A Malawi kuchulukana ngati mchenga: ana 1,628 abadwa tsiku la khisimisi lokha
Pokwanilitsa mau omwe amapezeka m’buku lopatulika pa Genesesi 1 ndime ya 28, lomwe limati; ‘Mulungu ndipo anadalitsa iwo, ndipo adati kwa iwo, Mubalane, mucuruke, mudzaze dziko lapansi,’ zadziwika kuti ana okwana 1,628 ndi omwe abadwa… ...