President Peter Mutharika has expressed the need for Malawians to uphold and respect human rights of all people.
Speaking at Masintha ground in Lilongwe during the commemoration of the International Human Rights Day, Mutharika said there is need for people to realise that everyone is entitled to rights regardless of their status.
Mutharika said it is time to overlook issues that have to do with differences in race, gender and other affiliations and focus on things that matter most.
“It is time to realise that everyone has the right to economic, social and cultural rights and there is need to uphold and respect human rights of all people,” said Mutharika.
He further said that people should remember to exercise their rights with a duty and there is need to have responsibilities for one’s rights.
He added that everyone has a duty to make sure that women, children and people living with albinism and other vulnerable groups also enjoy their rights.
The Universal Declaration of Human Rights was adopted in 1948 by the United Nations and aims to protect human rights of all mankind.
Thanks William Soza for your likeness on my comment.
Who is referring to
musatinyase za mwana wanuyo. osanena zina bwanji
apandiye waonjeza m’paka pamenepa
za ziii
Politicians need to respect us sure!
Ulemu sitipempha
Aaaaaah!!! Apitala muthalika osangonena straight bwanji kuti basi ma gay yambani kudalitsa maukwati basi ndi ma lesbians ukwati wa amai okhaokha fotseki go to hell ndi ufulu wakowo ihate u until idie r u real profesor or fake one? Ooooooh!!! Tidasankhadi olakwika mkasa sadaname
Nyapapi Wa mtsogoreli uyu Wa manyi khosi
Amalawi chachikulu tiyeni tipemphere kwambiri chifukwa kuseli kwa zosezi mulungu alinalo cholinga dzikoli.
koma nkhumba imeneyi itithandiza. ilibe ngakhale phatso yautsogoleli asaaaaa
Ine ayi mpaka kumanga muthu omwa mowa Malawi wayipa
Tamu uzani chimuthu chosavinachi chikutivuta ngati ng’ona woduka mchira
Zilibo
Himself is failing to respect malawian except the lomwes
Pitala ameneyo
nde ndikwatiwatu chaka chino
Ulemu umapita kwa anthu oyenera kulandila ulemu otsati kwa yense ndi Abwampini omwe
Ine palibepo chikundigwirapo mtima ayi. Zikakhala zogulitsa zinthu za boma anayamba ndi Bakili,
Malawi wathu adzavuta kuti alongosoke pokhapokhapo titamuyesa ATUPELE ngati president wadziko
I said something special I a gree, bt also make a country better interms of living
He should lead the example not just talking
Muno Mulungu analetsa zambili,nyama zina ndi zina,chiwelewele,kuledzela mpaka muli kampani yophika Mowa muno,mahule ali mbwee nyau zli muno,kuba kosiyana sitana,ndiye gay ingasowe polowela?
Bwampini ndi mbuzi zedi. Atitha amoyo amalawi.
Mukutanthauza chan a president???? Kod tiyambe kulemekeza maufulu ngakhale zimene akuchitazo nzopusa pamaso pa Mulungu???? Is dat wat u min, dat every1 can do watever he/she want,?? Koma r u not ashamed wt wat ur country is passin thru??? Wat du u think ts da root cause??? Is it not bcoz of all dis democracy thing??? Malo mot anthu apeleke ulemu ku mau a Mulungu mmalo mwake kukut tizilemekeza one’s democracy??? Mwalankhulatu mokuluwika kuvomeleza zinthu zina zolakwika apa….Malawi need to seek the face of God not all dis democracy thing…May God help Malawi….
Yah ! Apm must respect malawians rights not to privatise public health facilities.
Gays rights & lesbians.koma malawi basi anayipa.Iweso chitsilu eti pali za ufulu apa
Bwani peter akuphwanya ufulu wathu pogulitsa zipatala? Ndie pamasinthapo amanamaponso chani?
Don’t beat about the bush Peter, just beat the nail on the head that,malawians must respect the rights of the gays.I know that you are aiming at sighninig the rights of the gays and lesbians.
Pa 26 December nditulutsa mikango yolusa mu zinda wa Lilongwe apange ma Dimo ok
l think it an insult for mutharika to stand in front of Malawins advocating the need for respcting other people, yet he is violating our rights- that’s bullshit, he is not the right person on that capacity.
Tiyi sovaaa
The rights of fellow Africans especially Ethiopians you arrest every day..
Kumayenda kuno amalawi amangwidwa Daily man
Pitala akuti akufuna kugulisa phiri la Mulanje Guyz
Man peter aku thyolowa, kuyankhula zmenez?
Leadership is a gift frm Heaven not 2 much education.
Nde mukufuna ndani?
Angotula pasi
Zoona
koma ameneyi, akufuna akagulitsa atisiye pamoto iye azipita kwakalambira iye tisamale amalawi, apa ndiye zafika pa zero
tizisekelera zilizonse or ukufuna kutigulitsa ife mano pamtunda ? usiye kugulitsa zithu za amalawi fe den tikulemekeza Iweso ulibe ufulu ogulitsa zithu za amalawi
bwanji timuchose uyu! ndiloleni ndiyambise abale.
No comment ine ndim’mozi mwa amene munatimanga kumangochi Titapanga dem kuti Pete wanuyo asankhare msogoleri munya muona
zimenezo ndizibwana zamchombo lende petir kod wachokera kut iwe ndiwe malawi
zisamaone mbali imodzi. practise wht u preach mr APM.
Zalowa chibwana zili ngati ufumu koma jah akutaima
Search me chilipo chikuzemberedwa apa ena agwidwa just this week same week kumayakhukidwa mau ngati awa
tilemekeze ufulu wa anthu ena zauchitsiru uwunso ndiufulu kapena 666 zimene mukuzembera tikudziwa kale there is no secret under the sun
Eya nde ufukuwo kaya
iwenso pita uko palinso ufulu apa kapena #satanic
Mxxx ufulu upose umene Mulungu adapereka kuti mkaz akhale ndi polowa komanso mabere ; mwamuna nsonga ndi mazira kuti awiriwa akhutitsane kotheratuu????
Chonde mutilankhulitsa pa mphuno kamwa tilinayoo….
absolutely right Your Excellency but not on GAY RIGHTS….. NO 100%
Dzuwa!!!!
kamuzu adali wopusa pomanga zipatala zaulere ,pitala nkukhala wanzeru mpaka upanga plan yogulitsa zipatala zaboma
>3
KENDO.uthenga wangotipeza posachedwapa kuti pitala akugulitsa shire river.Pitala wasowa zogulitsa tsopano
#Ghettoyuttie samalowelera ndale
Usless president…kungoziwa kugulisa. katundu wa mnyumba…