Mumangidwa! Khonsolo ya Lilongwe yaletsa kufukula mchenga
Ngati mumafuna kupeza kakhobidi kudzera m’magobo ofukula m'chenga komaso miyala mkati mwa nzinda wa Lilongwe, pezani zina zochita kamba koti khonsolo ya nzindawu yati ikuthirani dzingwe. Khonsolo ya mnzinda wa Lilongwe yatulutsa kalata yomwe wasayinira… ...