![Electricity Outage](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/04/Electricity-235x176.jpeg)
Magetsi mpwechemphweche ku Tanzania mpaka achita kuthimitsira matchini
Pena ngati upemphe kwa a neba kuti mwina angotibwerekako wawo, ife tiwapatse wathu. Chifukwa zimene likuchita dziko la Tanzania ndiye eee ndi zodabwitsa. Patangopita masiku pa makina a intaneti dzikoli litadya wani ndi sitima za… ...