President Lazarus Chakwera in Egypt in November 2023

Chakwera akubwera lero

Mukaona mbendera petupetu, magetsi waliwali komaso apolisi atayima m'misewu, dziwani tate wa dziko lino wafika kuchokera kunja; a Lazarus Chakwera akubwera lero komatu apeza zinthu zambiri zakwera mtengo. Kapena a Chakwera abwera ndi mayankho? A… ...