DPP sidzabweleranso m’boma ndipo 2025 Chakwera awina ndi 70% – Chimwendo
Fikitsani uthengawu ku Mangochi kwa a Mutharika: zobwelera m'boma ndi maloto chabe, a Malawi onse maso nga! pa Chakwera, watero ndi nduna ya Maboma Aang'ono a Richard Chimwendo Banda. Polankhula potsekera zokambirana mu nyumba ya… ...