
Anthu ku Zomba ati zinthu zikuvuta chifukwa MCP ikufuna kulamula yokha
Anthu ena okhala mu Mzinda wa Zomba ati zinthu mdziko muno zikuvuta kwambiri pankhani ya achinyamata kupeza ntchito, njala komanso kukwera kwa zinthu chifukwa chipani cha MCP chikufuna chidzilamulira chokha osafunanso kumagwiritsa ntchito mfundo zachipani… ...