
Pasuwa wayitana anyamata kukonzekera CHAN
...Ekhaya yasonkha nawo... Timu ya Ekhaya yomwe yangolowa kumene mu mpikisano wawukulu m'dziko muno yasonkha nawo osewela pa mndandanda wa anyamata 25 omwe mphunzitsi wa timu ya mpira wamiyendo ya Malawi Kalisto Pasuwa wayitana, kukakonzekere… ...