Palibe kothawira, nayo kampani ya Salima Sugar yakweza mtengo wa shuga wake
Kokapumira ndi kumwamba basi. Patangotha ma ola bungwe la Blantyre Water Board litalengeza kuti lakweza madzi ndinso kampani ya Illovo italengeza kuti shuga wake yakweza, nayo kampani ya Salima Sugar yalowa m'bwalo pofuna kuonetsetsa kuti… ...