
Chizindikiro cha chipani chatsopano chiutsa mtsutso
Mtsutso wabuka pa masamba a nchezo pa nkhani ya chizindikiro cha chipani chomwe changobadwa kumene cha People’s Development Party (PDP). Chipanichi, chomwe mtsogoleri wake ndi membala wakale wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP), Kondwani… ...