A Malawi akhazula Med C

A Malawi ang'alura katswiri oyimba nyimbo zamakono Medson Kapeni amene amadziwika kuti Med C, kamba kakhalidwe lomwe waonesa kuti asiyane ndi kampani ya Magic Fingers LL yomwe imamuthandiza. Malingana ndi malipoti, mnyamata yu sadapite kojambula… ...