
Kunabukanso moto ku Nyumba ya Malamulo
Kunali chipwilikiti ku Nyumba ya Malamulo kum'mawaku lero pomwe ena mwa anamandwa opanga malamulowa amafuna kuponyerana zibonyongo. Chatsitsa dzaye nchakuti pomwe Madalitso Kazombo, wachiwiri kwa sipikala wa nyumba ya malamuloyi analengeza kuti oyimilira aMalawi-wa akatchaye… ...