
Aphungu ambiri akumajomba ku Nyumba ya Malamulo
Zadziwika kuti aphungu ambiri akumajomba ku Nyumba ya Malamulo pamene dzulo aphungu okwana 141 anajomba kunyumbayi. Pa nthawi yoitana mayina m'modzi m'modzi aphungu 51 okha ndi omwe anabwera. Mtsogoleri wa zokambirana mnyumbayi a Richard Chimwendo… ...