M’busa Yasin Gama ‘akugendedwa’ polalikira za omwe amabwera ndi mabigili pochoka ku South Africa
Anthu ena akwiya ndipo akulavulira za m'kamwa m’busa Yasin Gama kaamba ka ulaliki omwe amadzudzula anthu omwe amabwera ndi zinthu monga mabigili otungira madzi akapita m’dziko la South Africa. Lolemba sabata ino, a Gama omwe… ...