Kwavuta kumsewu, mitengo ya zilango yakwezedwa
Pofuna kuchepetsa komanso kuthana ndi ngozi za pamsewu mdziko muno, boma podzera ku bungwe loyang'anira za pansewu la Department of Road Traffic and Safety Services lakweza zilango kwa anthu olakwira malamumo a panseu. Izi ndi… ...