Chakwera ayankhanso Mutharika: ulamuliro wanga wakumana ndi zokhoma zambiri ndi chifukwa ndalephera
Iyi ithera ku waya ndithu. Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera akuoneka kuti sanathane ndi moto omwe owatsutsa a Peter Mutharika adayatsa ku Blantyre lamulungu lapitali pa msonkhano wawo wandale. Adakapitiriza kuwayankha mokuluwika. Lero… ...