![Malawi Mozambique](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/01/Mozambique-Malawi-border-violence-2-276x176.webp)
Mkangano wa malire: Anthu aku Mozambique atchetchaso chimanga cha a Malawi ku Makanjira
...phungu wadandaulira boma kuthetsa mkangano wa malirewu Pomwe pali kale chiopsyezo cha njala yadzaoneni chaka chino, apolisi komanso anthu a mdziko la Mozambique, pa 17 January, 2024 komaso usiku wa loweruka lapitali, atchetchaso chimanga cha… ...