![Mr Ibu](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/03/John-Okafor-Ibu-276x176.webp)
Thupi la Mr Ibu lalowa m’manda
Patadutsa pafupifupi miyezi inayi (4) chimwalilireni, thupi la katswiri pa nkhani ya zisudzo m'dziko la Nigeria a John Okafor omwe amadziwika kwambiri ndi dzina loti Mr Ibu, layikidwa m’manda tsopano. Thupi la Mr Ibu omwe… ...