Bungwe la MEC lati kugwiritsa ntchito zipangizo za boma pa misonkhano ya ndale ndikosaloledwa
Bungwe lowona za chisankho mdziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lati kugwiritsa ntchito zipangizo za boma monga galimoto pamisonkhano ya ndale yokopa anthu pachisankho ndikosaloledwa ndipo bungweli lati aliyense opezeka akuchita izi adzayimbidwa mlandu.… ...