Boma lakhazikitsa mtengo watsopano wa chiphaso choyendera
Boma la Malawi kudzera ku nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka mdziko muno ya DICS, tsopano yakhazikitsa mtengo wa K50,000 ngati mtengo wa tsopano wa chiphaso choyendera cha anthu wamba. Nkhaniyi ikudza pomwe nthambi… ...