…only 6 hours of electricity in a day
The current electricity situation is expected to go from bad to worse in January once the Electricity Supply Corporation of Malawi Limited (ESCOM) decides to implement its plans that will see the closure of Nkula power generating plants, media reports have said.
According to the reports, a leaked document in which ESCOM met with Corporate organisations has revealed that ESCOM briefed them that it has plans to completely shut down one of its plants, a situation that will see electricity production reduce drastically.
“The climax of electricity shut down will be in January when they will scale down for two weeks,” the reports say quoting the document.
It is said that ESCOM has warned its valued customers in the Corporate world who contribute 44% of its revenue that in January 2016 they should brace for tough times.
It has been established that among the things that ESCOM suggests will happen with the closure of its power plants is that there will be only 6 hours of electricity in a day to its customers.
ESCOM however hinted that it is contacting Mozambique and Zambia to support it with electricity regardless of the fact that Zambia itself is failing to supply electricity to its citizens.
Currently, Malawi is battling with the worst ever power cuts. People have accused the DPP led government of failing to manage and contain the electricity situation which has continued deteriorating. President Mutharika has advised that the situation will be contained after three years.
It is said that ESCOM will shut down both Nkula A and B for 12 days in January then it will move to alternating the shut down between the two Nkulas meaning that the situation is not changing anytime soon.
Anyani!
https://motherlandfatherland.wordpress.com/2015/10/29/fight-the-power/
Katoto,mchengautuwa,area4 Ku mzuzu athima 5am, kwanuko nanga?
nyan iyi yiti vuta koma , why
Malawi suuuuuuuuuucks!!!!!!! Got a frend lived in the US lyts only went out once in the 13 years he’s been there. Crazy stupid Malawian Old leaders! Nigga can’t even tok proper. Y’all voted for trouble. Anthu enawa ngati ungowaombela utakhala ndi mfuti! So boring. Devilish individuals. Damn
Nanga kutan kongogulilatu ma caddle box la machesi
Eeeesh guys escom kayaaaa
This is not a promise its a threat!!!!
Eskom! Ukuona ngati ukamazimitsa magetsi zimatisangalatsa? Uli ndizifukwa zambiri zimene umatiuza. Kuteloku mumalemba anthu ntchito kuti azikazimitsa magetsi basi! Heeeee
DPP munalephera/mukulephera ndipo mudzalephera
Towards no power all day everyday
eish JB must come back again kukanakhala mai ssibwez izi zkuchitika
Panya pao
Escom, Escom for how long shall imention your name..poor company ali mkanzi,eeeeeee galu weni weni…
indi Peter kawulisani amalawi ndiwomwe anakuyika pampando,akazatopa nawe azakuchosaso.akuwulidwe kwambili a DPP,
Ngati kuli kukoza zinthu kuti zikhale bwino patsogolo sitidandaula koma ngati alimasewela muzativa mtchere
mulibenso manyaz mwez ukadutsa osalipla mumabwer nkumat mudzadul magec chonsecho mumadula dairy
#PamtumboPawo Agalu Amwenewa Akutiwonjeza kwambiri Chosecho Timalipila2 Koma Fck di State
Kodi bwanji boma ili limakhala ndimavuto nthawi zonse, mtundu waminyama ngati uwu sindinauwone ndiye bola ma masten ajatu? Vote yanga ndinabesa ndionana 2019 basi.
Shit z ova iwe pitala patumbo pamako wava kod unalowelanj galu iwe chimulomwe , chimulomo ,chimutu mbunz yamunthu
Iweso wausilu et mesa alomwe nd amene akuonong dzikoli as ov nw thaw ya mai kunalibe matudzi amenewa fokolo
Agalu amenewa ine andithina bwanj aaa bas its beta kungokhal wthout electricity
Sounds pretty bad
Apa nde mwationjeza kd vuto nchani a escom dairy magetss kuthima mmm bola mnthai ya mayi aaaa
Zachamba basi!
F**k ’em
Hope mw z deterioting y nt ppppppuuting gud measures 2 elecrify de problem foolish
Chilala chamagetsi koma kuba Boma basi
Tandionetseni wa escom apa!! awone tsoka….!!! zopusa eetiii!!!!
Yaaa ! Ndilikhe mitengo nditakate makala tsopano.Nde wina aziti potopoto kuzandifusa ngati mitengoyo ndi yake ,ine ndiziotcha ya chilengedwe basi yomera yokha . Zavuta ku likuru.
Malawi amalawi ndalila nsopano ndatopa nanga nditani poti ndilibe podalila ophuzila ali kutipondeleza ndipita kwina ine ndizabwela Pitala muthalika akazachoka bolani jb unja ndapita
pajb panalibe mablakout why now
iyi ndi escom ndimadziwaine imafuna malawi tidzifanana monga amalawi pasakhale kusiya wakumudzi ndi watown
zmnzo ndy zachamba wamva iwe.kukhar alOmwe T DOZNT Min qt akuknder maudindo wamva!sunave qt watr table yaska? usilu et..
eeeeeesh zobowa heavy
Nothing new.
eeeh koma
Magetsi akumalawi amayakayaka coz amakhala ozima alwayz
It shos wina wajomba kuntchito,y magetsi sakuzima? Asamalengeze akafuna kuzima but wl make sense azilengeza akamayaka coz thats something strange.
electricity bills and blackouts will be canceling each other nsaone wa escom akubwera kwathu kuzadula magetsi. tizakhapanapo
nde muzikamba za development wth ths rubbish.electricity on itself is the development engine.
Vuto ndi boma,nthawi zose ulamuliro wa Dpp magetsi amavuta. Akafuse nzeru kwa JB kuti adatani kuti magetsi asamavute. Ngati zakuvutani tulani pasi udindo, wena akoze dzikoli musatizuzepo yapa.
bola thawi ya masten. we mis u mama m
Pathako pao anthu amenewa ,chimene amatha ndikudula magetsi mwachipongwe koma satha kupanga supply magesi!!!!!
Pathako pao anthu amenewa ,chimene amatha ndikudula magetsi mwachipongwe koma satha kupanga supply magesi!!!!!
Koma kugula magalimoto a mabwana opanda nzeru pa ntchito basi.
bac guyz ma expert odziwa zamagesi ngati ine tiyeni titsegule company ina awa atizudza ko kwanira zachamba tizigaisa kuti apa nde wakumudzi bac
Mitengo ndie makape amenewa kukweza alaaaaa,kma nd zxilu.
This is right time to be connected with mozambique electric
Imeneyi ndiye escom ndimaidziwa ine, mwaiwalatu kwathu kuno kuthimitsa
What a shame to our ESCOM….sunny time you complain,”comes rainy u complain about mud….where can we go now.
Ma engeneer akuphunzira and graduating every year ena mwa iwo ali ku Escom konko koma tizingokamba nkhani imodzimodzi yomweyi zoona? Dzulwa lonseli, why not going the solar way and suppliment, what about the winds we have browing us every day. kumakafikaku ntchito tili mbuuu! ma windmills amapangansotu magetsi. Tidalire Shire basi? A Escom mukuwerenga chani masiku ano?
Very Sad Koma Muone Magalimoto A Mbuzi Zimenezi Kuchuluka Koma Kumalephela Kukonza Dam Shame Cashgate Iri Paliponse.
akumudzife tilibe nazo vuto zimenezo ife tidazolowera kugula mabatire parafini ndima kandulo kutchaja foni masola olumikiza ndi inveta moyo mkumayenda… Kumudzinso mkwabwino et i dint knw
yaah umfaso timasinja pa mwala ife
Nde wakwela pa pholoyi akutanipo?
I promise you a blackout, eesh! promise!
U said promises
khalangati apanga collabo ndi the candle company bwanj?….eish osapanga fixed date kuti pofika dayz iyo magetsi azakhalapo…koma ey treating us like trash…..we R customers!!!!!!!….n the customer is always right
Palbe Zacilendo Magetsi Anazima Kalekale Amangoyaka
Koma Kumalawi!!!!!!!!!
Apa nde kuikana CHIMWALA pansanaaa tu…….
boko hallamu ya ku malawi
I am kenyan and i need 10 frnds frm malawi please like my cmnt or send frndrquest i add you to my frnd list.Thangs in advance
aaaaaa thats what iwanted kkkkkkk ……
very promissing indeed
Eeeehh eeehh mpaka promise more blackouts??? Nde palibe chabwinotu
kkkkk nde muziti Kamuzu palibe chomwe anapanga. Mkula mukulephela kupanga maintanance wo anapanga ndindani?
Help Lord!
Fire Dem Again Muzachose Chigwechanuci Lero Ndimadana Ndi Zausilu
Zopusa Ai Apa Mukuona Ngat Zikutisangalasa Mbolizanu Nonse(escom Diss)
A Solar Power please am serious, ud u come to my inbox? Or anyone knows about solar power company, please help me.
All of these things are because of that former nkhalamba ija for burning the ESCOM house. Munthu oipa, kuipa, choipisitsa
I think sora can be the solution of this problem
@[0:order of de day,tinazolowera moti tikumadabwa kuti why magetsi akumayaka for 2hrs,mungothimitsiratu for a month kuti mukonze bwino,,fodyaaaa basi]
Bola solar panel tsopano
Koma Alex nde wandikhwacha….ayiwone andalewa kikikikiki,daily basi nkhani zosathandiza komakadzikoka ii!
Tisamve zopusazo,mmalo mokonza mavuto mungoonjezera chifukwa chani?Ndinu zitsilu nonse ku Escom pamodzi ndi mtsogoleri wanuyo tatopa nanu tsopano SHIT!!!
This is rubbish, Escom are only shutting down Nkula A&B in August 2017 for upgrades. This is when we will have major problem with power. My advise is get solar .
there is nothing to promise here.
Shaa!! Koma ma bill nde azitipatsabe ma sauzande, mmm gulitsani company yi anzanu alongosole zinthu..tatopa nazo Ife izi
why always malawi? Magetsi + njala is equal to death.
Kufa kulipo.
nde bolanso joyce banda..if it wasn’t for cashgate leak..we weren’t experiencing this shit..mwationjeza kwambiri, ndipo osamayasa kuli koyela bwanji nkumathimitsa usikuwo
Ena ndiye mukaona anthu anyamula makala mumalanda, ndiye tiuzeni tizitani tikafuna kuphika ku malawi kuno?
Eeesh! Towards black out everyday.
Ndikatukwana muziti ndachimwa peter muthalika pamsana pamako mapazi ako pa mt….. Pako
These people of escom have dilapidated cerebellums that they are failing to develop valid reasoning on how to excavate the practicable predicaments presently available , thats too absurd to malawians
최주용 disappointing promise of ESCOM. T.T electricity for only 6 hours a day in Jan.
Mvula ikayamba kugwa timva ayi shire wadzadza matope chifukwa cha mvula nde makina akukanika kupukusa…. ayi ujeni…..
Vomelani kuti Malawi si dziko lokhalako ma foreign investors.Ifeyo tinazolowela basi.
chilichonse mavuto, whts this?
Koma nanga mumabweleranji ndi zi ma bill zandalama zambiri? Chikhalirecho magetsi sakuyaka?
Hahahaha! What a promise.
Zawonjeza koma
Koloboyi ndie bwenzilanga.
Kukhala m’malawi mkulimba mtima.
Then after that you will tell us that price of electricity is up again
e so called engineers mukugwira ntchito kumeneko.amadziwa ndi kuzimitsa
koma yah
ahaha at promise
hehehe..achita kupanga promise
its high time gvt must learn to appreciate that liberisation in the energy sector is important.again,the gvt must sure that those entrusted with running ESCOM are competent enough& patriotic.if u go around BT& Lilongwe,u will see many new Toyota Hilux with ‘B’ registration #s belonging to ESCOM.seriously,driving new vehicles can not be priorotised at the expense of malawians economic welbeing.energy is a hub of malawis economic sustainable development
SOLAR PANNEL NTHANDIZE,,,TISAVUTIKEPO NDI ZAMDZIKO IZI
Kodi ku ESCOM kulibe ma planners? I believe any type of machine amakhala ndi lifespan b4 they depreciate to zero. Amadikira equipment iyambe dzimbiri? For them to upgrade? Shame on the big boss
and the biggest boss too . .
Lame promise
Thus malawi !! bwanji tingoligawa dzikoli into 3 ?
Atwonjeza amewa kuno chzmilen cha dzulo xanayakebe
tina bhadwila mu nyali…zimenezi sizikutikhuza
Hop the Electricity Bills will also be reduce due to those 6 hour/day if not then ur loking for my troble…waiting…
Akabwela Kwanuko agendeni a Escom Atikwana kwabaaasi.
Iiii basikwathuko muchotse magesianuwo tizipanga asola yah, mwachitabwino kutiuza tikhale ndizigayo za dzl basi
incompetence leadership
Tinazowera Sizachilendo Agalu Amene Ationjeza There Just Trying To Find Excusses From Road Shadding Now Tikuika Mapolo Later Nkula Wazaza Ndizinyalala Bola Kuma User Makoloboi Alla Shupiti Ndakwiyananu Mukanene Kumene
Panyapawo
Kayamumati proffessor kutholo konko za u proffessor iyaaaa!
Shit it is better to have no electricity in Malawi; we’ll use charcoal.
Bora sora dzuwa nd daily
Are they telling us kuti January kudzakhala shire ali ndi low H20 level.
Vote for candles en paraffin u will never regret.Abale athu akale kale dziko likadali ndi mphonje
Not acceptable, where is your plan B. How do we operate industries
Government should fire the Authorities because they have failed.
we ar now used to load shedding in zambia.
ngat pali company yomwe ikuyenela kuchita manyazi pa malawi pano nde ndi escom..ikupanga zinthu ngati ili maliseche
Bola Angoyigulisa Anzawo Ayeseleko Izi Ndiye Za KuMache……….Tatopa Ife
Ndiye Kumalawi Kumeneko. Lets Introduce Wind Energy
Gosh!!!!! Than this worse?????????????
Ma bills azizabwerabe ma thousands chonsecho ukungounikira basi
Ndiye azibwera ndi ma bill andalama zambiri koma magetsi sakuyaka a boma angolola ma company ena abwera tatopa nazo izi every day Malawi 24 comes with bad news zachamba bwanji.
They have to change their name from ESCOM to Darkness Supply Commision of Malawi(DSCOM)!!
Amalimba mitima ndikumati towards power every day malo mwa toward black out every day
anthuwa kuwatengela ukhoza kusemphana ndi ufumu wa ambuye
Maybe it must called Electricity Shortage Commission
Maybe it must called Electricity Shortage Commission
Akanamati timasankha kobadwira Malawi bwezi ali Nkhalango ekha ekha!!!…..tinabwera kudzavutika ku Malawi kuno!!
good news to our president n his entire cabinet
Even if you say 23 hours
palibe chikuenda ku malawi
Marian Forkin
Chifukwa chani bungwe lazamagetsi lilipo limodzi la ESCOM basi. Pakufunika papezeke bungwe lina laphavu ya zamagetsi. Ndikukhupilila kuti vuto lazamagetsi lizachepa kumalawiko.
Asachite kutiwuza Mesa zinayamba Kale Kale zimenezi? Shupiti!
Welcome to Malawi.
Welcome to Malawi.
Thank u
Gloria wamuona Thipa angozimitsa magetsi uku.
Kkkk ndmuuza akumenye
Umuchosetsa mano, kiki! Kodi anasiya ku limbe kuja?
ESCOM promises more blackouts……am speechless.
kkkkkkkkk amalawi limbani mtima mavuto sakuchokani aapa bas eish koma yaaaaa
It means 10 days ov elelectricity nd 20 days ov bblackout in a amonth.
Lol!, what a promise!
paja magesi akuno ku mw ndiothima amachita kuyaka,sizachilendo izi
Malawi at 50. Ndiye chi president chingoyang’ana bac. Zachamba
Malawi a day can’t just pass by without bad press .
ESCOM promises more blackouts……. zasiru
Dziko lokanika chilichose ndili kuno mpaka pitala azachoke pampando nde kubwera kwaine
Kodi mesa mumkati ndi katakwe? Zataninso kodi? We need wise leaders not the intelligence ones.
Ine ndinavotera UDF sindingavotere anthu opanda nzeru ngat amenewa tiyen tingotchonapo apa
Kkkk!olo titatchona adzasankhabe zokhazokhazo basi.
khope zothandiza zili ngat zimenez kuipa ngat njila yakumana kkkkkkk
Kkkk! Mumangidwa nazotu!
ZACHAMBA!
Amene Kwawo Magetsi Samathimathima Saali Mfasho
I think other companies should come in Malawi. and invest in this service. Awa alephera.
lol…. Now they are making promises for problems??????
why can’t u plant ur machine in likhubula bcoz dis is shithine
Uku ndiye kubelana tikuona ndi maso magetsi adakweza koma sayaka?
the heading sounds as though its something positive
Angozimitsira2 bax apa tazoloweranso kukhala mu mdima nanga magetsi kuthima 4am kuyaka 10pm,nanga anthu omwen amadalira magetsi kut agwire ntchito zawo atani,nanga mmakomo mwawo hw do they survive,am totally disappointed with this situation
Mmmm ai ndthu
Expect stages of loashedding .Malawi now is becoming more scary.
My Malawi My ESCOM
Nde ma bill azibwela openga adzalipila achimwene
Nde ma bill azibwela openga adzalipila uncle ndukuuza
we don’t want ur power plz, we now using nyali za paladin.
The headline should read:Escom warns of more black outs,not promises. cheap journalism.mwxxx
Nde mbolatu. Mj akumathima before 5am nkumayaka madzulo. Anthu azigaitsa nthawi yanji pamenepa?????