chisawawa.Kuchititsa Manyazi!!!

 21. Si aku Angola okha ali ndi mkhalidwe umenewu even akumalawi or dziko lose lapasi chavuta apa ndi umunthu. Not all Malawians r gud en not All Angolans r bad

 22. Koma abale kumalawi kuno kuli amuna ambirimbiri olongosokanso oti akufuna banja basi inu kuwasiya nkumakakwatilana ndianthu akunja oti kwawo simukukudziwa bwinobwino nde ndi izi zimene mmafuna kususuka basi!! Chabwino pepani poti ndimaliro aliyense alindinjila yake yochokera padziko pano, akause mu mtendele

 23. kujijilikako akazi akumalawi mukusiya zanu koma zaene nde kaya zanu izo kumeneko thanani nokhanokha mutiuza zotsatira zake

 24. ..makwatirakwatirawa..kumalawi kuno malawian single males milumilu oti utha kumamvana naye bhobho koma kufuna kutchuka kukwatirana ndi wakunja..kaya ndangonenapo ine..

 25. ..makwatirakwatirawa..kumalawi kuno malawian single males milumilu oti utha kumamvana naye bhobho koma kufuna kutchuka kukwatirana ndi wakunja..kaya ndangonenapo ine..

 26. malawian ladies do face such problem due to poverty where there is money they do open their legs quickly instead of knowing the person his habital way of life friendship is the first step of love amuna kumalawi kulibe kuti mpaka ukwatiwe ndi othawa nkhondo ok anyway get well soon #lizzie am wishing all the best

  1. nothing but the truth hate it or like but the truth shall set us free many girl do fall inlove when they see that there is money they dont count how old r u they do say age aint nothing but the number

  2. Admn is it that a way of introducing an agenda or what? I mean this is the second time to see the same photo on here with a differ topic. Tiuzeni zoona zokhazokha admn

  3. Let’s not be judgmental people. The man did not stub this woman because he is from Angola, or because the woman is from Malawi. Whatever wrangles they had, he stubbed her because he is wicked. Our very own who chopped his wife’s arms was not from a foreign country. He was (is) a pure Malawian breed. By the way, one does not marry a foreigner because of shortage of marriage partners in their respective countries, but because they’re in love (with the person, their money, or both). I wish her a speedy recovery.

  1. zafikiramo ndizofunika kumuthandizira, sangamvurazidwe pochitiridwa nkhanza up to 17 times, sizoona zimenezo! as we are malawians lets help one another!

 27. Maiko ena manja ndiodyera ndipo mpeni or mfuti ndiye chida chawo so azichimwene anu amathera ma mbama nde neba amangoombera or kubaya
  RIP

 28. Azimai nso akwathu kuno mdede, kungomva kuti mamunayo ndi wakunja basi kudzikoleka, mmaona ngati mavuto anu onse atha yet munthuyo sukumudziwa mbiri yake…..muzionesetsa mukafuna kukwatiwa azimai

  1. Aysha ma comenet ako umakonda kulemba zomwe zili mmutu mwanga ndiye tipange chonchi iwe uzilemba ine ndizipanga like basi

 29. Akazi a kuMalawi kutengeka ndi amuna obwera muli maBurundi ambiri mbiri mmaderamu akwatirakwatira aMalawi azikumana ndizimenezo coz anzathu mmaiko mwawo sakhala ofanana chikhalidwe ndi Malawi, abambo kuno akukumana nazo koma akumangopilira koma awo osaimvatu RIP

 30. ♪♪♪We’r th viiiiiiiiiiiiiictimz eeeevry tym. We gat double trouble eeeeeevry tym♪♪♪…… »»»singing«««

Comments are closed.