
Aliyese ali ndi ufulu osintha chipani – yatelo DPP
Chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) chatsimikiza za kutuluka m’chipani kwa a Dalitso Kabambe, koma chati sichikudandaula ponena kuti ngakhale banja limene limatha ndipo aliyese amalowera kwake. Potsatira kalata yomwe a Kabambe omwe anakhalaposo… ...