Nzika zauza Escom kuti ikonze magetsi pasanathe maola 24
Gulu la nzika zokhudzidwa ndi vuto la magetsi ku dera la Majiga 2 m'boma la Balaka lapeleka maola 24 ku kampani ya Escom kuti likonze vuto la magetsi lomwe akukumana nalo. Gululi kum'mawaku lidachita ziwonetsero… ...