Malonda a ng’ona avuta, ati maliseche ake akumapangila gondolosi
A Malawi ndi kutheka tipeza msika wina oti utenge malo a malonda a fodya akuvutavutawa. Mmalo mwa fodya, mwina tizingogulitsa ng’ona za mphongo basi. Malipoti ochokela mu dziko la Egypt ati ng’ona za mu dzikomo… ...