![Pope Francis has approved the blessing of same-sex marriage in Catholic Church](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/12/201021-think-pope-francis-ew-439p2-235x176.webp)
Papa wati mpingo wakatolika uzidalitsa anthu a paubwenzi wa amuna kapena akazi okhaokha
Papa Francis waloleza mpingo wa Katolika pa dziko lonse, kuphatikizapo kuno ku Malawi, kuti uzidalitsa anthu a pa maubwenzi a amuna kapena akazi okhaokha. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe yatulutsa ofesi yoona za malamulo… ...