Fisi anakana msatsi: Bushiri wazitaya, akuti zamukwana
...wakana anyamata awiri omwe anafa pangozi... Mneneri odziwika bwino Shepherd Bushiri wati zamukwana komaso zamutopetsa zitonzo zomwe akulandira. Bushiri wanena kuti ndiwokhumudwa kwambiri ndi zitonzo zomwe akumuchitira anthu m'Malawi muno. Bushiri yemwe ndi mwini wake… ...