Bishop wa Diocese ya Chipata wadzodza ma Deacon 20 kuno ku Malawi
Mwambo wodzodza ma Deacon 20 ampingo wa Katolika udachitika Loweruka ku St Peters Major Seminary mu Diocese ya Zomba ndipo adatsogolera mwambowo ndi Bishop wothandidzira mu Diocese ya Chipata Mdziko la Zambia Ambuye Gabriel Msipu… ...